Kkkkkkkkkk koma chakwera ndiye ndiye zikuchoka kuti zimenezi
@RamseyWasi
21 күн бұрын
Blasa, Malawi saadzatheka mpaka kale kale. This is my second SMS to you mr Dangerous Child (DC) My opinion: Kungosiiya utsogoleri wa anthu osawukawu.chfkwa or titatan,kusawukaako sikudzaatha.
@SmartMoles
20 күн бұрын
Zofunikila kulangura mwayangure kumene
@BlessingsKalonga
20 күн бұрын
Ubwino wake ukuzimenyera wekha khondo uzalemera wekha
@ChisomoamitoniSauzandeamiton
20 күн бұрын
bwana ng'alurani ndithu tili nanu nanu
@JuliusMunthali-z7j
21 күн бұрын
Awuzeni
@directorkfuture118
20 күн бұрын
Ameneyo asamwe mowa 😂😂😂
@gerrardgladstone2473
21 күн бұрын
Akuti kufuna kumangidwaaaaa 🤣🤣🤣
@user-dm6xq6cp1m
20 күн бұрын
Ai zikomo 🥱
@HendersonDziwa
21 күн бұрын
Dzelu zachepa kkkk
@maxwellcaptain3937
21 күн бұрын
Kalindo samaopa😂😂
@TshepoModise-xs4qu
21 күн бұрын
Koma nkhaza zake mpaka licence ya mnchenga Mmmm zovuta bwanji eeee
Пікірлер: 81