King of truth dc licening from Durban sourth African
@KingDavedNkhata
40 минут бұрын
Welcome back the DCCCCC may God bless you❤
@PatrickWinifred-z3l
3 сағат бұрын
Welcome back dc
@FaithDonald-ts2pp
3 сағат бұрын
Tinakusowaniso nafe the DC ❤
@MarthaChigonero
2 сағат бұрын
Welcome back ndimasowa ntendele masiku amenewa kuti mulikuti
@Lovemore-i8c
3 сағат бұрын
Very straight forward
@OwenZimba-b4s
4 сағат бұрын
Welcome back the dc tinakusowani ndithu koma tikufuna tithandizepo paanthu akudya chiteze tipaseni number yolondola kutino ndalama yikafike isabedwe ayi
@ShaibuYahaya-qv6in
2 сағат бұрын
Welcome back DC 😊
@isaihmagani5697
4 сағат бұрын
Here am watching from Johannesburg moti ndagawa kale 10 kuchokera mu Utube,komwe ndimamvera za A Kalindo
Ine ndimamva chisoni Bon kalindo ndii munthu olephera anazakhalapo Mp ku dera la kwao koma chifukwa cholephera kupanga chitukuko kuderako anthu anamukana ndikusankha m’bale wake lero azibwera😂kuti ndi president wa anthu osauka zoona ndimadabwa antolankhani samamufunsa ndichifukwa chani anagwa pa Mp kudera😂kwao kulephera kuyendetsa kadera kakang’ono dziko angakwanitse?
Kumalawi timasogoza hate instead of helping our own country to prosper we always pull them down no wonder Malawi is on number 2 in Africa for the most powerful witches and wizards and witchcraft.shame on us
@RaffickVadrah
3 сағат бұрын
Story yomveka bwino Mr kalindo
@MynessChirwa
2 сағат бұрын
❤❤❤
@NaldodasilvaSilva-s1l
55 минут бұрын
Munatisowadi bg mn takulandilani
@GreysonLimula
2 сағат бұрын
Atlast the dc
@EusébioLucianoGaiondo
3 сағат бұрын
DC🔥
@HassanOmar-v2e
3 сағат бұрын
❤
@FidreckKamapalira
Сағат бұрын
Uku kunali kulira kwa Bon kalindo ndi chipani cha dpp
@NelsonMzoma
2 сағат бұрын
Afana omasuka osaopa
@EnockMatick-p1j
Сағат бұрын
Takulandilan ndinalindinkhawa bwanji
@DaimonManda
2 сағат бұрын
Yes
@PatrickChirwa-cv5cd
Сағат бұрын
DPP inamaliza UDF powalanda chipani ndi Eastern Region yonse. Out of 38 MPs UDF inatsala ndi 7 okha pomwe UDF imaphatikizana ndi DPP. UDF ikaphatikizananso ndinso ndi DPP itheratu tsopano. Bola MCP yomweyo olo angoima paokha. DPP sinathandize UDF.
@FidreckKamapalira
Сағат бұрын
Palibe yemwe angadzavotere nkhalamba yanuyo. And musaipangire chochita udf chifukwa ndichipani choima pachokha. Munamumanga chair and mzanu wabwera kudzamukhazika kukhala mfulu... Ekha munkamukonda chair ndichipani chake cha udf bwezi mutamumangabe chair ndikumamuvutitsa?? Anthu woipa inu. Zipangani zanu ku dpp kwanuko asiyeni anzanu apange zomwe akufuna
Пікірлер: 45