Nde wina kumanena kuti boma ndi lomweri 😭😭😭Mulungu akuonen
@GeshoMwakitwile
37 минут бұрын
Kunena chilungamo anthu akumwera akuvutika koma ma president awo anaba ndalama zambirimbiri kuli peter uku ,joice ,bakili uku Ali phee anthu awo akumwalila
@ChomboNgosi
51 минут бұрын
Our president ❤❤ ise osauka
@Mohammed-sk1fy
2 сағат бұрын
Zosayenda eeeehh amalawi tili pamamvuto kwambiri 😢😢😢😢😢
@PililaniChingo
2 сағат бұрын
Eee ndalira kwambiri chifukwa cha dziko Langa, MCP ndi chipani cha ufiti
Mwaika kumayambilirozotu szabwno bwana zkuchedwetsa kut tyambe kuva uthenga
@ShamimuBisani
2 сағат бұрын
Aliyense alindi ufulu oyakhul zmwe zamusangalasa phone yake data yake palib kupheran ufulu ky kuyankhan mabomba mabomba nthawi yatha iyi Kalindo umakwana
Пікірлер: 16