Even the MEC chair herself knows that things are not going fine but seems like she is just there as the name, the salary and allowances only.She is just doing and even said what she always told but in her head knows the truth. My God be with our Country, Amen
Afotokoze zoona aNRB akapanga zibwana 2025 atiziwa kuti ife sitifuna zibwana tiliononga ndi zipolowe ife si Ana am a 1940 ife ndi a ma 2000 aphunzira mcp sitikuyifuna yatizunza pakwana.
@MillieMalakam
13 сағат бұрын
Inu kupoto ndikubwela kulibe athu ochuluka ndikubwela ndiye sitheka bwanj kuchuluka athu ku central ndikupoto 2m kumwela 8k koma mcp anjaila kwambili amec agulidwa ndj nrb agulidwa ndi mcp uyuyu wameyu wagulidwaso koma mcp isalowe boma mulungu yankhani pembezelo langa
@HaroonMKWANDA-r4x
7 сағат бұрын
NRB chilungamo chikukuvutani ma guy 2018-2020 MEC and NRB amagwilira ntchito limodzi and applications form ija ya NRB sticker ija imatuluka pompo pompo 😅
@peterchikwakwa8476
18 сағат бұрын
Kikikikik koma Brian amaziwa kutsila mchere😂😂😂😂
@Kamwachale
3 сағат бұрын
Where are the ID cards printed. Zokondera ndizaona, umboni ndili nawo Ndithu. Amaweruka 3 okoloko and I even called one of the Officer and all the people that came after 3 o'clock were referred to the district NRB head office
@faroukmejah.9169
13 сағат бұрын
Chifukwa chani ku Lilongwe analebesa ambiri more than ma boma ena even osakwana one million ma ndela ena
@justinmalala-e4o
12 сағат бұрын
Nkhani ndiyoti winaaliyense akalembetse mu kaundula wa chisankho basi. Nkhani ndiyoti umboni ulionse ukagwile ntchito, ngakhake chikalata chakwamfumu .
@elijahkasawala9122
6 сағат бұрын
DPP yaluza tisanavote😂😂😂😂
@RestarUmi
12 сағат бұрын
Zisiluzi zaonjeza kongoelekeza kubela nde aliyese azipanga zake Malawi muno
@geoffreykankhomba
13 сағат бұрын
In time of DPP mec and NRB were working hand in hand polembetsa chovotera opanda ID amapita kukalembetsa awa akufuna atisokoneze
BT anthu osakwana even 1 mita eti koma LL ndiye mpaka kuthamangira 2 mita eeeeeee kuli zinthu eti !!!!
@JulietMunthali-g9b
16 сағат бұрын
I don't understand why Lilongwe mean ku BT anthu aliko omwewo basi kkkkkkkkk ayi sizoona ndekutu the hole Malawi anthu ambili amakhala ku Lilongwe zaboza iziiiiiiiii inu mwatani bravo times ❤❤❤❤❤
@elijahkasawala9122
6 сағат бұрын
Akuphatikizatu ndi a 2020 aja
@allieadam3235
17 сағат бұрын
Guys mumatiyimirira ndithu, Tili ku Pretoria koma timadzitsata through Times
@TrezzarSmart
17 сағат бұрын
Iwe wa N R B bwanji kusalima sunabwele kuzalembetsa komaso tikalimbetsa sakumatuluka mukumawasiya kut inuyo
@RobertLuka-wy9cl
14 сағат бұрын
Agwirizana basi ndi boma kuti abele
@SamuelKaphwit
8 сағат бұрын
Kumalawi munthu akawina u president amarephela kuyamba kupanga chitukuko amayamba kupanga ukampen mwalo momanga chitukuko saulosi chilima adalakwa chani inu achakwela kupanda saulosi chilima mukanawina inu relo mukurephela kufotokodza mkhani ya ndege why
@saidimwanyali8969
16 сағат бұрын
Kulilongwe ndikumene ali anthu ochuluka papenepo
@FloraMakoka-r9i
17 сағат бұрын
DPP ndi yakuba Jane assah komanso jean mathanga onsewa ndi a DPP panopa onsewa Ali ndi ma udindo kuchipaniko
Пікірлер: 37