Malo moti ma foreigner ngati ali andalama azigulitsidwa Malo abisness okha kuti nyumba azipanga rent Malawi kuwapasa pokhala azitasa ngati alikwao maiko otizungulira rent yeniywniyi foreigner amafuna akhale ndi residence permit koma Malawi tulo
@kidneyblessingschilinguloj7292
3 ай бұрын
More fire Boni we're behind you
@jameskamanga628
2 ай бұрын
Dziko la south africa ingakhale eni ake(mzika)alibe malo Malo onse ndi aboma 🙌🙌
@DawoodChisale
3 ай бұрын
More love to you Mr Kalindo
@charlesnota
3 ай бұрын
Bigup Mr kalindo
@Qspy-b9m
3 ай бұрын
Power speech
@Mohammed-sk1fy
3 ай бұрын
DC ndidolo ndthu fire 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥
@Vascomw
3 ай бұрын
Powerful 💪💪💪💪
@Shelifibraheem
3 ай бұрын
You are strong MAN big up bro!!!
@Mustafaaliki-tr2kv
3 ай бұрын
Best tv
@DavidJohn-x7c
3 ай бұрын
Dc
@JunaKananji
3 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤karido Dc
@moniqb7373
3 ай бұрын
Koma nde tisanduka North Korea via Zimbabwe tu...😢😢😢😢
@BrightKaotcha
3 ай бұрын
Kaswili, born kalindo.
@MerryWayson
3 ай бұрын
Mwana Wakwathu Ku Mulanje watulukilaso ndi chilungamoooo mulungu azikutetezani Kwa adani Boooooooon Kalindoooóoooo
@MerryWayson
3 ай бұрын
Mwadzuka bwanji
@MahallaMinistries-fv1hw
3 ай бұрын
Tembelero likakulitsa nkhutu ni mtima sidzitseguka. Too cursed to pick advice.
@ZioneMkwanda-y6i
3 ай бұрын
Ukamuzonda Bon Kalindo , yembekezera kt atamwalire nda abambo ako akuba ndalama za misonkho m' bomamo. We love the DC😅😅😅😅😅 moto kuti buuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@MirriamKambale
3 ай бұрын
Ndipo chilungamo ma foreigner kumakhala motakasuka kugula Malo motchipa opanda or ndondomeko ndipo dziko lophweka sinaonenso
Koma inu a Chakwera choti mudziwe ndi ichi,dziko ili ndi dziko la democracy,si dziko la chipani chimodzi.Ndinenenso kunena kuti dziko ili ndi dziko la ulamulilo wosiyilana koma chenjezo ndilakuti tsiku ndi limodzi lomwe muzaone ngati kuti dziko lino lakhala ngati dziko la South Africa munyengo ya xenophobia.Dziwani kuti simuzathawa ndipo muzasanza magazi
@ZioneMkwanda-y6i
3 ай бұрын
Watulukiranso Mr DC president wa ife wosauka,Bonnnnn Kalindooooo The DC mwana oopsya kwambiri😅😅😅😅
@AugustineTheu-of6nv
3 ай бұрын
Our president of poor pple speaking the truth without fear
@Robbie-w4w
3 ай бұрын
Powerful speech fadah
@BlessingsWickson-fv1xf
3 ай бұрын
Tell them bro were together 💪
@MustafaMausen
3 ай бұрын
Munsatope kutiyimirira bwana DC
@TalazanGamah
3 ай бұрын
😢we follow u brz
@ZioneMkwanda-y6i
3 ай бұрын
The DC Tell them 😅😅😅 liyaliya
@RichardSandfol
3 ай бұрын
The DC❤
@Lazarus-qo1sl
3 ай бұрын
The DC
@AnusaAwali-yh3wf
3 ай бұрын
Power speach mr kalindo
@GreciousMeleca
3 ай бұрын
Dats true
@JonathanBonongwe-f3s
3 ай бұрын
Osaonetsa kutopa Dc tinenereni
@ZiwaniMaseya
3 ай бұрын
chilungamo bomalasonekela
@DaitonKabila
3 ай бұрын
Kwanthele mboli yake
@MphatsoMzingeni-fg2lr
3 ай бұрын
Big man timakunyadiran
@eliasmpita3916
3 ай бұрын
You are very correct. Kukuoneka ngati tilibe unduna wazamalo and as if we don't have land policy.
Пікірлер: 54