This doesn't make any sense,,what we need to know is the real cause of the accident,, we will be keeping in prayers to God so that he must exposed what happened.
@UmaliIshmael
3 ай бұрын
Akupatsani zingat kumeneko
@LaynaAdam
3 ай бұрын
Kwafa ndani kwa chakwela kuti mumpepese ? Mmalo mupita kwa mary amaliza mwana ndi bambo wa ana ake plz muziganiza azibusa inu popanga zinthu
@jamusnamwino-br2iz
3 ай бұрын
mukumuseweresa mulungu
@BrightZionga
2 ай бұрын
Kkkkkk chonyansa chija adachiona Daniel
@ExcitedCornflowers-nw9oc
2 ай бұрын
Chokanipo apa mbuzi zaanthu kukonda ndarama basi kupusisa ndani?opemphesa kulondora ndarama basi oapepesa ndi ameneoooh?osapita Kwa ofedwa bwa?kuseweretsa mulunguuh?akukantheni pamodzi ndi kwantere wanuooooh.
@donbastora854
2 ай бұрын
Zimapepesa zitchani izi zazii
@hamiltonsolomon3756
2 ай бұрын
Ine sindikumvetsa ayi.....Bwanji osakapepesa kwa Mayi Chilima kunyumba kwao kapena kwao Kwa Mr Chilima ku Ntcheu......Mwalandira chimbazi kumeneko? 🤣🤣🤣🤣
@MWAZANGATIPATRICKPAUL
3 ай бұрын
koma dziko la malawi mwalowa satana wamkulu, mutichan apapa
@emilynthite6545
3 ай бұрын
Mupha mipingo ndi dyera ranulo
@anthonysawa2039
3 ай бұрын
But why these old men?
@TrizaGeorge-q8w
3 ай бұрын
Pali athu ena anangikula koma m,zelu alibe wamwalila ndi Monica
@GiftFredoh
3 ай бұрын
Aaaa zachani mmalo mopita kwa chilima ndi ma banja enawo
@Alice-z7t4z
2 ай бұрын
Eti inu aaàaaaaa
@francismphande7181
3 ай бұрын
Sindikimvetsa chichewacho akuti akupepesa chani?
@MwaiPotani
3 ай бұрын
But guys sure the whole of you. You playing with God. Moti mu aye kwa MA Anja ofeledwa.
Пікірлер: 25