The good history BG brother sitimaziwa kuti zinali choncho tinakusowani kwambir Sono chimwendo Banda akamati njala abweresa ndimavenda mavendawo ndima president kungonena kt zikoli talilemphera bwanji mavenda ndi amene anaseka handimack. Watching from Mozambique 🇲🇿 mumakwanira bg never give up bg brother timakunyadirani kwambir potiwululira zisisi zambavazi
@tasiyanakasalu6228
8 ай бұрын
Best historian ever in Malawi keep on the good work
@webstermbewe8395
8 ай бұрын
Thanks for the video Also bring out the video from Zambia over balotse Land conflict
@e.r.mchanel1460
8 ай бұрын
Yah that's good ,ifetu timadabwa ,kuti ma ma vn tawssowa,well done for back again Bakili Muluzi Tv
@ZeckBMalawi
8 ай бұрын
Long life mr bakili Muluzi tv we love you
@Shaabann
8 ай бұрын
Zoona zake man ameen
@sanuhabdullah5998
8 ай бұрын
Thank u for ur voice we love n we ll b wt u always peace
@sanuhabdullah5998
8 ай бұрын
This is very painful Jone Chilembwe ws Malawian freedom fighter for our National . I dont gat a point here y Malawi Gvmnt still treating Chilembwes relatives a like ,N while thy keep changing buildings in Chilembes name .We lv Jone Chilembwe bt we re not
@AlgentChilanga
8 ай бұрын
Lero taziwa Jeffrey kobe kamba ka Bakili muluzi TV kp it up big
@Razarusmbavachakwera
8 ай бұрын
Big ambilife ndiwophuzira ndipo inuyo ndiphuzitsi waifeyo for now we need all update. Ukraine war Israel war Hought war Zotsezi tikuyembekezela kuva kwainu😊❤❤❤
Koma ndiye yah kamuzu analipondeleza dziko lathu iiiiiiii
@williamchunga9398
8 ай бұрын
Bas ul bizy kuvotelaa mcp walozedwa et
@greychizaka4088
8 ай бұрын
King❤
@BonexMaruanha
8 ай бұрын
Tiuze za ku Ukraine ndi Russia
@عثمانايامعبداللهملاجيلا
8 ай бұрын
Kutsatila mwachidwi
@ConexJailor-bc1ns
8 ай бұрын
Inu mumathaa
@YunusuOfesi
8 ай бұрын
Ulemu wanu big
@joebrown1158
8 ай бұрын
But after all the evil 😈 things where is Richard Armstrong who was so called Kamuzu Banda? The answer is in hell.
@jaychikumbu5898
8 ай бұрын
tiuzen zambili za geoph cobby
@AlgentChilanga
8 ай бұрын
Chakwera ndi bibi kwabasi iya
@StazioChitsulo
8 ай бұрын
Umakwana Big
@HendryChiwezo
8 ай бұрын
Njala yayamba lero kkkkkkkk malawi
@shamextchuwa4722
2 ай бұрын
CHACHA
@JOHNSANGWALI-ox8mu
8 ай бұрын
Umatha
@NasonSalimu
Ай бұрын
😢😮 🎉🎉😢😮❤
@MarizaHoracioMario
8 ай бұрын
Chakwera ndi wopanda nzelu
@HakeemSilaji
8 ай бұрын
Second ine
@jimmybema7684
8 ай бұрын
🎉🎉🎉🎉
@RoslenaMahlanyana
8 ай бұрын
Wautsilu
@DickMdala-pn4pd
8 ай бұрын
Thank you bro
@GiftMusorola-l2o
8 ай бұрын
Zabodza izi sanaphedwe mu msinje wamigowi
@mbwindinga
8 ай бұрын
Pangani history yanu pa khan yomwe mukuziwa
@ephraimchigamba
8 ай бұрын
Iweyo odziwawe unali kut nthawi yonseyi umaleka kufotokoza kut timve nawo.. Mamina ako wamva kape iwe
@Ushermchebe
8 ай бұрын
😂😂😂😂
@ChiccoJelly-wp5wj
Ай бұрын
Man of history we love you
@tisuhmakhwah7085
8 ай бұрын
Best KZitem channel in malawi ..well narrated history.
@AlexKaunda-x3p
8 ай бұрын
Chakwera amakonda brue movie
@frezargamah3438
8 ай бұрын
Zilimabuku mwa mcp zankhadza zonse i mcp ndi mcp singasiye nkhadza taaaaa angopelera kuti chakwela wakumana ndi amalawi wokwiya sangapange mistake kukaponyela munthu kung'ono
@FebbieNjewa-g3k
21 күн бұрын
Eish kamuzu?????
@anafieintuka8090
8 ай бұрын
Zambiri timaziwa kuchokera kwa inu basi
@DouglasDazuKamwendo
8 ай бұрын
Iwe ndi munthu ase
@madalitsomakawa9708
8 ай бұрын
I like your presentation but your hatred towards MCP mmmm
@CHARLESJUNIORMPHELANJIRU
8 ай бұрын
Not like that koma mcp zavuta basi
@chilembwekanjirawaya4296
Ай бұрын
Bakili Muluzi TV ndiye dolo zomwe ukuyankhula APA true story. Magret Durham alipo mpaka lero. Kuli mbumba yaikulu kwambiri Ku America. Grace Chapunga anamwalira mchaka cha 1999
@frankfriday3141
8 ай бұрын
Muthu wachakwela siumuqwila ntchito
@JamesLeonard-r4p
10 күн бұрын
Zovesa chisoni ana ake anafa ndiwumbawi relo bambo awo ari pandarama
@isaaczuze
Ай бұрын
Chipani cha anthu okupha ....anthu ankhanza chakwera ine toto olo zitavuta bwanji
@EricMilandu
24 күн бұрын
Ka sound ko kamandiwaza heavy
@RodgerOvertonmbewe
Күн бұрын
ndipo live kkkkk
@victormaulika6523
8 ай бұрын
History iyiyi tinaisowa pano ndithu
@JoyceBanda-k8t
Ай бұрын
Cakwera ndiwasatanic okupha oononga comwe akudziw ndi kukhetsa mwazi
@MjombaMjuba
8 ай бұрын
Wanama, history ya John Chilembwe timaphunzira, khala ndimanyazi kukamva za bodza
@DavidMontford
8 ай бұрын
Koma ngat akufuna chipatalacho chikhale dzina lake la chilembwe akanayamba kufufuza abale ake a chilembwe ndikuwalemekeza chifukwa kulibe ulemu uliwonse since this regend died as of now no 1 respected in his tribe
Пікірлер: 209