nkhani yokhudza age singapange affect utsogoleri zosatheka because tikayang'ana dziko lonse lapassi azitsogoleri azipembedzo komanso ena andale ndiachikulire so ife amalawi tisafoyire ndi bill ya agemet leadership isnot age but wise.
@ShabaniKuswere
4 ай бұрын
Akulu mukuti Chaweziwa ndi mbuli yamunthu ndithu mmutu mwawo mwadzadza mamina. Zoona munthu amene ali nzika yamalawi sangamatsutse kuti zinthu zakwera ndipo zikusiyana kwambiri ndi nthawi ya a Mutharika. Amibawa chonde mudziyamba mwayeza ubongo wamunthu musanamibweretse apa. Ndimati ndikuuzeni kuti akuluwa akubwera awa a chaweziwa asadzabwereso pano ndipo muwauze apite adzikapanga campaign ndi a Chakwera coz uyu ndi wa MCP
@chimwemwechathapo6405
4 ай бұрын
iweyo kulesa kuti ziko siliri pabwino?.. omwe mukunjoya ndi boma ili ndiwomwe mumabakira bomali... koma ziwani kuti akamakupasani dolazo sakupaza ndi azibale anu omwe. abale anu akuzunzika ngati ife ndipo akugona ndinjala inu mukudya bwino ndi chakwera
@YohanePatrick-lc2lq
4 ай бұрын
Iwe dpp ndi matchini wena lilongwe mene anayisithila
@TarPoor-ye9jx
4 ай бұрын
Vuto ndilot ukakhala pasana pa mjovu usamati kulibe mame ngat Inu muli oziwa mavuto amalawi osamangopanga blame dpp only u should blame also government as well. When dpp was ruling thing wasn't same ndpanopo things is worse Inu zot amalaw akumfa ndingala of course mvura inavta koma ena sanakolole kamba ka fertilizer anadura and wa sabuside sanalandile pitan ma shop akumudzi mukayang'ane soap,salt,soda, body lotion and chigao chadura umeneo ndi umoyo wamunthu wakumudzi that everyday life ndemusamabwele pano kumanena za dpp that nonsense inuyo mwalandila ndalama kuboma ndipo muchta kuoneka kut ndnu a mcp please amibawa musatipangise kusakupangan follow pazawande ngat ameneyo ndibwino mundu aziima pachilungamo but don't blame dpp just blame all politics if their doing wrong. Mcp is very corrupting government don't think the Malawian their don't see it ... let's wait and see 2025
@Allan-bk1
4 ай бұрын
Kkkkkkk amufuse hope chisanu
@hawabanda-xs5fx
4 ай бұрын
Bola ndi Peter sitimagona ndi njala timwamwaso tea
@isaacchirwa9518
4 ай бұрын
Nde dziko limenero m'bale wanga, or nthawi ya Peter ija enanso tea sankamuwona because 900 kwacha ankati wakwera mtengo kwambiri, panonso chimozimozi
@riversofgrace8350
4 ай бұрын
Inu mumadya ena samadya that time mwene .. moyo sukoma mbari zonse or nthawi zonse
@Sanney-vm5mw
4 ай бұрын
Peter yemweyi Ali khenge
@peterjoshua2595
4 ай бұрын
Uyu mukumuti Chawezi agwesa mibawa, I follow Mibawa chifukwa cha Bima
@esthergweje4038
4 ай бұрын
Amibawa asamamutenge chawezi
@kondwaninampeya5780
4 ай бұрын
nzelu ulibe
@DavidPhiri-o6w
4 ай бұрын
Chawezi keep on reminding Malawian kuti Peter muthalika palibe chomwe azapange kukoza dzikoli
@robertnambazo9936
4 ай бұрын
Chawezi sukuziwa how Malawian are crying out there uzipita kumudzi and see how much people are suffering kulephela kudya phalala ayise
Mr Sandra ma feel anu mkulu akuyakhula mfundo zompand mzeru chawezi wanuyu,alanine kuti Malawi wakwera kwambiri muthWi yachakwera,koma akuganiza ameneyu.
@JusticeSalema
4 ай бұрын
Chawezi...by the way you are very very very useless. Don't think you are too wise. Sandram plz tell your friend Zasataniki zunena nzakoyo akagwereuku Kaya
@ShadreyChinga
4 ай бұрын
Ndi kape
@YoungMwacho
4 ай бұрын
Account number one ili ndi ife? Why blame the people, Chawezi you are exposing your stupidy ndipo uwononga Mibawa TV imene sinali political.
@petersomanje5632
4 ай бұрын
Aaaa chawez ndwe mbuzi ya munthu ndwe wa mcp galu iww
@Sanney-vm5mw
4 ай бұрын
Chawezi mbuli ndiwe ndi makolo Ako ndi mcp nonse
@StevenLeoJana
4 ай бұрын
You are so pompous. You can't say over 20 million Malawians are savages. Thus stupidity.
@FrancisChalamendo
4 ай бұрын
Apm my vote inu mwatumidwa
@MayankhoKalenga
4 ай бұрын
Chawaz amakonda amalawi alind zeru l would like to meet dat dude
@khumbomunyenyembe8107
Ай бұрын
True..Malawi kudana ndi chilungamo ..
@PeterMaster-yi9ep
4 ай бұрын
The guy is right
@DjshukulanGift
4 ай бұрын
Mmm chewis ukuchita kuonekerat kt iwe ndi wa mcp bas ,anali ose ku amaleca
Joyce banda anawononga dzikoli apm anakudza apatso akudziwakuti ama sokonedza ni chilima ku dpp ndiameneso akuba ku mcp dpp moto
@BilalAliyah-k1f
4 ай бұрын
Chawezi which side u re?tell us now,
@NicholasKwajama
4 ай бұрын
Anyamata onsewo akufuna ku parliament
@EmmanuelGasiten-fo5dr
4 ай бұрын
MIBAWA! musawononge wailesi yathu yokondedwayi chifukwa cha FISI uyu. anali ku MBC ndi program Amati TIMVESETSE, tinasiya kumvera wailesiyi. Lero mwamutenga uku, tisiya kuikondanso MIBAWA. sangatiuze zochita ameneyi ife timadya zathu. Chitayireni kunja chisanunkhitse wailesi yabwinoyi.
@chiefmalindi4070
4 ай бұрын
Achawezi amakonda kunyoza Malawi Kuti NDI mbuli
@ChikondiChagoma
4 ай бұрын
Km utolakhani kumibawa walephereka, objective palibe mmmmm mkwa bwino ndsiye kusata mibawa radio. In truth ma president ose Ali ND maweekness and strength km zopanga point Muthu mmmmmmm Chawezi sindngamulembe ntchito
@Milanzi-nb5fv
4 ай бұрын
Zonsezi nzopanda nzeru, chanzeru ndichakuti MCP singawinenso koma😂😂😂 or mukambe za ku America athu akumuzi chomwe amafuna kudya. You don't know how people are suffering mmizimu, ukayankhule mmizimu uone ngati ubwele wamoyo😅 I understand ndiwe wa MCP koma simukuwinanso😅
@KellyHart-pi4hd
4 ай бұрын
Koma mkulu uyu mukuti Chaweziyu ndi mbuli yophunzira srs ndipo wandinyasa
@AhamadiAlifu
4 ай бұрын
Akuti chawezi kaya akuti kawiza ameneyo wawukape zedi komanso ndi mcp mmaso mthinamo mumuwuze
@alexanderchamgwera-jm1qy
4 ай бұрын
Chawezi akugula aboma iwe galu zako zimenezo chakwera pa zaka 4 wapanga chani olo amangapo chani nziko muno
@ShareefSladge
4 ай бұрын
Mwangodanaye APM achawezi Banda moti Nima akupanga konkuno Yu nkhani yake
@YohanePatrick-lc2lq
4 ай бұрын
Komasotu ulwamulilo wa dpp unasitha dziko lamawi
@PeterMakaika
4 ай бұрын
Ameneyi ndi kape Chawezi...
@NtchindiChirwa
4 ай бұрын
Chawezi vuto ndi umbuli more 🔥 fire
@EmmanuelKaipa-rg1lj
4 ай бұрын
Achawezi mumalankhula ngat modzindikira koma ndnu opoira zomwe mukambadzo,usasokonedze mibawayo timaikonda ife ,Peter boma anasiya 1.9billion us dollors koma zonse munadya achawez muli ku mbc muja
@Donnexbatumeo
4 ай бұрын
Mibawa with Chawezi is now useless. Mapwala ako Chawezi
Agalu Inu ndinu andale A MCP why you just blame DPP kumanena kuti MCP Ikuyendesa bwino ziko
@D.RJALLI-qo6yd
4 ай бұрын
Eeee ndachakwele ndi amene wapangisa 10 tirion yabwela bwanji galu iwe peter anasiya 3 tirion ngongole ndiye mukubwebweta pamenepo mwakuudza Ana akupasa chani achakwela anuwo chimuthu ngati chakwela wanuyo galu iwe
Paja mwati this program is paid for.. Mcp is behind... Paja akmaktumizani kunja.. Kazidyani ndalamazo😅
@davienomale1722
4 ай бұрын
I don't want to insult chawezi but please don't let him come again find someone neutral not msabwe ya mcp iyi.
@PrinceKachimanga
4 ай бұрын
Chawezi ali mbuuu...he is not even rich.Uyuyu...ayipitsa mbili ya MIBAWA TV
@isaacchiwaula731
4 ай бұрын
Nonse muku- comentar apa ndinu a dpp simungaone zoona zomwe chawezi aluyankhula, anunkha dala inu. Mwaiwala kale zomwe dpp inapanga this few last 4 years yomweyi?? Iiii koma alomwe inu, mbuzii za anthu. Chawezi💪
@AsanteSainet-sp5pg
4 ай бұрын
Mbuzitu zkmakhala mnkhola kma ndati tiwonana 2025
@Sanney-vm5mw
4 ай бұрын
Dpp ndinayitaya koma apa ndabwelelanso osati abakhawa
Ndiwe opusa ulibe fundo unaphuzirs Za chuma ndi wekha buli ndiweyo iwe ndiwe buli kwambiri akupatsa ndalama .COVID munthawi labomo la dpp inaliponso. usatipusi
@OdreckNdemanje
4 ай бұрын
Yes,Mutharika did it in 2014,he tuned around the economy after Joyce Banda and cashgate. I think Chawezi is out of his mind.
@RodneyWandani
4 ай бұрын
Mibawa tv please asichiru awa ndisazaoneso
@ChikondiChagoma
4 ай бұрын
Ku mibawako pepho langa ngt muyifuna business muchoseni Chawezi
@JohnPetro-vv3er
4 ай бұрын
You are also one of them munthu osazindikila chawezi
@DavidPhiri-o6w
4 ай бұрын
DDP has no problem to run Malawi but not under peter muthalika ayi peter muthalika nfi munthu woipa kwambiri, munthu ozikonda. DDP supporters mukapita ku conventional mukasankhe musogoleri wina not Peter muthalika. Peter muthalika sazalowaso munoma weather you like or not
@Cosmassaiwa
4 ай бұрын
Mmmmmmmmm not Peter, ukudziwa kuti atenga boma. Wait and see
Пікірлер: 531