We are not scared of anything as youth. Whatever step they are taking against us will still not give up. We are youth representing 75% of this population. Let's be united and not give any chance to play us these recycles politicians. UTM 2025 Boma, whether they likes it or not.🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@stevengeorgechakhumbira1508
2 ай бұрын
Don't worry we v youth ere behind you
@AishaChibwana-b8o
2 ай бұрын
Utm my votes ❤❤❤
@JoeSawa-m9e
2 ай бұрын
Give this guy a chance to stand he can make it
@alickkachepa3801
2 ай бұрын
Kwa batsi
@JohnConar-kq4hi
2 ай бұрын
The king of king 🤴 🎉🎉🎉 brother bt I don't understand the language
I like his confidence akamalankhura a true soldier 🪖
@AnthoniohMazengera
2 ай бұрын
My king fredo God bress you
@henrymalepula2934
2 ай бұрын
Fredo u deserve to be the president kunthazi uku
@blessingsmuyeya
2 ай бұрын
Nsaname These guys can be a better opposition party. Izi zomati osafooka, osaopa izi... Simfundo zolamulilira ayi....😂
@AishaChibwana-b8o
2 ай бұрын
Osaopa osafooka osatopa ndi chimodzimodzi kunena kuti DPP woyeee kapena kwacha aaaa tisiyeni mawa muzachita manyazi
@SangwaniThika
2 ай бұрын
UTM WOYEEE
@VailetnyirendaShamah
2 ай бұрын
Chonde ngwilizanani ndi azanu mugwetse galu otchedwa chakwelayu please
@NancyNyirenda-v9o
2 ай бұрын
Imwe mwajiyika pagulu uli akulu wake lamunkhwele or mbuu 😅😅😅
@innocentjuma2950
2 ай бұрын
My team ❤ love you guys
@PrinceKachimanga
2 ай бұрын
fredo...akakhala ndi ukali...he can,make a good leader wa UTM
@DamaliceWamalanguluko
2 ай бұрын
Ima president fred mulungu ali mbali yako usafooke usatope
@MercyKatongo-p9b
2 ай бұрын
For sure saulosi chilima in our hearts rest in peace bro
@jamestembo6724
2 ай бұрын
Fredo walindichikoka heavy ngati skc
@GeorginaChaduka
2 ай бұрын
Sawina u mp bwaaa😅😅😅
@ConnexMtika
2 ай бұрын
God will help us to go through
@stanleynampuluma4292
2 ай бұрын
Bingu ankaoneka opanda mfundo akamalankhula koma ntchito za manja ake zinamuchitila umboni. Awa amene akuoneka opanda mfundowa akhoza kuzakudzidzimusani mutawapatsa mipando. We have tried the rest and in my view, they have failed miserably. Komanso note that ku ndale kulibe woyera mtima. Just choose the devil you like and move forward. Ine ndasankha omwewa a UTM wa🔥🔥🔥
@FosterBochwana
2 ай бұрын
Mafana oganidza booh
@MercyKatongo-p9b
2 ай бұрын
With you guys Zambia
@Andrewmwamadi
2 ай бұрын
Northern region z for utm wina chake kulibe chake
@aggiemlotha1208
2 ай бұрын
Koma anthu musowa zochita... awa ngowadalira😂
@PrinceKachimanga
2 ай бұрын
chipani chili ku mala ichi...apa tingatimbanga kuthengele cha😂😂😂😂
Mabala akuwawa. 4 hrs mumafuna kut aphuphe mpaka afeletu.
@FannyThengo
2 ай бұрын
UTM my vote🎉🎉🎉
@MakhiMakhi-w6t
2 ай бұрын
UTM never to win
@NovemberMmangathayo
2 ай бұрын
Ndikumalila gyz chilima
@ElinesevitaGondwe-cq7tn
2 ай бұрын
Ohooo zangoyambaa
@DavidPhiri-o6w
2 ай бұрын
Vote for me Fredo and USI only
@FannyThengo
2 ай бұрын
😂😂😂😂😂Boma ilooo❤❤❤😂😂UTM
@OBEDIENCERENOLDSKAMANGA
2 ай бұрын
UTM BOMA OSAOPA , OSAFOOKA
@lenardmakuya
2 ай бұрын
Fredo iweo nd one
@0wenNkhambule
2 ай бұрын
Amen ❤ good Message
@abota71
2 ай бұрын
Awaso a Freddo alibe ndi fundo zomwe. If this is the type of leader Nalawi is looking for, then Malawi is doomed. Bola azingoyimba tima Rap music tawo tija.
@SafariBvumbwe
2 ай бұрын
Kkkkkkk yakubayani broh
@FanuelSoda
2 ай бұрын
Ntchana ❤🥳🔥
@SherifaG.Mlelemba
2 ай бұрын
A fredo naonsotu apole mototu......
@stevengeorgechakhumbira1508
2 ай бұрын
Akaliat omwewo kuti wawaw
@Prianka567
2 ай бұрын
Ma power hungry awa akukunamizani iyi ndindale chilungamo mulibemo adzakutayani paliponse
@Aaronsimbeye-e5m
2 ай бұрын
❤❤❤❤
@gracemkandawire8769
2 ай бұрын
Oaopa osafooka,,chipani ichi sichizatha
@EstherBonga
2 ай бұрын
Fledo ndi usi wanfundo ndi fledo
@stevemtambalika
2 ай бұрын
Ai Ali ndi chikoka😂 mwanayu
@isaacknbotha169
2 ай бұрын
❤
@chippakaribafox2865
2 ай бұрын
He didnt mention the short guy
@actuarialscience2283
2 ай бұрын
I love you UTM. I love DPP.
@SaidiMbawa-st6bj
2 ай бұрын
Ana inu ndale mwachepa nazo
@Pangolinimw
2 ай бұрын
Inunso mwachepa galu iwe
@trynessmsowoya4187
2 ай бұрын
2025 bola kusazankhale kufa may God Guide our malawi
@NancyNyirenda-v9o
2 ай бұрын
A fredo kazingoyimbani uko ife timakokondani zandalezi ayiii
@AlexKatete
2 ай бұрын
Feredo mmmm ndiwachikoka
@AshrafSadala
2 ай бұрын
Tchayyaaaa....!!!! tchayaaa..!
@soulkanyinji982
2 ай бұрын
Congrats UTM members
@NovemberMmangathayo
2 ай бұрын
Fredo ndi kaliyati limbanintima yehova alinanu
@chirwaellace1093
2 ай бұрын
Be blessed all
@talimilejosephmakawa4967
2 ай бұрын
Ma guys awawa Ali ndi chikoka
@Biath-m4b
2 ай бұрын
Fredo usasiyane ndi mai kaliati pachipani mukukwanitsa gwilanani manja ifetu pambuyo panu anthu olimba mtima ❤❤❤
@LukaJaulanchirwa
2 ай бұрын
So ife tili kusouth africa mzatirora kutenga National ID
@DerlinNyirenda
2 ай бұрын
As you are talking you are being used by your leaders
@chifundoKaluvi-ey5uw
2 ай бұрын
Imila upresdent fred o ife akutheba tibwela tikakuvotela
Пікірлер: 126