A Bon Kalindo tikuku yamikilani potimenyera nkhondo ife anthu Osaka.God be with you Kalindo.
@user-us8um2gr5d
7 күн бұрын
I like the decision yosonkha ndalama kuti tikagule chakudya tikapeleke ku Machinga please Bwana DC Pangani mwasanga anthu tisonkhe tikawathandize anzathu omwe akuvutika ndi Njala.
@CollinsCharles-d9w
6 күн бұрын
Glass P
@dominickandunde-ml7jn
7 күн бұрын
Mtendele kuno ku South Africa palibe kuli bwino kubwelela kumudzi Mr Boni Kalindo, plz timenyeleni nkhondo kuti boma litengepo gawo, zinthu sizili bwino kuno ku South Africa
@charleskadammanja5539
6 күн бұрын
Kkkkkk kumeneko mmesa munapita nonkha ku Joweniko Pangani so plan yoti mubwelele kumudzi kuno.
@Kassim-rb9ol
6 күн бұрын
Zoti kumalawi kuli president ndakaika
@user-jv8zn6bc5n
6 күн бұрын
Zoona zake agalu awa zoti tilindiboma ndipo ndoochititsa manyazi kwambiri
@TecksonKaima-dr6er
6 күн бұрын
2025 muzangoyimira,ife tidzakuvoterani boss born kalindo osatopa komanso osafooka
You are welcome in malaw to be president doctor boss bon kalindo
@andrewchirwa2193
6 күн бұрын
Ine ndkanakhala Chakwela bwezi ndkanathula pasi udindo president aziyanganila athu Ake akanakhala pasi ndi a president Kuno Ku South Africa atipase mupata mmena anachitila Joice Banda
@hashimbakali2164
7 күн бұрын
Mr Kalindo I'm ready to join and support your good plan
@lewisdicksonmlozi130
7 күн бұрын
Muthu amalakhura chilungamo kwambili
@OwenKumwenda-k4j
4 күн бұрын
On point mr
@CosterMustafa-m6h
7 күн бұрын
Bon your the king ❤❤
@AhamaduKareem-x5y
7 күн бұрын
Send number yanu bwana bon kalindo ndimakudyadilani
@RhodrickMataya
7 күн бұрын
Biggy continue I zatikwana kwambiri
@ChanceJasten
6 күн бұрын
😂😂😂 Ndipo zabwino ndi ng'ombe zomwezo athu akudya chiteze si athu ayi Born Kalindo Ndiwe katundu kwambili
@ChemandandacassimMilanz
6 күн бұрын
Best TV
@davidkadyakapita8836
6 күн бұрын
The only man who stands for truth is Bon Kalindo. God bless you Sir
@jennyx6914
6 күн бұрын
kalindo bakili tv and mntanyiwa these 3 people are dangerous plus some activits who do their job secrectly
@charleskadammanja5539
6 күн бұрын
mwana owopsaaaa kwambiri Bon kalindo the DC l sulut you brother.
@TrizaDzimbiri
7 күн бұрын
Zoona zake nthawi ya bakili muluzi ndi nthawi ya bingu muntharika ana ku school ankadya phala, koma president chakwera sangapange zimenezi
@samanthamuller7643
7 күн бұрын
Tipaseni number ya Dc ine uyu amatimenyera ufulu wabwino
@Underson-d9z
6 күн бұрын
Am ready to join kusokha nao ndalama tikadikila president titha kuluza miyoyo ya anthu ambiri kochepa komwe tilinao tiye tithandize ambuye azadalisa
@AdmoreSingini
6 күн бұрын
Tili ndi President koma tsogoleri tilibe muno mu Malawi...
Mr Bon Kalindo........ Musalengeze mawa zoti mwakoza plan yoti muthandize anthu ai.... Azanthu omwe akuyendetsa boma ndiwokwanila kuthandiza anthu omwe akuvutikawo...... Musaiwale kuti mkati mwanu anthu ena ndima spy.. Mawa zitembenuka timva kuti boma lakupatsani ndalama kuti mukagawe ufa
@AnoldJamuteni
6 күн бұрын
Bon kalindo mumatmilira komano anthuwa sava
@DennisKalima
7 күн бұрын
Mumatiimilila malawi Ali pa moto njala Achoke chakwela
@augustMag
7 күн бұрын
Chisoni chandigwira Poona kuti anthu amene amalawira kukavota lelo sakuonedwa ngati ofunika akugona ndi njala osakumbukilidwa Mulungu kumbukirani anthu Anu ku dziko la Malawi the DC Boooon Kalindo president wa aphawi 🔥🔥
Zoona ivn ine kwathu kn Boss anamwalila ana awili km akt galu ameneyu ali mdziko momuno ayi chakwela mulungu azikuwona srs zoona km anthu amenewa uzafunaso mkumamiza kt akuvotele?
@ChrisparKauteka
6 күн бұрын
Koma plezidenti uyu alindinzelu ngat mzimayi okhala ndi ana owapeza pabanja
@amoshilsonsiliya9335
6 күн бұрын
Kmano to be honest Mr born you stand for us for seriously
@OdettaLowrence
6 күн бұрын
Allah atichitile chifundo atipulumutse 😭😭😭😭😭
@AHMEDMOHAMED-i2h7c
6 күн бұрын
Kumalawi ndikwatu koma kulibe president azapezeka 2025 basi
@JoyceLiwonde
4 күн бұрын
😢 So sad 😢
@Sabina-hw4js
6 күн бұрын
God is watching
@BoiDODO-d2k
6 күн бұрын
True boss
@actuarialscience2283
6 күн бұрын
Mukhola la akalulu ngati muli Kalulu wammuna mmodzi ndiye kuti onse aakazi ali ndi mimba. Ku Malawi mkazi wina aliyense okongola ali ndi mimba. A Malawi mukutombana kwambiri.
Ngat president wa anthu osauka, mwapangapo chan to help anthu amene akusauka ku ma midzi ko. Have an act and speak here.
@Henry-vw2cz
7 күн бұрын
Chakwela president omvesa chisoni kwambili
@chirwaellace1093
5 күн бұрын
Chisoni cha boma, too bad
@Dentera215Music
6 күн бұрын
😢😢😢afitidi
@NaomieBanda-t6g
6 күн бұрын
Pangani zoti muthandize ntundu wamalawi osayankhula chabe take adecision kuyankhula mwayankhula bwana koma phindu silikuwonekaso
@Sabina-hw4js
6 күн бұрын
I wish I could speak to him and tell him facts.
@user-jv8zn6bc5n
6 күн бұрын
Ine ndikupempha kuti amalawi kuno ku SAfrica kuti topange chionetsero chosonyeza kusakondwa nalo tikapeleke kalata ku malawi embassy ,ndiye tipemphe boma la SA komanso amkulu wa mizinda kuno
@EstherMbisa
7 күн бұрын
Ndife amasiye ndithu 😭
@Sabina-hw4js
6 күн бұрын
Not even rich countries do that
@Hellenistic109
6 күн бұрын
What is Chiteze?
@JoyceLiwonde
4 күн бұрын
😂😂😂 Ndiwe wakuti dad
@KennedyKanyama-ce8lb
7 күн бұрын
Kulibe presdent kumalawi. Koma tili ndimbava basi. Ichichi chanditopesa koopsa ndikungolakalaka titavoter lero
@WillmotChiuimia-vr6ou
6 күн бұрын
Koma zowonadi mmmm
@IbrahimDailes
6 күн бұрын
Kd tchito yanu ndichani kmsotu anthuwo akuthawa dziko muno chifukwa cha umphawi kd nzelu mulibe zokonda anthu Anu kd mpando wako tchito yanji?kuba kuli palipose passport ya 120 anthu akutipeza ndi 300 000 ndrama mene zikusowelamu kd katangale umati atha uja ndi UTI chakwela km chakwela mulungu amaganizilaapo km dziko si lamakotu ili la 40 likubwelatu ngti umati siuopsezedwa ndye wina aliyesetu kmtu zinazi muzafa chiimile anthu atakwiya.
@ivymakiyi
7 күн бұрын
A kalindo mukulandira zambiri ku zipani mwathandizapo ndani inu?
@graciousmsema243
6 күн бұрын
That's not his mandate. He's not in control of our taxes
@Iponga
7 күн бұрын
The d c ulemu wanu mumatiyimilira mulungu azikudalisani pa tchito imene mukugwirayi
@AtupeleChitenje
7 күн бұрын
Chikangawa simuthu
@RabsonMwanza-d6m
6 күн бұрын
Ndipo zoonadii ambuye kumwambaku atinthandize
@SsBakali
7 күн бұрын
Silute
@CleverChiumia
7 күн бұрын
Kuti titumize kangachepe.
@MadalitsoBenjamin
6 күн бұрын
We are at stake of death
@OtamandaMusic
7 күн бұрын
Talking is cheap... cheap for chakwera and cheap for Kalindo too. Akhalako gao limodzi la athu oti adakathandiza, kod adatithandiza??? Stop Talking, Start acting. Ife tikujoinani pa actions po, it doesn't start with a president only, its starts with a citizen. You and me, not world or imf.
@CleverChiumia
7 күн бұрын
Mutipatsire nambala yu a DC( ABONI KALINDO)?
@JonesManyeka
6 күн бұрын
Ambuye yesu tithandizeni
@KondwaniJohn-mm3gk
6 күн бұрын
Illegal immigration ilibe zoti muzikambilana.... umbuli bwanji nanu? South Africa ikakambilane ndi Malawi kuti anthu anuwo azikhalabe akakonzeka azanyamuka😂😂😂😂😂😂 School ija osazaiphweketsa guys Salary ya mphunzitsi sinakhalepo yokwera kuyambila kale even nkhalamba Yako ili ku opposition yo imkalamulira. We know ukugwira ganyu wa DPP and you are paid for that to cease umphawi wako and continue doing but chakwera will be voted again
Пікірлер: 94