President chakwela ndi wamwanotu alibe nazo kanthu kuti anthu ati chiyani iye akuchita zimene iyeyo akufuna basi.kuno ku south Africa a Ramaphosa samayenda ngati chakwela ayi.chikangawa ayi
Ine ndikuona ngati Boma ili lazama kwambiri ndi ntchito zakumidima. Chifukwa ndiye lakhazika chete ndi kumata pakamwa anthu pamodzi ndi azipani zosusa. This is not normal at all........ Sangatenge gulu la anthu onsewo kupita nawo kunja pamene Malawi wayaka moto ndi mavuto.
@MlecheFatch
23 сағат бұрын
Koma Mulungu simunthu atimenyera nkhondo
@eliffagondewe8214
15 сағат бұрын
Ndalama sakumagula anthu uphawi sizinthu. 💔💔
@ChilinguloRobert
Күн бұрын
Fisi ndi Fisi ngakhale mutamugoneka pa Bedi, adzilowa pansi pa Bedilo ndikumaphwasula Bedilo.
@RiteRoderick
Күн бұрын
Zoonad zedi brother
@BlessingsMakalani
Күн бұрын
AMalawi Tinachita mistake kusakha Boma ili 😭😭😭😭
@hanifahmponda8711
Күн бұрын
Iiiii uyu president wamitsala pafika Malawi pano kutenga anthu chigulu kumawononga ndalama za amalawi ANTHU AKUDYA CHITEDZE ENA GAGA aaaaa KOMA MCP MULUBE CHITSONI NDI ANTHU INU AGALU KWABASI
Mmene munkalemelera inu muja mesa munkamanga page house ma church a 50million kumanga ma lodge mu zenzamu kugula ma plot ndiye iwonso zivute?? Ngati simunalemele nthawi ya dpp basi zanu izo
@LovemoreSambuke
Күн бұрын
Tsiku Lina kudzacha 😢
@samanthamuller7643
Күн бұрын
Boni kalindo the DC mwana woyipa kwambiri
@EmmanuelMpalagule
Күн бұрын
Tsiku lina kuzacha ndithu osaopa
@MlecheFatch
23 сағат бұрын
Mulungu aweruza and watsala pang'ono
@ChikupizgaKajawaMkandawire
6 сағат бұрын
Awa a bon kalindo muntima munazaza nsanje kwabasi kulimbana ndi munthu oti samayankha ali ena akanachita manyazi
@SaeedMaunde
17 сағат бұрын
Ku Hungary wapita kotaninso abale chi munthu chosamva ngati ixhi sindinachionepotu ine
Sindikudziwa kt malamulo Amati chani a president zikafika apapa kt amenera kt apitilize kuramura eshiii 😢😢
@medsonmangani2685
Күн бұрын
🤣🤣🤣🤣
@MalikiAlex-wn8jc
14 сағат бұрын
Madala King 👑 cobra 🐍 ku chokela muzinda wa Maputo inetu ndi mapemphelo 🙏 angatu ndi MCP ituluketu 2025 mwinaso ifeso amene tilikunjafe mtendele tidzawupeza Born kalindo ulemu waketu Allah adzimupatsa moyo wa utalitu
@ChikupizgaKajawaMkandawire
6 сағат бұрын
Mcp szachoka mmboma
@ChikupizgaKajawaMkandawire
6 сағат бұрын
And chipani chilichonse chikuzapita chokha chokha pa ballot
@MosesDzonzi-em5px
Күн бұрын
Mmmmmm koma ndizokhudza kwambiri zimenezizi amalawi tiyeni tichitepo kathu
@PrinceBlessings-bv5bs
Күн бұрын
Mmmmmmm koma zaonjeza... Abusa alitenga dzikoli
@harrisonmacheso
Күн бұрын
The Deeee Ceeeee
@WarriorKB-u3k
20 сағат бұрын
Zoona kalindo chikangawa ndiwosamva,khutukumve,mbuzi za anthu MCP chipani cha anthu Osama,okuba
@SelinaGamaliyere-q8v
Күн бұрын
Ndipo chakwera ndi munthu oyipa mtima iiiii osaganiza za anthu ake ndipo mizimu ya anthu aja yamupengesa
Пікірлер: 82