I respect your mtanyiwwa and everyone else has been in Malawi arraund shitpha two nsanje
@ShamimuBisani
2 сағат бұрын
My broh ur welcum MCP ikufuna anthu adziwapembeza wauze kuti ife ai timaopa Mulungu yemwe analenga kumwamba ndi dziko lino basi uthenga umenewo ukafike kwa asatanawo
@RoseThindwa
2 сағат бұрын
Eish Malawians tinasakha molakwika boma ili more tricks Tiyeni tigwirane manja pamseu commission of inquiry ikuchedwa
@violetpotani
2 сағат бұрын
Yofunikatu yeniyeni osani manyaka and anthu wo okhudzidwawo plus boma asakhale nde zithekadi
@chirwaellace1093
2 сағат бұрын
May God protect you comrade
@EryvinMhango-zl3oh
3 сағат бұрын
Wlcm bck Mr mtanyiwa
@MariaNyamwera
2 сағат бұрын
Or achonge mavotiwo koma mcp ikuchoka afune asafune out
@PetroMatias
2 сағат бұрын
Koma abale musamasowe
@EllenGomani-i4f
2 сағат бұрын
Mumakwana big🎉🎉
@Halima-i4x
Сағат бұрын
Ausen aziwe 😅😅😅😅 aona chaka chamawa kkkkkkkkkk
@mcsellahntv6896
Сағат бұрын
Mpakana achina Makhazi kuzaimba ku nsonkhano?? Mhh Chikangawa Party Misalatu iyi. Ndiye azabwelensotu azavote.
Пікірлер: 36