Anthuwa apengamisala simukuona zimene akuchita tiyeni tiwadyele koma vote osawapatsa
@EllenPhiri-xt8pt
22 күн бұрын
Mbamva ndi afiti awa sangawine tangonani anthu ndi anthu amabanja mwawo okhaokha amenewo
@user-ot8no9ex2z
22 күн бұрын
Azakuvoterani ndi ambuyanu ndithu nsonkhani umakhala ndi anthu awiliwo kuousatu uko bwanji manyazi zimvereni chisoni
@ChimwemweJuwao
17 күн бұрын
Haha koma ndiye mukungooneka Mano okhatu kuli kuda Kwa athu kumeneko ndye kwati mukufuna u vice Muthu ukafuna kufa umankhotha makutu kaye
@VictoriaWilly
22 күн бұрын
Kunamizana ndi kosavuta, zinamizanani
@BrightNyoni-yd4ip
21 күн бұрын
Gulu iwe usamaseweletsa dzina la yesu nkhumba iwe
@WilliamblackvPaul
22 күн бұрын
Kwinaku ndingatukwane
@user-yb3su3hi9f
22 күн бұрын
Ofunika kuwatukwana kumene. Onsewo panyero pawo
@SolomonNjolomole
23 күн бұрын
Akulu awa ndi achitsilu kwambiri ndi azizawo onsewo kumeneko
@CatherineDesire
23 күн бұрын
Xx2
@JackNagoli
22 күн бұрын
Let them talk guys ndipo apange ma plan awowo km ubiwno wake malawi siwaathu atatu tiyeni tikakumane chaka chamawa basi khani ndi vote not to talk too much angochedwa nazo
@ChikumbutsoDzukwa
22 күн бұрын
Munamizana udya Galu amawawa muziona this is new generation
@YohaneChitseko
22 күн бұрын
Manje mapephero amene chabe mulungu sangamve anthu okupha ngati inu
Ndi zausiku mumuone or zikhameyo khope yace ngati chidzukwa
@user-yc5uc6oh6u
21 күн бұрын
Usi afela za eni😂
@Eric-gb9ms
22 күн бұрын
Nanu inu makolo anthu siyani ndi kutengeka ndi mbamva izii mukuzinamiza mukamati 2030 nkhondo izabuka mudziko lanthu serious anyani inu
@phanueltalekana5416
23 күн бұрын
Mukhaletu ndima ghost voters mwinatu😂😂😂
@mollymasangano473
23 күн бұрын
Kutereko Mwadya zibazi,A UTM mwawamva mawuwo apephere Zikhale Ng"oma adzakhale vice President koma kuli kale Vice President Usi ,(Mang'anya) zayambiranso AMalawi tidziphuzira phuziiro,Chitozo Chomwe amawona Malemu Saulosi Chilima,UTM why don't you make a heavy discussion by conducting early elections izi sizitisunga.
Пікірлер: 540