On Nyasa VoiceBox, Pastor G. Tembo reminds His Excellency the President that his presidency is based on trust. Without the people of Malawi, he cannot be President. Therefore, it is imperative that he condemns the violence being perpetuated by the MCP Youth.
Pa Nyasa VoiceBox, Pastor G. Tembo akukumbutsa a President kuti udindo wawo wa utsogoleri ndi kukhulupirirana. Popanda anthu aku Malawi sangakhale Purezidenti. Choncho, mpofunika kuti adzudzule ziwawa zomwe zikuchititsidwa ndi Achinyamata a MCP.
#malawi
Негізгі бет A Chakwera Opanda Anthu Mukhala Mfumu? - Pastor G Tembo
Пікірлер: 22