Apa nde chakwela akutitola kwambiri mulungu mumve kulilira kwa amalawife mupaka kugilitsa mutchenga uli wachilengendwe ayi zikomo magamuro anu chakwera adutsa muyetso mitsozi yanthu kuvutika kwanthu dzikhare pa panja lanu achakwera 🥲🥲 inu aboni kalindo keep it up kutiuza anthu opepelawa 🔥🔥🔥🔥
@FRAVIOKUNSANJA
19 күн бұрын
Koma boma ili lafika posauzana n'chenga umene akulesa wayamba kuvuula lero ameneyu galu kwabasi chakwera atimaliza tonse
@LysonMtalika-tb6fk
19 күн бұрын
Powerful talking from our beloved president, president for the poor always there for poor Malawian citizens the Dddddd Cccccc!!!!, proud of you always. May the good Lord continue to guide and protect you always 🔥🔥🔥🔥
@GanizaniKamvazaana
19 күн бұрын
Akuti apolice adzisilira mpunga WA Ana school koma ADC inuyo ndi wa wani long live a kalindo anya manyi achakwera achitsiru amenewo , nde bwino akalindo ineso maganizo amenewo nariwo kuti athu asavotere chauzika akalindo inuyo inuyo ambuye akudaritseni ife kwakwataine sitikupanga nawo zopusazo tikulira ife ku Ntcheu😢😢😢 koma God knows chakwera adzafa imfa yowawa
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
19 күн бұрын
😂😂😂😂😂 DC ndiyakatundu zoona
@user-hk3hg1to4e
19 күн бұрын
Anatiloza ndi malemu chilima aise pomuchita follow achinyamata ife😢😢
@StevieChikaonda
18 күн бұрын
Uku nde kung'alulatu 10,000% ayi zikomo ndithu💪💪💪💪💪💪💪
@FisherAction
19 күн бұрын
Big mulungu akudaliseni ndipo pitirizani kutiombola kuwachosa amalawi mw agaluwa a mcp
@EllenPhiri-xt8pt
18 күн бұрын
God bless you Mr DC you always stand for the poor this government of chakwala is useless ever
@GoodsonDiwadiwa
19 күн бұрын
The Dc Bon Kalindo anthileni fire anthu osowa umunthuwa osanyengelera ayi
@GospelSoldiers-sr7np
19 күн бұрын
This two much guyz..koma kuli Mulungu amatha kumuchitsa munthu pa mpando ndikuthamangitsa kukamusiya ku ntchire..koma mmawelenga baibulo????? Inalipo mfumu ina imachita zimenezi koma ngati simusamala Mr president ndi nduna zanu mupalanura mkwiyo wa Yehova....take my note
@EmmanuelMpalagule
19 күн бұрын
Mr kalindo u are a hero, the opposition the very week, the opposition is in deep slumber,
@vitumbikokamanga5869
19 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤go deeper mr kalindo you are the best ❤❤❤❤❤❤
@raytavares2256
19 күн бұрын
Mr president the DC we love you and greetings from North London UK
@GamaGama-z8p
19 күн бұрын
Tell dem the dccccc!!! Never stop fighting for the poor innocent people we vote for purposes Mr born we are on ur side
@DalitsoMatope
19 күн бұрын
Kalindo we are failing to thank you but only God will thank you
Mr Bonnnnnnnnnnn kalindo DC big up kodi bwanji osayambisa madem bwanji kumalawiko galu ameneyo ife kuno atikwana kwambiri ndithu tiye nazo Mr bonnnnnn kalindo the DC
@GRACIOUSKENAN
19 күн бұрын
Timanva nanu kukoma nsaname🎉🎉 ndipo mau anu amatitothoza ifeo,ndiposo pa mpando wa upresident inuo mwafika kale bwana,zolembalemba zangosala tsiku loyikika bas
@kelvinmphande3754
19 күн бұрын
It's the sikusinja Gwenembe song for me
@HawardStainly
18 күн бұрын
Akubwila fodya wamagogo wakuzino uja,(maganga).
@InnocentEdasi
19 күн бұрын
The DC 🔥🔥💕 Chakwera atule pansi udindo..., Palibe zoti asintheso ai.., tikumunyengelela uyuh.. _
@limbanimtitima9170
19 күн бұрын
Kung'alula big man,ife Angoni kuntcheu ndife oganiza kkkkk😂
@chimwemwemasamba2880
18 күн бұрын
Allowance ya manebbtatenga koma ndiyochepa kobasi....polingalira ndi mmene zinthu zakweleramu
@gwatandingo9502
19 күн бұрын
Muli bwino koma Anthu Ena sakukhulupilira inuyo boss munatitenga kutisiya ku sewo inuyo munapita kunja nokha mukadya ndalama zatha lero mwabwera 😂😂😂😂😂😂
@user-vh9uk1jy7w
19 күн бұрын
Our president more fire 🔥 Booooon kalindoooo 🔥 🙌
@MartinsKhumalo
19 күн бұрын
❤❤❤ ndimakunyadilani 👏👏
@user-xd1cm7tm7t
19 күн бұрын
The dc our poor president in Malawi
@pacharokoloviko1694
15 күн бұрын
😂😂😂😂 ati kufuna kumangidwa!! Komadi ndiwe DC
@ChimwemweBottomani-hc5ju
19 күн бұрын
Make mbuuu mwana mbuuuuu long live the DC
@JabesAlfaiate-t4v
19 күн бұрын
A kalindo tiyankhulileni ife tili nanu mcp ndi yoipadi ifeyo a malawi amenetili kuno ku Mozambique tili o khuzika ndi zomwe likuchita boma la a chakwela , ku vuula mchenga mpaka laicence zinachitikako kuti ? Keep it up a kalindo.
Where are we going to make our hustle now😭😭😭 mpakana nchenga omweu tkatenge chilolezo? 🔥🔥🔥🔥🔥
@user-gd6zb2bv8f
18 күн бұрын
Koma funso nkumati kuti, Kodi Chakwela ndi Zikhale wacheyo, samachita manyazi konse akamamva izi? kapena umunthu wanu unatha?? The DC tell them shit
@densonchiwaya8439
18 күн бұрын
Mau awaa sikalindoo
@happychimwemwe-1805
19 күн бұрын
Umakwana booooon kalindo
@ChondezVick
19 күн бұрын
The DC himself 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@user-qc7qg4cy6k
19 күн бұрын
Totally agree the dc
@dinahmunthali5324
18 күн бұрын
Ine nyimbo ndi zomwe zimandi waza koophya ati Sikusinja ndi Gwenembe amkaimba agogo awake DC popita ku Mzuzu akudutsa mu chikangawa 😂😂😂😂😂 DC makina 😂😂
@JamesKambale-s2c
18 күн бұрын
Koditu uku mcp kwangokula mbuzi za anthu
@LinoMatchado
19 күн бұрын
Iyayi na ya mchenga yokhayo boma likunena zoona chifukwa mchenga is in the group of minerals and any mineral is a government property which is minored through the government permission. Everywhere in the world illegal mining is prohibited citizens are allowed to collect sand ndi wilibala basi not with a thipa truck then you have to go face the law which is in the constitution every country.
@user-nf3ik3ff6y
19 күн бұрын
The Dc bon kalindo good Messnge
@user-hb1ll8lj3v
19 күн бұрын
Gwenembe ND sikisinje yemweyo 😂😂😂😂
@MynessChirwa
19 күн бұрын
😂😂😂 book la gwenembe kodi kkk
@texonkautera
18 күн бұрын
Anthu amene amabweresa Mbatata Ku nsika wa Limbe Ku chokers Ku Mulanje akuzunzidwa kwambiri akafika kuti asise a Police akuchosa misonkho akuti alakwa akalipire. K20 Pamene anthu akupangira mavuto mafuta anadula Palibe chomwe akupindula
Aborn kalindo nde mumatiziwisa nkhani zambili mumatiyimilira koma or mukuyankhula anthuwa palibe chomwe akuva bwanji kuti kupangike mademo poti apo akuwona ngati tikusangalala ndi ulamuliro wawoo kukufunika ma demo kuti Ave ngati mumene anapangila azathu ku Kenya lizaini sangapange popanda ma demo 😢
@stanfordnsona
18 күн бұрын
Kalindo umatitsekula maso
@mlimolubanda6348
18 күн бұрын
The DC .....
@Sugerman-tw4do
17 күн бұрын
Big Bos DC mumakwa
@user-fq4kv8dj4t
19 күн бұрын
Zoona aliyense akavote opanda cha unzika basi nanga izizo nchilungamo
@samuelgambatula2415
19 күн бұрын
Tiyambe mademo.... Ulemu wathapo apa
@Vascomw
18 күн бұрын
Ndipo live eeee a police eeee akuwo jeza
@user-sv5yi9gt4u
19 күн бұрын
Zoona Born Kalindo auzeni ife tikuvutika kwambirii pa msewu kuno ku Kasungu chamama
@ZainuluNsalule
18 күн бұрын
Good
@user-eh1mg3ww6d
19 күн бұрын
Koma m,chenga wa mulungu abale koma chakwela ambuye mutengeni watituza mokwanila mulungu mulangeni galu ameneu
Пікірлер: 223