Kusachosako ndipomwe muziwe kuti ndi plan oseo anaphela limodzi sangachosani tichosa 2025 ndikuonanao zochita
@MustafarBridon
10 күн бұрын
Dc boniiiiiiiiiiii kalindoooooooo
@user-wx1jt5fd2j
10 күн бұрын
Munanena mawu a DC kuti amalawi siwowafera ndi chifukwa chake ziko lamalawi likupita aliyense akungoyang, ana tizionerani limodzi popeza tonse tili momwemu
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
10 күн бұрын
Basi khani ikhare tiwadikire 2025 Mesa kupusa ko tikunena ko anthuwa chaka chino akanayimisidwa akanayitanidwa ku bwalo lamilandu
@UthumanMwangala
10 күн бұрын
Amalawi ife tulo chomwe tkuzwa ndikudikila kut bakili tv kapena bon kalindo ayankhulalit pa social media tipange coment bas
@JoyceBanda-k8t
10 күн бұрын
Pepani aprezdent anthu osauka pp asakhale mawo pa mgwirizano chifukwa ndi joyce Banda mmmmmm timamuopa
@Mustapher-fb4qp
10 күн бұрын
Boni karindo warowa udf
@paulvan9306
9 күн бұрын
Zoona
@RobertPhiri-gt2cr
10 күн бұрын
The Dccccc❤❤❤
@user-wx1jt5fd2j
10 күн бұрын
Pangani gwilizano nonse mwatchulidwa apawa ma udindo oyamba akulu akulu muzapereke mofanana pozasata ndi m, mene chipanicho chizapezere ma percent ake
@SamuelLiwonde
10 күн бұрын
surely ma guys aku defence ndye anayenera kuimitsidwa
@ChimsyUlemu
10 күн бұрын
Kkkkkkkkk akakomoka kumangowathila acid basi Malo mwa madzi
@user-ps5tv4hq3c
10 күн бұрын
Yes ❤❤❤❤❤❤
@RobertPhiri-gt2cr
10 күн бұрын
Malavi onfire
@Cubotenterprise
10 күн бұрын
Amangidweee onseeewa
@Biath-m4b
10 күн бұрын
Koma iwe wayankhula bwino bwanj mpake tikuti ndizopangana bwanj sanamangepo olo mmodzi apa zikumveka koma so akuthawa chian mdziko muno kukakhala ku china akusowa mtendere uyo
@ChisomoBanda-g5s
10 күн бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉😢😢😢😢
@user-wx1jt5fd2j
10 күн бұрын
President chipani China vice chipani China secretary chipani China ndimaudindo ena zipani Zina mwina malawi angazaoneke kusintha
@williamlyton8016
10 күн бұрын
the DC mwana owopsa kwambiri
@violetpotani
10 күн бұрын
Uyuyu muti president yu asatiphwanyitse mutu tingoonda nazo izi
Anthu nde mwayankhula km sizikusintha pangofunika kumukolaso mdege yakeyo chakwela
@DalitsoTanganyika
7 күн бұрын
Nkhondo yathu tayisiya mmanja mwa Mulungu
@FrancisKamwendo-p2i
10 күн бұрын
Go deeper.ang'alulidwe basi
@NeemaMatewere
10 күн бұрын
❤
@jamesjolichi2026
10 күн бұрын
Bornnn kalindoooooooo
@Cubotenterprise
10 күн бұрын
Pagan comment smnuye
@Cubotenterprise
10 күн бұрын
Agalu a MCP
@AuphieBannet
10 күн бұрын
Diiiiiiiiiiiisiiiiiiiiiiiiiiiiii
@BarnettKathumba
8 күн бұрын
imfa ya chilima siizaiwalika
@AlickChima
10 күн бұрын
Kodi a born kalindowa anaphunzirapo za ndegeso?? Anahwiraposo ku army¿? Aaaaa zili zonse komenti. Asiyeni ma xpert azikamba zinazi za sewero la ADRAzi sizikuthandiza atah
@EmmanuelZiba-qz6ug
10 күн бұрын
😢😢😢😢😢
@SalahMhone
8 күн бұрын
Vuto lake chilungamo chimawawa
@LidyaGoodson-fb4tt
10 күн бұрын
Kkkkkkkkkk
@HendrickBanda
10 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥
@VincentAndrew-p8l
7 күн бұрын
Panyopako
@humphreyskasonde7096
8 күн бұрын
Iweyo ukazangopeza anzako ena atatu olimba ntima ngat iwe dziko lizasitha
Пікірлер: 56