😂😂 bro you got ma fact opangitsa munthu achokeko kuno
@ivychithyoka1551
5 ай бұрын
Tikuvotera Apm
@martinnyirongo2892
5 ай бұрын
Chakwera ndi chilima ai ma crook awa, atipweteka kwambiri. Bola apm bas.
@OsmanOsher-sh6gp
5 ай бұрын
Man SKC must be given Coz He is a wise Man
@NovemberMmangathayo
5 ай бұрын
Chilima ❤❤❤
@petermsamariamapira8933
5 ай бұрын
Koma munthu wamkulu muli very strong 💪, walk long journey ❤
@AbrahamLLoyd-xb2xc
5 ай бұрын
According to what has transpired during the reign of Lazarus Chakwera, the man of God himself, Malawians could never ever repeat the same mistake again by voting for another man of collar.
@ChomboNgosi
5 ай бұрын
Chilima my vote
@EnochleonardMwale
5 ай бұрын
Palibe cha nzeru apa . Pitani kameteni ndevu zanuzo . Chakwera 2025 Boma .
@ShukuSh-vi1hk
5 ай бұрын
Iwe ndi chakwera wakoyo nonse nda garu
@KellyHart-pi4hd
5 ай бұрын
❤❤❤❤ bro mumagaya ndipo ngochepa Ngati inuyo big up
@mutafire
5 ай бұрын
hahaha mwatipopa...cheers
@petermsamariamapira8933
5 ай бұрын
Mukulankula zomveka bwino kwambili, i do like it keep up
@NchebeMilliyano
5 ай бұрын
Zausilu
@francismhone3086
5 ай бұрын
It's the last words for me😂😂😂
@binalidjeyshabahzombamalawi
5 ай бұрын
Apm ❤
@edgarlastone
5 ай бұрын
Uthengawutu ufunikila ufikire anthu mumakayamu anthu sakuziwa choyenera kuchita very true angot ndine mulomwe votera DPP ndine wapakati chipan chamakolo MCP or utapha anthu sangayisiye yyyyyy koma malawi tiziti umbuli or ndife ozikonda
@vitumbikocobysinyiza-5116
5 ай бұрын
APM my vote
@jacobranuga
5 ай бұрын
Why u didn't talk about UDF chipani chomwe chili number 3
@mutafire
5 ай бұрын
Ndinati ndikamba za serious okha okha
@RiteRoderick
5 ай бұрын
APM woyeeeeeee ❤❤❤❤
@LovemoreSalima
5 ай бұрын
Kodi or ukusokosera choncho ukuti akusankhile ndani poti ukuoneka kuti suli kuno?
@prudomaninc7643
5 ай бұрын
Nde mukati tisavotere chakwera nde tivotera ndani? Enawo nde michabwa yeni yeni
@wilsonbanda5260
3 ай бұрын
Ku china nako ma overhead cables kungoti mbwee kuposa ku Malawi
@MatthewsLungu
5 ай бұрын
I thought you will suggest the right candidate Malawians must vote for this coming 2025.
@mutafire
5 ай бұрын
Malawians already know...and it is not the best candidate they want, they want the one from kwawo.
Iwe ndye chimene tingakuwuze ndchakut Mutharika alowaso ubwino wake avota alikumalawi osat ku Chain 😂😂😂😂
@Posterplumbing
5 ай бұрын
Ka uku ukuyenda uku ndiku china?
@mutafire
5 ай бұрын
yes, decided to showcase mbali ina...but as you can see, i turned a corner and the city appeared.
@FrankMkwala
5 ай бұрын
Yes yes boss Joyce wanaononga ziko
@jamesgama5489
5 ай бұрын
Kodi ukumenya ka road work ase, chilima ndiwa timing. Ndale zaku malawi zimayendera region kapena zigawo example ayawo sungasunthe ku udf achewa nde mcp ndi yamagazi atumbuka aford ndi chipani chakwithu alomwe nawonso anapeza chawo chipani cha dpp. Pamene utm ikusowa strong hold ndikuthokoze umalankhula.za nzelu.
Пікірлер: 168