Iwe usatipusise mr dausi munthuyo anali waku ghana osati malawian
@chrissygama8678
Жыл бұрын
Kod atanena chilungamo kut sadali waku malawi zingachtike
@MrcharsCollen-cy6cr
9 ай бұрын
@ dausi you are chamilion
@frezarphiri3480
Жыл бұрын
Kamuzu uyu anapha real kamuzu wakukasungu uyu analamula Malawi uyu kwake ndiku Ghana uyu not Malawi ayi anapha anthu amalawi ambiri azelu zawo ndikalingalira anthu awo ndimawawa mutima kwambiri ndi chipani chake cha mcp
@frezarphiri3480
Жыл бұрын
Dausi ayi osathawa fuso kamuzu ndiyo anati tikhale ndi chipani chimozo not aleke banda ayi
@yusufsadic2930
Жыл бұрын
Program ngat izi pls tamaperekan mpat ot anthu azimufunsa olankhulayo kups kt munth mmodz azingowanamiz anth wabodz uyu
@maskinmsungeni8763
10 ай бұрын
Ukumuyamikira umamuziwa bwino koma? How many kilometers from kasiya to South Africa? Anakupasa zambiri eti?
@dondamissonchdziwe3958
Жыл бұрын
Kamuzu Banda sanali wakuno kumalawi,koma anali wabwino woipa amapha wanthu anali osatira ake joni tembo, kazamira,kamwana,ndi amzawo ife tinali kusukulu tikuziziwa,uyunso dausiyu akubisa zina ine mwana wa pasapitwa pa Mulanje ndikuziziwa bwino ngakhale ndiku kalambira kunja
@yasitafuphiri-nw2he
Жыл бұрын
Come in Malawi and explain better about Kamuzu Banda
@maggiekamphinda5699
Жыл бұрын
Hahaha anali dictator
@MitengoFrancis-sp9ox
Жыл бұрын
Kodi mwafuna Kuti. Anthu amve Za kamuzu kapena Matamata amayankhulidwe?🎉🎉🎉
@user-vh9uk1jy7w
9 ай бұрын
Nichoka Dausi bodza sanali mmalawi
@yasitafuphiri-nw2he
Жыл бұрын
Inu mukudziwa zambiri za kamuzu Banda pitani ku Radio mudzatilankhule zoona ndinuyo ,osamawawata pa KZitem pano ai
@gilamwelekedwa4889
Жыл бұрын
Just google the Kamuzu Malawi history Wikipedia page tells it all .
@gamammwenye
Жыл бұрын
who wrote the history if not people with biased minds....
@chiyenangomba3330
Жыл бұрын
Kamuzu olephera kuyakhura chichewa, he was from Ghana
@user-nt5cx3qj4m
9 күн бұрын
The same as Kenneth Kaunda who was a Malawian ruling in Zambia
@johnman4619
Жыл бұрын
Zopusa munthu wanji osatha kuyankhula language yadziko lake ..inuyondamene mudaona dziko ATI kamuzu.osati chigawenga
@user-qh5jo5qh3b
Жыл бұрын
Koma akat alowenze maina 😂😂😂😂
@daviekamanga1417
Жыл бұрын
Kaya anali wakugana kaya mumalawi zonse zilibe ntchito za dictator izo olo masiku ano ziliko mukumuona piter akufuna kuimaso ndiwo udictator woooo kusaona adzake kuti angayime
@kariyobaker9617
Жыл бұрын
What language is this ? It sounds like some of the languages spoken in Uganda, Rwanda, Burundi and far north western Tanzania. It is a language I can learn easily and quickly.
@maxwellchibwe5956
Жыл бұрын
Chichewa language that's the local language in Malawi
@kariyobaker9617
11 ай бұрын
@@maxwellchibwe5956 Thank you. This proves that African peoples are one or have the same origin.
@user-pn7ek7wb7n
Жыл бұрын
Peter munthalika chichewa chimamukanika bwanji
@gilamwelekedwa4889
Жыл бұрын
Who was the first prime minister that time? You’re not saying the truth about the history Kamuzu was not the first prime minister after the federation you don’t know our history 😂😂😂 go back to our country’s politics history Mr Dausi
@frasernamaona-qs6ts
Жыл бұрын
Mmalawi wosatha chichewa Komatu akuti anachoka kaya ali ndi dzaka 11. Ndan angayiwale chiyankhulo chake? Ghanaian uyu
Пікірлер: 27