Poor leadership from the beginning its scandal after scandal nothing is going well
@FrancisDominic-w1s
4 күн бұрын
Chisilu olo kuchitibura muntondo sichingasinthe chisilu ndi chisilu basi
@Lydia-t4b
9 сағат бұрын
Apatu ndiye mwaonesadi kuti ndinu independent Times proud of you Times TV
@shotsfired588
4 күн бұрын
MCP ndi MCP, yomweyo ya m’busa ikukana kuvotera kuti Israel isiye kupha a khristu ndi asilamu ku Palestine mmanja mwa ayuda odana ndi yesu, inalinso mbali ya boma la tsankho ku South Africa.
@ConradccjSokoSoko
4 күн бұрын
Zolalata zopanda fundo nthawzina. ATI miseu mtown ayi koma kumidzi
@user-ux3ed3ni1p
3 күн бұрын
We are our ancestor's dream. We can not stand for such criminality in our Nation. #CommissionOfInquiry #Democracy
@GodfreyMaliseya
2 күн бұрын
Munthu wosamva ngakhale mutamuyikila ma speaker 🔊 kuti amve sangamvebe 😅😂 chikangawa sanalowe u president kuti azawathandize anthu ai koma kupeza zofuna zake
@MadibaGonani
4 күн бұрын
No secret under the sun
@AbdulmalikAmanu
3 күн бұрын
Koma achakwera chaka chino ndiye munya manyi nditu musiona
@JafaliAkimu-ll1bf
4 күн бұрын
chakwera ndi mbuzi ya munthu mzimu alibe chilobote chabe
@user-ux3ed3ni1p
3 күн бұрын
Why must the wife of a leader of our nation have to beg to get justice in her own country.
@giftkanjuchi-qm8hf
4 күн бұрын
Bravooo guys. You are doing a great job. God bless you all
@OsmanOsher-sh6gp
4 күн бұрын
Ma facts mesa
@CharityChirwa-t1e
3 күн бұрын
Akutiseka kimaso katukule chifukwa choti amagonana ndi chikangawa asaneme likoma akufuna kutenga ndi chakwela pamozi ndimwawake Nik nde asatitole. Ulemuwanu makoswna inu pobwelesa khani zobisika poyela komaso musalole kuti mugulidwe chifukwa chiyembekezo cha amalawi pofuna kuziwa chilungamo namba 1 timavela ntanyiwa namba 2 timava kwainu nde plz osafoka osawopa
Kodit uthengau chakwera amauva koman ali ndivuto ,ndimuthu yemwe mulungu anamumana umuthu kapen kt chison,mm and ali ndi nduna zake zot samamuwuza zabwin
Awapha pajat zikolo likulamulidwa ndi athu akumidima
@Rose-wu5ef
3 күн бұрын
Fisiyooooooppppp chakwela
@kondwanivyalema9449
14 сағат бұрын
Chikangawa amangopitilako kukakongola ndalama pano zifika 20 tillion chizete cha u PRENSDENT sichizapezekaso muno mu ziko la pansi MBUZI ziyanthu zoyipa za MCP
@FLEACHERMsonthi
13 сағат бұрын
Kulibeso kupita kut akakumane ndi munthu kumuuza kut bwanji wapita kuchikangawa osatiuza mmene amkafunsilana ndi SKC anamuuza ndan WA boma
@DesmondTaulaye
4 күн бұрын
George kasakula asegula mmimba
@Martha-m6e
3 күн бұрын
Poor leadership iyaaa.
@CharityKaonga
3 күн бұрын
Makamaka chimwendo amazitenga ngati half mulungu but time will come and you shall see
@ussimasi2458
2 күн бұрын
Ndipo munthu akundinyasa ameneyu mmm
@alexsumani6823
4 күн бұрын
Azibambo inu ulemu wanu basi ,inu MUMATHA and Chauta azikutetezerani basi
@AgnessKalindo
3 күн бұрын
Palibe zoti apite akakumane ndi chikangawa face to face kuti akufuna chilungamo.
@robayami-xz2wg
4 күн бұрын
Udf ndi chipani chaku banja pamene MCP ndi chipani Cha dziko la Malawi. Boma ndilomweli .
Пікірлер: 54