Mtambo you are Malawian julias malema and your party aford you get 9% of the votes that is my prediction
@ChrifordBiziel
28 күн бұрын
Zimenezo2 zithera konko mwene
@chrisboyce2
28 күн бұрын
UTM ikuyenera ibwerele ku DPP ndipo Ife angoni a ku Ntcheu tili ready kudzawavotera DPP Pamodzi ndi UTM ngati alliance
@KikaImran
28 күн бұрын
You re very right. Sindinavoteko and if DPP coraborate with UTM i ll vote for them though am 100% sure that andale ndi oipa onse, they re there for their empty bellies
@ntombiunice8637
28 күн бұрын
Mtambo ndikhuluku...u minister unamurephera
@Pangolinimw
28 күн бұрын
🫡🫡🫡🫡🫡🫡
@yassinn5634
28 күн бұрын
Chipani cha UTM chija ayamba kuchikanganirana. Chizungu chake SCRAMBLE FOR UTM. Ena apita kwa Aford, DPP ndipo ena atsala ku MCP. Thats my opinion. You got yours take it or leave it.
@MercyNkhoma-b6h
28 күн бұрын
Koma a Mtambo akunena zoona kuti samafuna mpando? kkk
@user-jn9tz3li3v
28 күн бұрын
Mtambo mpaka kumuziwa Mulungu kkkkkkkkk ndale ndizovuta
@emmanuelsambo1158
28 күн бұрын
It was only SKC
@HappyAntenna-sf9qx
28 күн бұрын
iweyo ukumenyela ufulu wako ndalama zakuthela
@josephgabriel1016
28 күн бұрын
Timothy sangatinamize for the second time.....
@MercyNkhoma-b6h
28 күн бұрын
Koma chaka chino ziliko ndithu.
@BestonChagala
28 күн бұрын
Koma a Enock muchenjere ndi mtambo,mugawana zida 2025 isanafike chifukwa aliyense akuyankhula ngati ndi president payekha.Nanga mmene akuyankhulira mtambomo akuyankhula ngati vice president wa chipani ngati?Akudziwa kuti kupatula Ku hrdc sangayambitsenso gulu lina lotchuka paokha,nchifukwa chake asankha AFORD.Akuti safuna mpando chonsecho amayankhula ndi zodiak kuti afuna Udindo ngati platform yoti adzikhala influential
@BestonChagala
28 күн бұрын
Regionalism inamkanika chihana ,you can't win the national presidency without people from other regions.Nthawi zina musanayankhula mudzikhala Kaye pansi nkuuzana kuti kodi izi ndizoyenera kudziyankhula pagulu?Mukuti unduna simukuufuna chonsecho mukudziwa kale kuti simungadzawine u president wa 2025.Ngqkhale iwe mtambo pa ticket ya AFORD sungawine kuchitipa u mp ,nthawi imene munali nduna palibe chomwe munawathandidza anthu aku chitipa
@BrightNyoni-yd4ip
28 күн бұрын
Mumakwana a hot 265 watching you from lusaka Zambia twatotela sana
@user-im7sc2my4w
28 күн бұрын
I don't trust NTAMBO ,NTambo vuto nngosamudalila Komanso nkovuta kumukhulupilila uyu . Ife aMalawi mukanakhala Ngati Bingu ,mmali ndi munthu wosavuta ,kungomupangila njira ya chakudya basi ,President ameneyo adzakhala WA muyaya. Ngati dziko Lili ndi chakudya ,ma business amayenda BWINO .Koma aaaaa uyuyu ayi mwina
@actuarialscience2283
28 күн бұрын
Ngakhale banja limayenda bwino ngati chakudya chikupezeka. Zovala ndi zina zimaphweka kugula.
@MosesNyalugwe-ll8hh
28 күн бұрын
Maloto achumba
@Donnex-gn2sf
28 күн бұрын
Aford akuwona kuti ku UTM kulibe utsogoleri komabe sizingatheke chifukwa a Aford akufuna mpando and UTM nayo yikufina mpando 🤣🤣🤣🤣
@user-qp8kh2hj9o
28 күн бұрын
Ife tapanga kale ndi UDF musavutike 😂😂😂😂😂
@samdiverson9733
28 күн бұрын
Kkkkk mtambo sungatunamize adah ndife a utm we are together with DPP
@spargomw
28 күн бұрын
I agree with you 100%❤❤
@BestonChagala
28 күн бұрын
Vuto ndiloti ena pa imfa ya chilima afuna kutchukirapo.Aford yakhala zaka 30 but no progress koma pano they are claiming to be friends of chilima just to capitalise on the direction less supporters of utm.Ku AFORD kuli ndani odziwa ndale kuposa kaliati?And in terms of popularity utm ili pa mwamba kwambiri kuyerekeza ndi AFORD
@chrispinechirwa2655
28 күн бұрын
Ili ni lirombo yayi 😂😂😂😂
@VungaQueen
28 күн бұрын
Kkkk😂😂😂😂😂
@chrisgremu740
28 күн бұрын
Ndiye Chakwera akawinaso 2025 Mutani?
@petertaulo8014
28 күн бұрын
Sangawine mark my words
@TiyesNayuma
28 күн бұрын
Chitsilu iweyo you failed as a minister
@user-eh1gn1nj9d
28 күн бұрын
Kodi imfa ya Chilima mukupangira campaign Mulungu akukanthani ndithu
@MercyNkhoma-b6h
28 күн бұрын
Koma a Mtambo akunena zoona kuti samafuna mpando? kkk
Пікірлер: 66