I don't understand zikuchitika pamenepa titsekuleni maso
@BENSONRANGWANI
5 күн бұрын
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zache
@EdwardGeorgeKasabola
5 күн бұрын
Zikuti bwanji???
@DanielJuwawo
5 күн бұрын
Zikut bwanji apa
@JeremiahNgwira
5 күн бұрын
Inu inu don't be naive, there is AI where people can use this to imitate someone else's voice exactly...this is the era of technology don't be fools..
@aubreytiyess
5 күн бұрын
Kkkk
@user-lx9ly6sp6x
4 күн бұрын
No it's not Chilima
@MemoryMugala-cm2yr
5 күн бұрын
Amupha di
@user-ji4xn6me8d
4 күн бұрын
😂😂😂 chilima ankayankhula choncho?
@maureenshepherd368
4 күн бұрын
Chilima wouldn’t mention plane as prane … the audio was edited it’s not him… I mean the accent though!! the person behind the audio is trying too hard to speak English 😂😂😂😂😂
@MacphesonNkuluzando
2 күн бұрын
Kkkkk koma nde masanje eni eni voiceyo amayamkhula modekha choncho mundege atapangakale ngozi kapena akudikira kuti ipangengozi kkkkkkkkk pangozi ungamayakhule choncho komanso background yo nde mbola mwakanika kuipanga edit mwaonetsa kupoira kwanu, musiyeni MULUNGU akhale MULUNGU kkkkkk kusiyana ndikupakana matope
@NicksonHarawa-pe9se
5 күн бұрын
Mau akufanana koma zitayeni man, let's just not for them this coming year than sitting here and make noises
@user-ji4xn6me8d
4 күн бұрын
Sakufanana mauo man
@MarvellousTech-kz6no
5 күн бұрын
Zopanda umbon ,
@joshuasibande2942
5 күн бұрын
U just played past video
@SaidiMbawa-st6bj
5 күн бұрын
Akulu inuso ndinu mbuli bwanji zikugwilizana bwanji ndi nkhani imeneyo
Пікірлер: 30