Born inu muli pawiri tsopano kuopwa ndi ndi luntha chifukwa mita mumaionela patali kodintso ADPP mwayaba zotani Chonde tengani malangizo a born Kalindo wo koma ngati mukuopa munene tikuphempha born Kalindo kuti ayambitse chipani or asawinne bola azikazuzula komweko mwina muzizachita manyazi zoti kuli zipani zambili kwangoti ziiiiiiii AUDF bwanji nanunso mukudya nawo AMCP koma ndiye timakudalirani musamago pomwe alangizidwira namwali nawenso chimozi mozi chenjerani patawuni a chair adatero zikomo born Kalindo mawu ako sapita pachabe😭😭😭😭😭😭😭 kumulira Malawi komwe akunka nayo achitsilu Achakwera anthu tsiku ndi usana kuli osatsintha iyayi musintha liti😒😒😒😒😒😒😒😒
@user-dk6yc8pl2m
2 күн бұрын
The Dc❤❤❤ last mn standing for
@GRACIOUSCHIDZANJA
2 күн бұрын
🎉Mumakwana bro
@user-wu8kp7ui5j
2 күн бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥
@augustinechibbalazi8897
2 күн бұрын
We are all heartbroken to lose nine Malawians on 10th June.Should we keep on losing lives of innocent Malawians because we are lacking democratic philanthropy and patriotism here in Malawi.I entreat religious and traditional leaders to blaze a blissful trail of democracy.Join hands-on prayers our prophets not cheating us what future prophecies are all about if they can't redress the problems we currently facing here in Malawi.
@Mervic-vm8eo
Күн бұрын
Osawopa osatopa osafooka 💪💪💪💪💪💪🔥🔥🔥
@PatrickViyache
Күн бұрын
Bwana inuyo mumatiimilila kwambili ndipo anthu m,malawi muno ngati pali munthu amene mukuwafela anthu anu ndiye ndinu bon kalindo ndipo olo mukukumana ndi zowawa motani koma musasiye kutifera ifeyo?
@ArthurMukonkho-hg7hz
2 күн бұрын
Dolo wakwathu
@FosterMatungwe-r9t
2 күн бұрын
Za ziiiiii zeni zeni za umbuli basi
@EmmanuelLouis-t1x
2 күн бұрын
Kuyakhula mwa zeru heavy
@SamuelJohn-pc3ls
2 күн бұрын
BOOOOOOONI KALINDOOOOOH The DCCCC
@duncainjimmy
2 күн бұрын
Bon Kalindo wagwira ntchito yochenjeza malemu Chilima lero mawu a Bon Kalindo akumbukilidwa apanso a DPP alira
@SheenahMwalabu-iz3pr
Күн бұрын
Ndipo anayamba ndikale kuwalangiza malemuwa kuti aisiye tonse alliance chifukwa mcp ndiyoipa and akumupangila ziwembu, koma sanadziwe Chilima kuti amukonzekera motani ndipo akanadziwa bwenzi atawasiya a Chakwera ndipo chikanavuta chiwembuchi komatu kusadziwa ndikufa komwe 😢 amangoti zilibwino ndipo mdani amakupangadi attack pomwe mukudyera mbale ya nsima limodzi chifukwa amadziwa matemedwe ako anthongo. Bon Kalindo siwamisala ndipo ankanena kuti a Chilima samawada amawakonda, chomwe anaboweka nawo nchakuti zomwe analonjeza a Chilima wo ndi a Chakwera samazichita ndipo a Chilima amangokhala osapangapo kanthu. Ineyo since 2021 ndinaituruka mcp chifukwa chazomwe imapanga, Kuba etc ndimomwenso kalindo amanena koma anthufe sitimva ndipo kukanakhala kuti zomwe amakamba kalindo anazigwiritsa ntchito bwenzi alipo a Chilima 😢 aliyense adzafa koma not imfa zake zizikhala ngati izizi mmmmmh nzowawatu we hoped for Saulos ndipo sitidzamuiwala RIP our president ❤
@user-bd5kw8oq1r
Күн бұрын
Alibe chilungamo uyu ndi mzeru zomwe akamatero amakhala wafika pa munda pomwe amadyera ndiye ali ndi ufulu kupanaga zimenezo koma adzatuta zomwezo 😅😅😅
Пікірлер: 49