Why did we lost our grandparents so early just because of stroke while mr BANDA is there😭😭😭
@FrancisWaliwa
15 сағат бұрын
Brilliant research Joab. My interest is Banda's succession plan...this good work needs to continue even after his life; who is he training to takeover from him?
@isaackaphuka
2 күн бұрын
This guy (man) is well educated
@SelinaSingini-b9e
2 күн бұрын
Awa nde ma program oti munthu uzinvela ndithuu... thanks joab chakhaza ...tamphunzila ndikuziwa nawo zambili....
@EltonMithenga-zl3bu
3 күн бұрын
Akamuna awa, ndapeleka ulemu tidzacheze one day mwatsilizamo
@BonKuloweka
4 күн бұрын
Chonde tigailen fon namba ya mkuluyu
@CedricMbera
Күн бұрын
Very genious man, ndaphunzira zambiri
@KingsleyKaphwereza
Күн бұрын
Mkulu uyuyu simunthu wamba amatha. Respect DR
@andrewmngombe-qt9kc
4 күн бұрын
Engineer of human body.. Eeeh akaka kandiwaza heavy
@HajiraKapinga
5 күн бұрын
Ntchito yabwino neba
@MiddayDeleza
3 күн бұрын
Anthu timafadi chifukwa cha kusadziwa zamphambvu ndithu big man
@mcdontonchida4761
4 күн бұрын
mitu ngati iyi imazatchuka ikafa alimoyo ai ndithu
@andrewmngombe-qt9kc
4 күн бұрын
Sikunama ase
@fostersimbi8820
4 күн бұрын
Koma ndipo man.... Luso ndi nzeru izi azapita nazotu izi
@GreysonGrey-zd5wq
3 күн бұрын
So inspired n motivated, what a gift, groly be to God
@LumandoBanda-q2i
3 күн бұрын
Nanga tingalumikizanenawo bwanji pakuti simudatipatse ma number wawo?
@eliaschagonah8256
3 күн бұрын
Johnson Johnson Powder wandilira😂😂
@AishaAbdullahMustafah
3 күн бұрын
Awawa ndi madhala kuyankhura momveka bwino
@louisbonongwe8537
3 күн бұрын
Boma bwezi likugwilitsa ntchito anthu ngat awa nzipatala zathu.....bwez zinthu zikuyenda mkumaseva ndalama timapita nazo ku india.
Amalawife tili ndi lunso amatisokoneza ndi yemweyu ali pa mpando yu
@MphatsoKhumbulani
3 күн бұрын
😂zoonadi nacimeteyu ndamene amatilakwisa
@foscohSamboko-uz1ex
2 күн бұрын
Brilliant research amwene
@fbtalent4811
2 күн бұрын
which country is this?
@paulphiri-fz9me
2 күн бұрын
Malawi my dear
@patrickmasa7145
9 сағат бұрын
Spain
@tenexchikumba
4 күн бұрын
Zikumveka
@zayedmitawa8345
3 күн бұрын
Kuli kwina kwake mkuluyu Ali nao mu gulu lopeleka ma license ku anthu azitsamba. Mkuluyu ayenera alembe buku lake la zitsamba lomwe lizigwititsidwa ntchito mzipatara mdziko muno komanso kuphuzitsidwa masukulu just like Biology. Matenda wanena apawa ndi omwe akupulura a Malawi.
Пікірлер: 108