A UTM muchenjere mutha nonse, muganize bwino pamenepo mutsegule maso anu kumbukirani SKC m'mene anamuphera,SKC mzimu wake uwuse mumtendere and sadzakondwa nanu chifukwa iyeyo Ankafuna kuthetsa mgwiriano
@jameskamanga628
22 күн бұрын
Kkkkkkkk akuti sionse ali abusa ali azibusa 🤣🤣🙌🙌
@SymonYohane-i5q
22 күн бұрын
Athile fire amenewo amalenga bad
@IbrahimYusufu-z9d
22 күн бұрын
The DC fireeee
@zizipizganimunthali3653
22 күн бұрын
Boooonn !!!!! Kalindo the DC😂😂😂😂
@arnoldkaphasy69
22 күн бұрын
DC umakwanaaaaaaaaaa 💌💌💌💌💌
@user-nf3ik3ff6y
22 күн бұрын
Bon Kalindo number one, good Messnge
@MorresJuwatah
22 күн бұрын
Umakwa Bon👋👋👋
@vivianmkwate8536
22 күн бұрын
keep it with good work👏🏾👏🏾👏🏾
@MasterTaulo
21 күн бұрын
Sss nyooooo boni kalindo
@sukiemapemba4094
22 күн бұрын
Great man forever Malawi wathu wasala mwa bon kalindo basi ❤❤❤❤❤
@ModesterMbendera
21 күн бұрын
The DC Bon Kalindo tili pa mbuyo panu osaopa MCP chipani chakupha ndipo chili ndimapulani oyipa musatope Inu ngt pulezidenti wa anthu osauka
@TholoWisiki
22 күн бұрын
Umatha ase
@user-vm7iz6oz6r
22 күн бұрын
Izo ndiye fundo
@TanishaLiffa
22 күн бұрын
Awawa anabwela
@BlessingsKamwendo-z9g
22 күн бұрын
Umakwana DC
@SiphoZungu-tt9iu
22 күн бұрын
Andale samamva 😅😅😅😅
@vivianmkwate8536
22 күн бұрын
Good advise
@vivianmkwate8536
22 күн бұрын
Pls tell them 👏🏾👏🏾👏🏾👏🏾
@Patrick-cu5ey
21 күн бұрын
Ase ineuthenga uwu obelawu ndikuvomeleza anabwera kuno kuzomba kuzatinamiza zot atipasa ngongole paka lero Ena anakalembedwa ku anezi lodge Ena kunamilongo primary akuzilindoso analembedwa paka chinamwal chikanda 3 miles ndeno zot
Zaphabvu DC sitikufunaso kuvotela tambala komaso mbalame iliyose ayi
@AnaffSayamika-uh6vg
22 күн бұрын
The DC
@user-bf1sz6pu1n
22 күн бұрын
He want us to start worshipping dead people. He is losing his mind. Why should we take candles go to our rooms and mention names of dead people? Are they gods?
@RamseyWasi
22 күн бұрын
Mpanje saadzatheka mpaka kale. Mark my words. Ndipo chokabvotera chaka chamawa sindikuchiona. Solutions: Leave the one who is leading the country lead.till 2030.after that, then see if they are going to continue or 😂 Otherwise, they will be no peace at all
@@RamseyWasi komano inuyo nokha mukutha KUSIYANITSA pamene chakwera amatenga boma momwe linaliri ndi panopa mutha kuona kuti panopa anthu alibe chiyembekezo , ndi boma ili 4 years yomweyi ziri chonchi ndiye atengenso 5 Year's chidzakhaka chani ziringati tachoka ku kenani kupita ku lgupto
@RamseyWasi
22 күн бұрын
Bcz to be a president, is just the job or contract of 1830days. After that you pack your things and go. Ngati wachita bwino in those days, anthu amadzakulembanso ntchito for another 1830 meaning 10yrs (3660)days. Ngati walephera in the 1st term, anthu amadzalembanso wina. Koma zomangotukwanizana kumenyana chifukwa cha munthu yemwe inuyo kapena iyeyo sakukudziwa, ineyo nduuona ngati ndi mboolaatu blasa.eg: Ataytanisa anthu 5otchuka monga Apule, Atupere, Bushiri, Akwen +Bright Banda. Nkuwasiya line, then ask me to mention there names, I will definitely name them, you know why,,they are celebrities. Now there turn to call my name: Do you think they can???????? So:how can I support such a thing. Ndye ndzidana,kumenyana, kutukwanizana etc. For what exactly??? Mmmmmmm really?
Пікірлер: 48