Comrade ntanyiwa fans let's gather here much love you do open our eyes always ❤️❤️❤️❤️
@Fanie-i7z
2 күн бұрын
Ngati iwe ukuti anthu asamvere limpopo iwe amakutuma ndani kuti uzimvera ambiri timamukonda amatidziwitsa zobisika keep it up Mr. Mtanyiwa tikumvera pano pa Port Elizabeth RSA.
@chippakaribafox2865
Күн бұрын
Nuff respect comrade ntanyix....you got no idear how much pple likes this channel
@osmaniwen2979
8 сағат бұрын
Comrade Ntanyiwa Ur the One❤
@GiftMlinde
2 күн бұрын
Greatt abweleleeee kumakhululukilanaaa
@AuphieBannet
Күн бұрын
Tili nanu ❤Mr. MULUNGU adzikudalitsani ndikukutetezelani nthawi zonse
@augustMag
2 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥 Abwerenso ku DPP Tawalandira bwana Nankhumwa ndi wanthu wanthu amenewo🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤
@dalitson3558
Күн бұрын
We need him back he’s good man, anthu amakhululikilana
@YusufuYunusuSavielMakey
Күн бұрын
𝐮𝐤𝐮 𝐠𝐨𝐨𝐝 𝐦𝐚𝐧 𝐰𝐚𝐤𝐞 𝐨𝐭𝐚𝐧𝐢 𝐨𝐦𝐚𝐠𝐰𝐢𝐫𝐢𝐭𝐬𝐢𝐝𝐰𝐚 𝐧𝐭𝐜𝐡𝐢𝐭𝐨𝐰𝐨
@SaulosMbuna
Күн бұрын
Comrade osayamba kudzikaikira ayi...u are a real big boy..
@SolomonAmiduh-y6x
2 күн бұрын
Anankhumwa welcome back ku dpp siyanani ndi chikangawa
@KandawekoChirambo
2 күн бұрын
Viva Limpopo Vivaaa
@KingDavedNkhata
2 күн бұрын
Motooo kuti buuuuu Comrade, musatope, osagonja ndipo osafooka Mulungu ali nafe nthawi zonse Aaaah inuuu, kkk Ana achepa awa zayamba kuyang'ana kungolo mizimu ya anthu ochuluka munawapha osalakwa inu mumati
@WarriorKB-u3k
2 күн бұрын
Timakunyadira ntanyiwa,umakwana DPP oyeeee!
@stevenmwamadi3035
2 күн бұрын
More fire comrade ntanyita osaopa osatopa osafooka Allah alipo mpaka tituluke mukaporo tilinawo pano ndi boma ra crocodile
@BairdThomas-c2k
2 күн бұрын
mwana wolowerela nankhumwa timulandila
@MagretMakhumula
55 минут бұрын
Bravo nakhumwa go back that's we want
@WilisonWilliam-d9j
2 күн бұрын
❤❤ife waiting
@MonicaSteve-t5p
2 күн бұрын
Bas abwelere wadziwa ubwino wa adad ❤❤
@DCpangolin
Күн бұрын
Asamulole ameneyu
@amosphakira7936
2 күн бұрын
😎😎 Adawa amaitha 😅😅
@MiddayDeleza
2 күн бұрын
Kondwani nankhumwa ngati akufuna kuti abwerere ku dpp ndakayika bola asakakhale spy wa mcp
@DadyPatrickMtondo
2 күн бұрын
Because he knows that he won't be an MP again, writing is on the wall!!!!
@EmmyYafete
2 күн бұрын
Abwerere palibe nvuto timulandila,kunkhululuka basi ndimasewera adziko lapasiwa.
@JessicaManda-zm1ug
Күн бұрын
Yomweyo chikangawa iwe 🎉🎉🎉🎉🎉
@BilalAliyah-k1f
Күн бұрын
🤝
@FredKanyerere
2 күн бұрын
More fire comrade, zovetsa chisoni.
@BerthaKasambala-y5k
Күн бұрын
Nkhondo ndi anasi anampereka yesu ndiwomwe amadya naye rimozi amene atapereke u t m mmanja mwa adani ndiwomwenso akuwoneka ngati abwino
@MusaLion-os1lx
Күн бұрын
Uyu ngat abwere ku dpp basi azatenga udindo 2030 serious boss Anakhumwa your welcome Mr Nakhumwa
@JosephHill-fy1bb
Күн бұрын
Asayelekeze kupita ku Pej house,, ndipo asayandikilane ndi Adad athu,, angawapopele poizon.. Amutuma ameneyo, siza straight zimenezo..
@JamesLongwe-qz9fd
Күн бұрын
Mukhululukireni munthuyo abwelere kunyumba kwake
@Maickfoness
Күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 Koma nanuso mukati mukomese
@CatherineDesire
Күн бұрын
Koma mtanyiwa mwana iwe mmmmh ndi Junior wa Blenac 🤣🤣🤣🤣🤣🙌yomweyo mtanyiwa
We don't need him, he just showed us how an settled he is, ndale za nkodzo tatopa nazo, take us seriously, we are not going to stand and look anymore, malawi up, n do right thing
Пікірлер: 135