Malawi is lacking good leadership that's why is the poorest country in the world.
@CharityChirwa-t1e
2 ай бұрын
Chakwela asowe fiti yothelatu UTM ganizani mofasa musakonde ndalama kumbukani tsogoleli wanu chilima upangili omwe analinawo sitikufuna kuti kupita kwachilima ndizinalake lithe ayi mukuziwabwino zomwe amafuna chilima still I remember S K C ambuye sungani mizimuyawo 😭😭😭💔💔💔
@WestonGawaza
2 ай бұрын
UTM,mapulezident awa mayi chirima, mwana wachilima , Brayani Banda UTM awa ndi mapulesident a malawi, mukawasiya awa chipani chapita ndimazi, kongo kabira analowa ali ndi 31 years mundinkhulupirire , yeremiya, davidi, anali ana kaliyati ankhale muzati wa UTM, BY BY
@saadisadie3125
2 ай бұрын
Ayi kabira analowa Ali ndi28
@Musa1828-l5d
3 ай бұрын
Chakwera pamtumbo pakę anaba ndalama za fertilizer asamatipusitse azipusitsa zitsiru zake zomwezo
@BestonMakochera-qk4sz
2 ай бұрын
UTM president Tikufuna brian banda wisy man
@brainsmkumbwa6267
2 ай бұрын
Wathamanga kukasiya ma pepela opikisana nawo pa udindo wapulezidenti chifukwa akudziwa kuti munthu yekhayo amene akanalimba mtima kuti apikisane naye wamupha kale (Chilima)changucho sichina koma kusangalala
@MineMoyo
2 ай бұрын
Inu mudzikhala ndi manyazi ponena za covid....palibe anthu opasa manyazi ngati inu every statement of economics development....koma mukafuna Kuba ndalamazo Palibe za covid anthu onyansa mitima
@MartinMajola
2 ай бұрын
Chakwela satana wohipa ziko lamu nyeraaa
@Homeofpeace321
2 ай бұрын
Am still worried about Chilima, Chakwela Anapaga Zolakwa Kwambili, Sangamuphe Munthu Chonchija
@AishaChibwana-b8o
2 ай бұрын
Kwambiri ndipo ine zimandiwawa mpaka lero pano bwenzi chilima atatiyankhula zokhuza comvension imeneyi hmm😢
@YamikaniThoko
2 ай бұрын
Mwakweza ferteleza tsopano mukuti tizigwilitsa ntchito manyowa ayi zikomo Bola la chakwera
@AustinManes-m3w
3 ай бұрын
Asamango namidzila covid19
@ShuqItwa
2 ай бұрын
Mwalephera kuyendetsa boma osanyengezela COVID 19
@kubengovender6996
2 ай бұрын
Big up brother man!!
@JafaliAkimu-ll1bf
3 ай бұрын
chakwera asanamizire zimenezo chakwera ndi chitsiru chamunthu chigawenga
@dondamissonchdziwe3958
2 ай бұрын
Pongopha Chilima uja basi, Chakwera waluza, Chakwera must go
@AaronMsewezi
2 ай бұрын
President Chakwera akanabwera ndi chipani china osati MCP , nichifukwa chake mbiri yakale ya MCP ikumukhuza, but instead of kutukwana a president let us pray for our country, kutukwana sikusintha zinthu guys,
@HestingsZiba-d6k
2 ай бұрын
Chakwela akangokhala pamupando basi mcp yathela pomwepo ndithu galu uyo wakupha achoke
Пікірлер: 58