Kkkkkkkk Jessei yemweyo,koma umbuli uli Ku a m c p iiiii chipani chochitisa manyazi Mai kabwira zomwe mukupangazi mudpitadi Ku school?mwasavuka Mai sinthani,mwabwera uyo, uve weniweni,sinthani
@SamboMaria
18 күн бұрын
Tikadalibe muu kapolo. Mzungu akadatilamulira, akudawa ndizikwangwani...
@bridgetmajor3646
18 күн бұрын
Well done gyz kulakhuka moveka Bwino 💯💪
@MayesoBikefa
17 күн бұрын
Bomali ose saziwa kathu
@SteveChapola
18 күн бұрын
Kabwira akufuna kudyanawo ndalama kuba basi
@victormbewe7462
18 күн бұрын
I like the word tipatsane ulemu 😢😢 otsamangoti boma ndilomweri ngati ndi ufumu
@user-hd7wq2yc6m
17 күн бұрын
A Brian Banda program yanuyi yalero ikanakhala album tikanangoti, the very best of Brian Banda Hot current because mwayankhula chilungamo, kaya nchifukwa choti IMF yavumbulitsa Bomba mukanakhala kuti m'mbuyo monsemo mumayankhula chonchi bwenzi mwina zinasintha komakayankhulidwe kanu m'mbuyomu mumanyengerera andale makamaka olamula achipani Cha mcp zimenezo ndi chifukwa anthu ambiri ngakhale kumamidzi amakonda kumvera pa social media , ngati kumamvera achina Limpopo , Ntanyiwa, Bakili Muluzi TV ,Bon Kalindo ndi ena amene amanena chilungamo mupotolize monga m'mene mwayambiramo thank you guys
@lacksonsiyadi943
18 күн бұрын
Azungu atigwira ufiti
@AubreymedsonMbewe
17 күн бұрын
Akuti nansonjola alipo m'bomamo kkkkkk😂😂😂
@LenardJames-j1n
18 күн бұрын
Nde kt Wa bakili mulizi TV uja amakamba chilungamo
@imraanJafal
18 күн бұрын
Kkkk nose ulemu wanu lelo mwafika ndi truth
@LindaLimbe-fo1oy
18 күн бұрын
Job well done
@RobertLuka-wy9cl
18 күн бұрын
🙏🙏🙏🙏🙏 All guys God bless you all
@IssaJohn-cb8vn
18 күн бұрын
mcp ngakhale yitatani yitatani yikutuluka boma basi
@user-hd7wq2yc6m
17 күн бұрын
Akabwira ndimunthu wopita ku school, koma ndi mbuli ya munthu akakadayenderabe zomwe zija za Kamuzu ngati chipani chimodzi,sasiyanitsa ntchito za chipani ndi ntchito za boma ndichifukwa chake akufunanso kutengera dzikolli konkuja ku one party system ndiye za a Jesse Kabwira mbuli yophunzira
@stynessphiri
16 күн бұрын
❤ Mumakwana
@Vascomw
18 күн бұрын
We are with you from uk ❣️❣️
@evathamanga1242
18 күн бұрын
Adayedzeka kaye
@HaleemaAllie
18 күн бұрын
You guys God bless you
@IsaacAmiyele-w6y
17 күн бұрын
Well done
@AliceChipeta-pc3nb
18 күн бұрын
Tidakali pa thawi yakulila chilima mzimu wao uuse mmutende SK 😢😢
@PatrickKennith
18 күн бұрын
Boma silomweli tizasankha September 2025.
@CHIFUNDOCHINA-lp9lg
17 күн бұрын
YES 👍👍
@user-nf3ik3ff6y
18 күн бұрын
Good message Jonathan
@ChifundoChibande
18 күн бұрын
A malawi we dont know what we have to know!!! Dzik ili amalamula nda zungu, try to understand mmen dziko limayender la malawi kt anth muziwauza zachilungam coz pal zinth zambir zomw simaziziwa zimen mmaziona ngat ndiza normal coz munakula muzimenez km am telling you this organisation called IMF sindimaiona bwin.. try looking from the bottom of our mavut kt muth kuzindikira.... Let me ask you, azungu amatipats ngongol even when tili ndingongol ina kal y?
Inu ndinu ma journalists tell Malawians the truth for once….This govt is borrowing too much because it’s under pressure to deliver on its unrealistic promises
Jesse watengetsa anayenera kusiyanitsa ntchito zaboma ndi chipani
@user-tl9xg4fg9x
17 күн бұрын
Azibambo inuyo mumaona patali ulemuwanu
@AdenaGuest-g4b
18 күн бұрын
Mofaya Banda
@PrinceBlessings-bv5bs
17 күн бұрын
Iyii idali mbambande
@maxwellluciano4943
18 күн бұрын
Kkk kwavuta
@user-nt3mz7bu5r
18 күн бұрын
Man in the middle is just a rumour monger and not an analyst. Let only analysts continue to participate, otherwise the program will loose its usual taste
Anyamata mwandiyakhulira bwino Maka apo akumati boma ndilomweli pa mwalasa, tipatsene ulemu di, ndinthu fukwa choza mawa sichidziwika asamale mayakhulidwe awo
@HaliJana
18 күн бұрын
Program ikukoma kobasi anthu inuyo mumakwana kobasi
@SteveChapola
18 күн бұрын
Amereka yanenazona agobandalama
@ernestphiri5507
18 күн бұрын
Otsogolerayo ndiye olephela
@user-un6qv6sj3h
18 күн бұрын
Tiyeni nazo ❤❤u guys
@AlinafeNafe-s8p
18 күн бұрын
Palibe choyamikila
@AubreyMwale-y7q
18 күн бұрын
Muze wa mcpyo
@user-wl4nd7ic1s
18 күн бұрын
😂😂😂😂❤❤❤
@giftmakoyo1441
18 күн бұрын
Hot current iyi ndiye inalidi hot hot😂
@khamakumasewera9283
18 күн бұрын
Mwasowa zokamba a Chafumuka. Ngati munthu akupanga chitukuko osayamikira ndi chiyani? Ena akumati bomali palibe la chita. Zitukuko zomwe akupanga a Chakwera 2:15 ena anawonongapp. Pena ena anangomanga za substandard. Analysis apo pokha yakuvutani bwana
@BizweckMbwindinga-uh6fq
18 күн бұрын
Program ikukoma kwabas bwana muzimangilitu pitani pa TV 📺 mukasuse
@user-un6qv6sj3h
18 күн бұрын
Kaoneleni MBC malume
@AlinafeNafe-s8p
18 күн бұрын
Aaaaaaaaaa chitokukocho akupangila kwanu
@fortunekamdumli-xy5zn
18 күн бұрын
Awanso nde achitsilu bwanji
@MosesMwachande
18 күн бұрын
Kape uyu akatero wadya nawo
@AshimayeGama
18 күн бұрын
Chilima analichi vhitsilu wachabe chabe galu opanda tchoto mavuto osewa chifukwa cha iyeyu
@user-hd7wq2yc6m
17 күн бұрын
Akabwira ndimunthu wopita ku school, koma ndi mbuli ya munthu akakadayenderabe zomwe zija za Kamuzu ngati chipani chimodzi,sasiyanitsa ntchito za chipani ndi ntchito za boma ndichifukwa chake akufunanso kutengera dzikolli konkuja ku one party system ndiye za a Jesse Kabwira mbuli yophunzira
Пікірлер: 64