DC you're the best of the best man 👨 chikangawa tsakuziwa kuyendedza dziko ndi mbudzi ya munthu uyu
@MasterBlack-r2n
7 күн бұрын
Kodi pa audio ndipati???? Nditukwanano kwinaku.😭😭😭😭😭😭 Amalawi tikuchisungilanji chimfitichi???????????? Chonde amalawi tiyeni tiime njiii ngat ma Kenyan pls pls pls my pipo 😭😭😭😭😭😭😭😭
@rashidadan2533
7 күн бұрын
Anthu ena akusapotabe chakwela , umakhala ufiti ? Kapena kupepela
@BeatriceSaulosi
7 күн бұрын
Ndikuona ngati zonse 😢
@AmoTiamo
7 күн бұрын
Kupepera kosakanikirana ndi ufiti nanga oganiza booo ndani angataye nthawi yache kunsapota chikangawa munthu okupha
@AlexKaunda-ny2eg
7 күн бұрын
Ng'ombe imakaona ng'ombe zinzake komaso Mai wafukoyo ndi hule lolimba mtima
@Kashon1987Chakhwantha-ed3wi
7 күн бұрын
A bon kalindo inu ndinu openga mukungosowa zochita km muli Ndi mkazi kunyumba kwanu ngati alipo amati adapeza amuna kunena inuyo koma nde kukwatiwa Ndi tikufelanji
@ElizabethKamiza
7 күн бұрын
This is true bon kalindo athu akufa ndinjala in ntaja
@EmeriaSaliwa
7 күн бұрын
Eeeee kuno sizilibwinodi mñh 😢😢😢😢
@ChrisyMbewe
6 күн бұрын
Kalindo.azikudalisa.mulungu.akupase.moyo.wautari
@user-wx1jt5fd2j
7 күн бұрын
Bushiri yo zosatira zake simukuzionaa mumangobakira zili zonse thandizo lomwe akupempha anthulo ndi lawo la amalawi kuzera mu misonkho yawo zimene zikungoonongedwazi simuzionaa
@EmeriaSaliwa
7 күн бұрын
Eeeee kumachinga kuno nde zanyanya abale iiii😢😢😢😢😭😭
@doreenkaliati3166
7 күн бұрын
Ulemu wa A DC mwana woopsa kwambiri ❤❤❤❤❤
@cassimyusuf6683
7 күн бұрын
Zowona president kuyenda koseko ndithu kukawona ng'ombe, komaso ng'ombe zake zosakhala za boma. Koma amalawi ena osusuka mpaka kumasapotaso galu ameneyu
@OmarManjawira-up3ns
6 күн бұрын
Ine nde ndilibe naye mawu chakwera it pains kwambiri ndikamamva zomwe zuchitika kuMachinga 😢 Chakwera what kind of president are you,,,,? Look how our people suffer in RSA
@AngozoMalunga
7 күн бұрын
Mbambande
@GiftJulius-ro9ev
6 күн бұрын
Chakwela 2030 .....
@AmoTiamo
7 күн бұрын
Tisachedwepo apa awa usogoleri mulibemo ndi 0 pa 10 mutu mwa chichakwera mulube kalikonse mutu wangozaza mamina
asiyeni azifa ndinjala chifukwa aphawi ake ndiomwewa akuzaza misonkhano ya mcp makape aja ndikumayankhula mwamatama chifukwa choti anakanjalawo amakhala ali kumeneko akamabwelera kumakadya chiteze ndi nyika
@mtisungebonomali2004
7 күн бұрын
P on X gym
@PempheroAlli-v8y
7 күн бұрын
bushiri akufuna magazi sikuziwa ndikapeni imeneyo ya mcp cholinga azingotiphabe Dpp ilowa onse ali madzi kaya nde athawiranso kuti abusa anuwo
@ZakeyoChilambo
7 күн бұрын
Wathu wakulya khunga nadi pasono mmmmmm ma guyz khalani serious pliz so kuti tizafike February kuwengechi ?
@FaysonChimbalanga
7 күн бұрын
Makape sanje yokhayokha basi munyanayo chakwela akuwinanso
@HarlodLemwe
7 күн бұрын
Kod iwe bon kalindo nde iweo ngat ndiwe president wa anthu osauka nde osanthandizako bwanji ngat mmene amachitira bushri?umangolankhula chosecho ulibe kalikose pumbwa iwe
@LimbaniNyika
7 күн бұрын
iwe ndiwe wa mcp eti?
@InnocentKhembo-o4k
7 күн бұрын
Inesotu ameneyi ndimadabwa Nate, akuti president was anthu osauka koma osachitapo kanthu kumangolongolora akuti atchuke zaziii
@bridgetmajor3646
7 күн бұрын
Inu ndi Achikagawa eti...zinthu mene zikuyendela....simukuona eeeish
@HarlodLemwe
7 күн бұрын
Ine siwandale akulu vuto lamalawi munazolowela chili chonse munthu azikuthandizani kazigwilani ntchito ndi manja anu osati muzidalira boma zikuvutani ine ndimalima kudimba zimandithekela bho bho koma poyamba ndimkaona ngat ndikuvutika pano zanga zili pabwino sindinalira boma kapena nyau iyi ikut ndi president wa anthu osauka zopusa kungofuna kutpusisa apa
@MzadziWanga
7 күн бұрын
@@HarlodLemwemuziganiza kae musanalankhule zopusazo, ku Malawi aliyese ndi olimbikira fertilizer anali otsika mtengo anthu ankagula mkumadzilimira pano fertilizer mpak 100 thousand! Ndiangati angakwanise ngt akulepera kugula basin la chimanga, kukasiya anthu akulandira ma millions chakwera akungoenda zoduka mutu kuononga misonkho ya amalawi instead of kugulak chimanga mkuik mmadimak kt mwina anthu azigulak motchipa kma ai nde ukubwera apa kumalankhula ngt mutu wakhalira kt anthu anazolowera zolandira pomwe mukuwazuzira Dala anthu kt azikupembedzan
@captainmdima1102
7 күн бұрын
Inu za njala anayankhula kt chimanga chikubwela kma boma ndi lomweri 2025 !
@AshrafShadid
7 күн бұрын
Agalu pa midia inu faseck😅
@MzadziWanga
7 күн бұрын
Boma ndilomwedi tingosintha chipani ndi president chikangawa akapitilize kuchipiku mkomwe azikaphera anthu
@AmoTiamo
7 күн бұрын
Tisachedwepo apa awa usogoleri mulibemo ndi 0 pa 10 mutu mwa chichakwera mulube kalikonse mutu wangozaza mamina
Пікірлер: 45