ndipo zoona ine ndikudabwa kuti ena akuwona ngati boma ili likuyenda bwino chakwera chomwe akuziwa ndi bodza,kuba basi
@jamesjealous-p4v
7 ай бұрын
Khani zanu zimamveka bwino, muyambe kusakaniza ndi za kunja ❤❤❤
@JonesChingaya-yf4gg
7 ай бұрын
Ndimaganiza ngat Joyce Banda analephera kuyendetsa boma, koma mayi uja anayesesa koma Chakwera uyuyu ndi panja penipeni ndipo sindinaonepo boma la ziselekwete ngat la Chakwera.
@aggogokina8992
7 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂👍
@AustinChiyembekezo-cx4mz
7 ай бұрын
Ndipotu mbuzi zenith zenith zero pa 100
@AminaPhiri-pp9tw
7 ай бұрын
Boma lakanika basi kodi ngongole mukimabwereka zikupita kuti sono
@aggogokina8992
7 ай бұрын
Ndipotu kaya😂😂😂
@marryphili5419
7 ай бұрын
Vuto ndiloti chakwera akuyendayenda kwambiri Koma zoti muti mudziko muno mupezeka chakudya nje
@WonganiNyirongo-j6m
7 ай бұрын
Passport is not supposed to be something to make money out of, it is a legal document which every citizen is supposed to have
@FrancisDay-br7xb
7 ай бұрын
Chakwera niwolephera mbari zonse kupezeka vuto. 2025 sankhankoni ena dziko lamalawi idzakhala failed state ( bankruptcy). Uyu afunika ubwelera pa Guwa adzikanamiza anthu.
@josephmanyenje7107
7 ай бұрын
Am crying for Malawi the warm heart of Africa ,,the fact is all hunger thieves in this administration are selfish mostly in nepotism, tribelism ,regionalism and not thinking of the poor Malawian on the ground ,,,,shame on your rulers
@josephmanyenje7107
7 ай бұрын
Am crying for Malawi the warm heart of Africa ,,the fact is all hunger thieves in this administration are selfish mostly in nepotism, tribelism ,regionalism and not thinking of the poor Malawian on the ground ,,,,shame on your rulers
@josephmanyenje7107
7 ай бұрын
Eish koma apa ndiye tilimmavuto, zoona omwewo amauza Chakwera kuti asise kwacha lero atembenuka kuti kuchoka mchaka Cha 2020 boma silikuyenda bwino 😂😂😂
@ChimwemweSafelana
7 ай бұрын
Chinthuchi cgikutsogoleledwa Ndi munthu oti sadziwa chilichonse too much scandals ,kugula fertilizer ku butchery kubetsa ndalama kwamadobadoba apa akuti akambelembele eti mpaka kulamula boma kuti awapatse 2 billion kkkkk koma apatse mamembers mudyera pamodzi
@ThoccoBondo-mx7vt
7 ай бұрын
😂😂😂😂😂 Zawakanika bambo Chakwera munawonjedza kugwesa kwacha kaya anakunamidzani ndani kuti mukagwesa kwacha zithu ziyamba kuyenda bwino lero ndi izo inu munalakwisa kusiya za ambuye lero palibe chanzeru mukuchita
Mchewa angakhale ndi mzeru zaulimi? Koma kumwa tea ndi gule basi Alibe ndi phatso yomwe yotsogolera dziko, ngongole zili thoo mpakana 12 trillion something 😢😢😢
@augustMag
7 ай бұрын
Oo my God, this problem is very painful MALAWI WHERE ARE YOU GOING? 😭😭😭😭🙆🙆🙆
@YusufLeyaBlackWasili
7 ай бұрын
Zikhale ng'oma atule pansi udindo wake ngati nduna ya za chitetezo, chifukwa chobedwa (sistimu) yopangila ma passport.
@clintonhodda9830
7 ай бұрын
Chidule ulamuliro walephera
@paulnyondo7572
7 ай бұрын
Vuto ndi chakwera akuba kwambiri .so dziko ndipovuta kutukuka
@JoyceBanda-k8t
7 ай бұрын
Zikhale ngoma usabdilakwitse mbava iwe
@sydneyjamu8877
7 ай бұрын
😂😂😂 Palipose akuyankhula ngati walezera zikhale
@AleksaWilliams-qc6cn
7 ай бұрын
Sizikufunika anthu achifufu izi
@WilsLimited
7 ай бұрын
Chakwera sakusiana ndi yona mmalemba oyera akazachoka pampando yehova azabwezeretza zinthu mchimake kumbukilani nthawi ya bingu mulungu amakondwera ndi msogoleri oopa mulungu osati oukila mulungu
Пікірлер: 107