Ndipo I wish ndikanaonera live awawa udindo wawo akufuna anthu aziwaopa osat kutumikira anthu ndipo ahhh.....😊
@KinziwindassoniKinzi
3 ай бұрын
Nzeru ilibe ndunayo ubwino wake 2025 mbava zikuchoka
@SharmamontenJafalisharma
2 ай бұрын
😢😢
@ancientnkhata1137
Ай бұрын
Mbamva zinachoka kale 2020
@kondwanimunthali7401
7 ай бұрын
Anduna palibe chanzeru chomwe akuyankhula.He is argumentative for nothing
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
Жыл бұрын
Kodi mlendo anali ndani pa Hot current imeneyi.... nduna yoonjedxera nkwiyo kwa A malawi
@AshraphChimenya
Ай бұрын
Zikhale Ng'oma ndimuthu wovuta eeeish
@JoshuaChizampeni
Ай бұрын
Ndipo uyuyu zikhaleyu NDi machine mafuso enawa NDi ambwerela
@JosephMoyo-k2h
2 ай бұрын
The fact is sikuyendabwino,
@BrianBanyilah-ig8dv
2 ай бұрын
Eeee km chinyam ichi chikuvut bwanj km akuziwa chilungamoto
@moseskavalo3304
Жыл бұрын
The nduna himself doesn't know how to argue,,too much emotions ķkkkkkkkkkk hahaha MCP is dangerous party indeed
@ChimwemweJuwao
2 ай бұрын
Muthu oipa ameneyo koma ndiwabwino pamaso
@JacksonMoyo-tm8dv
2 ай бұрын
Zinthu zadula koopsa nthawi iyi ya Mcp
@MuhamadiPetermuhamadi-j1j
2 ай бұрын
Kodi zikhareyi amayakhura chomchiiiii
@MichaelChisenga-n4h
2 ай бұрын
Ndiolotse ndi kakudye nde ameneyu
@JacklineNiwahereza-ni3pm
Ай бұрын
This guy is called zikhale alibe nzeluuu 😅😅😅
@confidencezunguya7552
Ай бұрын
Zikhale amatha kuyankha guys
@YohannyMangulama
2 ай бұрын
Amanjaila bulaan apa wakumana naxo
@SusanPhiri-el3dx
2 ай бұрын
The program is nice but talking too much not giving each other Chance 😮
@AlexHenere-r6l
Ай бұрын
Musiyen wakan
@DeenesNurudMeke
11 ай бұрын
The Big 5 imeneyo ikhare Njobvu kkk
@stevekamangaFrancis
Ай бұрын
Program yanu mudzimpatsa munthu mpata kuti alongosolele mfundo zache kwa Malawi am not saying this for the minister in particular. Program yanu imaoneka kuti mumamuitana munthu kuti mudziputsitsa, osati akuyankheni, Inu timakumverani dairy. Hot current, editors chani chani. Pankuku learn to manage time,
@mercythom5868
10 ай бұрын
Poyamba ndimaona ngat Times imadana ndi DPP koma now ,,,,,ndazindikira kut it's only times yomwe tingaipange trust❤❤❤❤❤
@ChikumbutsoButao-h1s
3 ай бұрын
Iwowo akanalongosora wokha zomwe akudziwazo
@JonathanBanda-w6f
Ай бұрын
Abanda andunawo asakane kuno ku phalombe tinapereka ndalama 30 pin mpana pano ndalamazo zinapotera tinaberedwa bas aaaa
@KennedyPhiri-h9h
2 ай бұрын
Zikhale Ngoma machende ako maphwala akonso munthu woipa iwe and muwona chaka cha mawa agalu inu
Ndunayi ikamayankhula idzidziwa kuti Ili pa tv komanso palibe wa dzelu kuposa nzake pa dziko pano ngati kunvana kukuvuta thesani program
@MotivatedI
Жыл бұрын
This is exactly how government lives in denial. Very interesting. All this time there is nothing you can point that the minister was able to answer. Like nothing
@Littlefair7
Жыл бұрын
He forgot we're in a democracy with his dictatorship mentality.
@JamesLongwe-qz9fd
2 ай бұрын
Feteleza kuchoka pa 17pin mpaka 114pin ndiye kuti tikupaseni mpata wina zitsiru za MCP
2025 ndi Chaka chamawa Why panic with this thing Let's go and work for our better
@bi8942
Жыл бұрын
A Brian tamubooleni mimbayo zikhale ng'oma mwina mimbayo iphwe kenako aziyankha . Ndichinduna cha mwano komanso Makati kwambiri. Changoseza mimba uko phwiiii kumapanga makani apa ngati ndi munthu ozindikira power ndi mbuzi ya munthu. Musazachiitanenso pa hot current kawiri , chizikhala ndi chakwera wakeyo kudikira kuchoka 2025. AIP ikuyenda bwino pakhomo pakwawo osati kwa amalawi anthu okuba Mulungu awalanga pompano anthu amenewa
@eliffagondewe8214
Жыл бұрын
Kkkkkkk
@gavinpillay1253
10 ай бұрын
Galu wammpha dzikodi silingalongosoke ili nduna yaza chitetezo ikuyikiraso kumbuyo mbwererazi
@Extratremendouszeus
3 ай бұрын
Chilbe nzeru chunkhumba chimenechi He uses his udindo wrongly
@BennettNjedza
2 ай бұрын
😂
@AndsonAcd-j6i
Ай бұрын
Mumatha 😂😂😂
@hardworkkayuza6353
2 ай бұрын
Sizoopsezana😂
@kamuchirwa8940
Жыл бұрын
The worst hot current, zikhale is too much into politics.
@innocentissah2636
Жыл бұрын
Nduna yoononga dziko kwambiri, katangale ali thoooo
@PeterThawi-jc7zl
Жыл бұрын
Guys let's gather here for comments😂🤣🤣🤣
@MaxwellBinauli
2 ай бұрын
Koma boma la mcp Linangotengana zidepete zokha zokha ,Zikhale ndimunthu oti kumamutchula nduna zoona chitsiru ngati chimenechi
@BrownNamondwe
Ай бұрын
Oyipa awa
@BrownNamondwe
Ай бұрын
Awina akaba
@VictoriaKumwenda-k6o
Жыл бұрын
Azikhale akukwana pa udfend
@stanleymatolabanda5460
Жыл бұрын
Useless cabinet minister who could not explain 🚮
@rasulrayman4517
Жыл бұрын
Increasing the AIP beneficiaries will mean increase in poverty on household. This initiative is pathetic n we can't do better. Smallholder farmers are failing to extend their farm sizes due to high level of dependence on AIP same way as we depend much on foreign Aid. Teach more farmers on how they can manufacture mbeya fertilizer and do some extensions to their farms..
This zikhale ng' oma has shown he is an intellectual....he can cite his sources...Brian Banda didn't come prepared...this time.i hope u do better next time around.this minister has killed the interview.
@lumbizayigadama-wd9ox
Жыл бұрын
No ndiwopoira
@louisbonongwe8537
Жыл бұрын
Aaaaaa awanso
@GiftZuze-ge1ne
Ай бұрын
Palibe chimene wayakhapo koma kuchigereza khani Malawi sitizaremarad
...I really wonder why the anchor seems to be touting this guy a if he has some extra-ordinary skills and talent. What does nyama zikulu-zikulu mean? Lets not get excited and worship the same people who are promoting poverty amongst us. And I think we are micro-managed by Rwanda and collecting kickbacks by hunting refugees that he still seeks to kill. Well, I look at it as the most stupid thing for us to be proud of having more AIP beneficiaries. Instead of graduating these subsistent costly farmers into viable and productive citizens….on the US ambassador, I have never seen an ambassador who enjoys strange diplomatic protocol. He even finds himself in locations eating mandasi with locals, now, if he enjoys that freedom, then it is not a problem if he decides to walk into a media house as a news source. After all, the Malawi economy is surviving on debts, loans and credits that he approves every week, perhaps every day…The problem in Malawi is lack of ambitious leadership. We, currently do not have anyone fit for the position he holds in this government apart from the female ministers.
Пікірлер: 593