Nde mijedu imeneyo azibambo akuluakulu ngati inu mupindula chani kodi nde maumboni anu alikuti timve kuti a Mangochi ananenadi zimenezo? Or mukupanga sewelo la Nyuwani?
@harrisbanda5891
4 ай бұрын
Lyton mau osasawo ngati wadya manyi ankhumba, watibowa hypocrite iwee, amalawi tinakutuluka ndipo sitizamvelanso ma VN ( voice noteless ) ako osasa aja opanda mchele ajaa
We say Azaan not Muazzin. In fact, Muazzin is the one who calls people to prayers while Azzaan is the actual calling of believers to go to Masjid and offer their prayers.
@MadalitsoChisale-j2o
4 ай бұрын
Layton mangochi wathera pomwepo bas?
@MustaphaCassim
4 ай бұрын
Kodi chakwera ndi busa kapena wasataniki? Mc cathy chakwela mbuzi chilima mbuzi nduna zonse mbuzi imodzi imidzi..
Great for debunking him... I wish you had maintained your patience until the big fish behind the scene was exposed by Lyton... Next time take your patience until everything gets exposed
@ChristopherMadulira
4 ай бұрын
Apap bas galuu wagwidwa app
@naniibrahim7774
3 ай бұрын
Wayithawatu za dola wakana kunena ife timadikila tinve nawo galu wachabe 😂😂😂 appreciate guys let,s be together ❤
@MathewKalinkhu
4 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 wayaluka Mr.Mangochi, ndipo a Banda mwamutha Mangochi tathokoza.
@InnocentCcij
3 ай бұрын
Good work Mr kalindo ❤
@YasmeenYalabi-b2c
4 ай бұрын
Lyton tinakutuluka ndi mbava kuchita kukhala ngat simsilamu nayenso ndi mbava yotherati
@JaneMoyo-ws2di
4 ай бұрын
Wina ayipe koma zochitika nzimodz. Azbambo uthira kuwiri sumaakhala nza zimayi izi. Kumaona nkhani zokamba pa foni a Lyton
@Mickeykasambula265
3 ай бұрын
Eish malawi uja
@Yusufu-Daudi
4 ай бұрын
Mission failed 😅😅😅😅 mr mangochi
@Homeofpeace321
Ай бұрын
Leyton mangochi ndiozelezeka
@ChimwemwePhiri.1
3 ай бұрын
Ndikape Laiton Mangochi yu............
@SangwaniHara
2 ай бұрын
Malawi uli PA moto.. Akungulisa athuwa salibwino
@PhillipAcquaron
4 ай бұрын
Ati munthu woyipisitsa kkkkkkk
@kondwaniselemani8558
3 ай бұрын
Chakwera simungamukwanitse mwachepa muuzane nonse ndipo kongelesi ma vote ale ndi achikhalire
@IssahBannet
3 ай бұрын
Mboloyalo wanva napamnyelo iwe
@FauzaTabu
3 ай бұрын
Muthu oyipitsitsa kwambili ndi ameneyuyu mukunena kalindo
@Manuel-cm1np
4 ай бұрын
😂😂😂😂 malaw to the world😅😊
@DaireMusopa-rh2cy
3 ай бұрын
But why coming out this early with this info... Tinakaadziwa agalu akumpeza mangochiwo... Mwatilakwila
@DawoodIssah-mp1yi
4 ай бұрын
Malawi 1st You are true people to be followed thank you Mr president thank you Mr Masauko Banda and entire Malawi first organisation.❤❤❤
@EdwinBanda-ee1bz
4 ай бұрын
Kkkkkk
@PreciousChlima
4 ай бұрын
Lyton mangochi apa ayaluka kuposa munthu ozikozera akuyenda
@ThokoBanda-s9p
4 ай бұрын
Mangochi ndichitsilu chamuthu moti ndakwiya naye
@ApsChap
3 ай бұрын
DC for ReaL forever
@IsaacSuluma
2 ай бұрын
Zojudula izi, mwachepa
@AlihIbrahim-s7v
Ай бұрын
Ma comment awatu timangovutikatu sikuti amawafikila enuwakewoyi,,,amagika kwa emwe wapanga post mwiniwake wa page ,,,sikutiso amayimba kwauza zomwe gapanga comment ayindithu,,timangozivutapo apa kupanga comment
@JosephKeneph
3 ай бұрын
Awa ndie ma 3dom fight eni eni, not enawa angokula mazila nkabusula bas, mbambande The DC-BON KALINDO Mr President!!
@giftmandozamkwatula5032
3 ай бұрын
Life yabwanji iyi😂😂😂
@JefuKAFENKHATA
3 ай бұрын
pagorini umakwana the best 💥🦾🦾💥💞
@erickhowoya9894
4 ай бұрын
😂😂😂😂😂 mangochi alibho, kumachenjera pa town
@alickkachepa3801
4 ай бұрын
Kkkkkkkkk kalindo eti ndi wowopya 😂😂😂
@DeenesNurudMeke
4 ай бұрын
Anthu mukudyeleradi eti
@teezdada
4 ай бұрын
Lyton Mangochi 😂😂 anthu amutsika
@bakolomanyenje8360
3 ай бұрын
And kalindo was recording ndikuyakhura mwachocho ,,kuti aoneka ngt. Ali serious
@Henry-vw2cz
4 ай бұрын
Lyton mangochi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂kapolo galu
@OwamiSimeon
3 ай бұрын
We stand on you born kalindo from livingstonia Rumphi mantchewe village
@Wilardmavuto
3 ай бұрын
❤
@JoshuaNgosi-c8u
3 ай бұрын
All of u on this speech u ar after money.we are lacking gorvenance and good leadership.
Koma kumeneko akakhala Akila amati kuti kweeeeeeeee
@GiiiKatekesa
4 ай бұрын
Ine ndimazifusa Kut Lyton agakhale ndi nzeru momwe amalakhula munja ngati sipika yalowa nchenga
@Gwedeza-oz3jv
4 ай бұрын
😂😂km abale
@thomasyohane987
4 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@Gwedeza-oz3jv
4 ай бұрын
😄😄etidiyinu
@simonabraham7241
3 ай бұрын
How can I get in touch with Mr Bon Kalindo? From Zambia.
@AlexNjanje
4 ай бұрын
Mangochi mapolo akoo takudziwa ndiwe chitsiru ndi azimzako omwewo motii mmene tikumzuzikiramu iwe uzipanga zimenezi sure ambuye akukhululukire ndithu ndipo ngati ulindi mzeru usiya uchitsiru umenewu ndiwe galu kwabasi
@islamaameen2177
4 ай бұрын
Koma Malawi yoh
@MacdonaldMasamba-e2x
3 ай бұрын
Km nde yatonyoka osati masewera 🙄🙄🙄🙄awawa apwetekana🤔🤔🤔🤔
@BakaliPhili-es3xj
3 ай бұрын
Kkkkkkk yatonyoka? kkk
@GraceLimani-zw7dx
4 ай бұрын
Munakadikila akumana ndi anthu odzaapereka ndalama wo mutaika camera pokumanapo kuti ayaluke zeni zeni mangochi ndi Ben zitsiru za anthu umphawi wapweteka
@kelvindickson
3 ай бұрын
Amangochi apa ndye mwatikalkasa padazitu chifukwa cha ichi padakopako nkhope yophyanyikayo
Пікірлер: 142