You guys you are number one olo wina atapanga nanu ndale koma know this that you are talking for malawians
@JimmyMaster-l1x
9 күн бұрын
Gayz tikukonda TTV chifukwa mukulankhura chilungamo God bless you Mr Banda Mr pa mkuku Mr Zamwayii Tikufuna times ukhaleso pa Number one 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@GodfreyMurambiwaZhuwaki
9 күн бұрын
I like your tchutchu, Pali zabwino nenani and Pali zoipa nenani.... bravo
@hamiltonsolomon3756
9 күн бұрын
Love you More Guys....Kwayine ndimamva kukoma ndikamamvera inu.....More Fire ❤❤❤❤
@user-pv9uk6sc3w
9 күн бұрын
George Kasakula akukuwonani, ndipo sakusangalala nanu. Pitilizani akulu akulu kulankhula zoona kwa a Malawi.
@GospelSoldiers-sr7np
9 күн бұрын
Ndipo Ambuye azikudalitsani kwambili, George kasakula aziboweka zenizeni.
@sulleahmnyimbili1362
9 күн бұрын
Ndipo a kasakula azaziwona
@eliffagondewe8214
9 күн бұрын
Koma nde Ali mmadzi kasakula kumachita kukhotetsa chilungamo akuchiwona kkkkk
@user-gq4gl7fn3x
8 күн бұрын
God is using you guys to be our speakers you really went to school of journalism,,,,,, fear is the best enemy continue opening People's eyes and let them realize what is wrong/right may God cover you under His wings.
@mathewsnachuma8086
9 күн бұрын
Convid19 idayambila ku China koma ku malawi mmene tikupangila ngati idayambila konko Ukraine war lero akupereka chimanga a Ukraine omweo Anthu awawa alephera
@HakikaWiskes-yb6zq
9 күн бұрын
Musanafike poulula ndiyambe ine ndingotchura mmodzi yekha George Kasakula sakuonelani kukondwa
@ussimasi2458
9 күн бұрын
ndipo zoonadi
@AfickMustaffa
9 күн бұрын
Nkhaniyo ndiyoona
@ALLANNDALEZA
8 күн бұрын
Ndilibe loya😂😂
@TecksonKaima-dr6er
9 күн бұрын
Zi afiti as mcp zimenezo.osadandaula mulungu Ali nanu oasaopa komanso fire😎😎
@user-pk6vq1cr1b
9 күн бұрын
Guys you are the best ever in Malawi keep it up and more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@eliaskhofielias8152
9 күн бұрын
Guys you 3 your doing the great job in MALAWI.pitilizani osaopa musaope zoopsezedwazo mumayankhula chilungamo and you stands for malawian.mavuto amalawimuno mukuwaona komanso mukuwadziwa.your the best once again limbikisanani mitima okuopsezaniyo muyaluseni.kasakula akuluopani akudziwa ntchere wake ukutha next year.do your job for the benefit of malawians.keep it up all of you.may God keep protect you guys.
@user-pv9uk6sc3w
9 күн бұрын
Ndipo mwamutha George Kasakula, adasintha lero , kaya akufuna unduna kwa a Chakwera kaya!
@lysonmisanjo7316
9 күн бұрын
Brian akasowa pa radio ndi pa tv mtima wanga umawawa
@SamsonLevison
9 күн бұрын
Keep it up guy's osaoopa munthu Chilungamo chimapweteka ndithu akunva pain amenewo
@WillmotChiuimia-vr6ou
7 күн бұрын
Apa pokha ndiye mwayankhula zenizeni❤❤❤❤ we love you guys
@ussimasi2458
9 күн бұрын
ndemuve mwayakhulazi ku mbc 😂😂😂mawa izi mwayakhulazi kasakula ndi azache abwetuke kkkk
@ZivanaiGwatura
7 күн бұрын
Chawezi waluza talent akuona ngati ife taiwala
@johnsoldier
9 күн бұрын
Iweyo wander ukafuna kunyapula suyang’ana khope more fire gyz
@VascoMsowoya
9 күн бұрын
Koma times ,u are number one palibenso .
@georgesmart3791
8 күн бұрын
Powerful kwagwanji ❤❤❤
@GiftJossam-if2gt
9 күн бұрын
U guyz ur doing great job!!! Kip going
@hastingsbalaleya
9 күн бұрын
Athu anenepa ndi mutu womwe that's why akudana ndi Hot current Koma ife tikuwadziwa amakhala pompa pano alikuti? Keep up Guys- ponyani Bomba ku radio Malawiko
@AshraffZuliyani
7 күн бұрын
Good mushisha wa boowola paliwombo
@FranciscoJendala
9 күн бұрын
mwam, modzi amene analandila chi Bazi ndi joji kasakula , anakhutitsa mimbayake
@JustinChiwale
9 күн бұрын
Ndiye mwat kubwitaaa😂😂😂😂😂😂😂I like that chichewa akumbwita ndithu kut mbwituuuu
@charlesmbale7739
9 күн бұрын
I have a good reason why I watch ttv more than any other TV station in the country.... Mumakwana ...
Best radio in Malawi with good presenters keep it up
@SteveTigu
9 күн бұрын
You guys your the best mulibe Mbali osati enawa am radio enawa but sitiwatchula
@masterkachingwe7448
9 күн бұрын
Kasakula ndiazinzake akukamba mbweleraa
@charleshenderson70
9 күн бұрын
Zodiac
@FrankFrancis-ch3xv
9 күн бұрын
Ilike you guys,u always on truth when it comes to analysing Malawi politics,bravol you all,osati nkhalamba Zakuwailesi yaboma,they always brings nothing on their program but rather opposing against times that's how you the best TV in Malawi
@sulleahmnyimbili1362
9 күн бұрын
Very true Mlungu akafuna kumasula anthu ake samva kapena kuwona za munthu 🙏🙏
@TEC-SOOTHING
5 күн бұрын
Talking the truth... You are doing good
@meganabigail-ye7fw
6 күн бұрын
They are really mbwitings my Darling 😂😂😂😂😂😂
@NickeshNdagama
9 күн бұрын
This is great fact stories and true conversation
@GanizaniKamvazaana
7 күн бұрын
Siboma iri athu akudya chitedze adzipita adya Ena adzatidyereso basi Koma ife Bola tidzameze nsima😢😢
@AshraffZuliyani
7 күн бұрын
Wander mbwere mudzatenge thumba la punga zulian ku kk Kaka
Kuba akuba pamwamba pakeso akutitsowetsaso mutendere koma anthuwa
@leonardmalirana7423
9 күн бұрын
Kusintha mbava kubweraso mbava zina eeee ndichifukwa chake enawo sanafufuze milandu yakuba ya anzawowa poganizira kuti nawoso aziba
@AfickMustaffa
9 күн бұрын
Osaopa, osatopa osafooka keep the fire burning
@DjshukulanGift
9 күн бұрын
Pali chisilu chinachache amat kasakula mm asamare,amalawi siife opusa
@frezarphiri3480
9 күн бұрын
😂😂😂😂😂 brain banda ndawona zithu ine hahahahaha lero Joji kasakula lilime lake latembenuka akutamanda Mr chikangawa ever single day galu ija amavuta pano pa hot kalet kutukwana APM ndi dausi koma lero ayi ndithu
@chcmzuzudiocese5916
3 күн бұрын
Brian Amayenda olakwalakwa
@Christina-mo4qu
9 күн бұрын
More fire guys keep it up
@WestonMsani
8 күн бұрын
😂😂😂😂 Tikungositha mbava,,,,mbuli ndife timavota ndumbwani nalo dziko ndi lanu
@AllanMagombo-j1k
8 күн бұрын
Brani band uli ndivuto
@rashidphillip2506
9 күн бұрын
Pakhale lamuro kuti boma likapanda kuchita bwino in 2 years azitula pasi udindo
@MikeMwale-bw1xw
9 күн бұрын
Ku Malawi kuno kukonza malamulo okunza zinthu ikuvuta koma chilamulo chopondleza mphawi.
@DjshukulanGift
9 күн бұрын
Ndipo ine Malawi okhuzidwa ,timakusatan bwin bwin ,oti azadye ndalama tizamuziwa and pali tolakhan wina wake Ali Ku Radio 1 mm ndikape and sitizamusekerera .....akubereka satan kumbuyo
@IshmaelJames-qp2pr
9 күн бұрын
Mbali ya ine ndimadandaula Malawi sachedwa kuiwala kungopasidwa 500 wayiwala mavuto omwe akhala akukumana nawo tiganize bwino 2025 Malawi
@user-zq3uf5bc8v
8 күн бұрын
Don't give up brian and your boss we learn more and our go goes to that one ❤
@user-vg3os8xx5t
9 күн бұрын
Won't you make Brian like chiwanda adzipezeka in any problems because he's capable to say the voice that everyone is scared to say believe me
@MarkKaulembekampaliro95
9 күн бұрын
Corrupt brian who worked for Chakwera??
@user-zs3ty9dy1d
9 күн бұрын
This is the kind of programs we need,bravo to the presenters,nawo ati ku MBC ayamba program yawo,koma so pathetic,kupsyetsa mtima! Kuyankhula ngati achina Kasakulawo sakhala ku malawi konkuno.. Selfish motives,ati kufuna kusangalatsa mabwana! Mpaka a Mvula pakulira Iwo paja kumapanga nawo zopepelazo! Ndalama ndi satanaadi.
@MiracleMalichi
9 күн бұрын
Abrain Banda chonde mwachoka nao kutali utola nkhani wanu chonde musstengeke ngati akasakula ndalama inapha yesu
@BlessingsMbawa
9 күн бұрын
Osaopa ma guy kunena chilungamo pakana olepherayo ayaluke ndithu
@andersontembenu7054
8 күн бұрын
I need to know how we can write MBWITINGS in correct way 😂😂😂😂❤❤❤ I love you guys
@josephmanyenje7107
9 күн бұрын
Times ndi radio yoimadi pachilungamo, Kunali ZBS lero aonesa kuti amangodana ndi former regime lero kuli ziiii chibanzi chawaseka kukamwa Akati ayankhule amangoyezeka lero zikachitika tikumvela kwainu a Brain ndamzanuwo
@EmmanuellKajawa
9 күн бұрын
Lero mwayakitsa moto guys
@GeorgeNkhata-x1o
9 күн бұрын
Kumangotola chilichose😂😂😂
@charlesmbale7739
9 күн бұрын
Ali ku times amakamba zina ..... pano wafika ku MBC akulankhura dzina ..... Khaaaa Khaaaa
@ProspaDMitummba
6 күн бұрын
We ❤ you guys
@SamuteSamute
9 күн бұрын
Congrats gentlemen for ur conversation honest pains keep it up
@ChancyNgona
6 күн бұрын
Brian banda was also quiet when he joined state house,,,
@ChikondiBanda-ce8tk
9 күн бұрын
The change we r looking for in a desperate way. Being desperate for change creates wrong decisions. If now we think DPP is the party to change things is a desperation which will not help us as a country. MCP has failed, Chakwera has failed but I strongly believe DPP is not an answer.
@Nylon_
9 күн бұрын
Neither is MCP
@WilsonMagongwa
6 күн бұрын
Akuoneka zoona B waonadi zinthu
@raymondchilimba7010
9 күн бұрын
Guys muzikhalako serious pa TV, mukamakambilana kwa nthawi yayitali muzikhalako ndi madzi pa front okumwa Komaso imakhalangati decoration. Be creative! Mwatani Kodi....
@PatrickMangochi
9 күн бұрын
Palibe wabwino apa,Brian banda waba ndalama za Malawi osauka 100 plus million posachedwapa knowingly that he misbehave at state house
@EddieMlenga
9 күн бұрын
Especially malonjezo amene timalonjezedwa ngati pangano kodi theka lazimenezi takwanilitsa? Chotilankhulira ndinu guys keep it up! Ndinu mbambande machine.
@DavidPhiri-o6w
9 күн бұрын
Changing mbava 😂😂😂number one mwayankhula wakuba wava mbava Malawiian government since multiparity
@eliffagondewe8214
9 күн бұрын
Well spoken guys ♥️♥️auzeni basi adzimva zoopsezana ayi..
@PraiseMasina
9 күн бұрын
Inuyo mumakwana bcz mumanena mosakondera mbali keep it up gyz
@GraceChenda-q2g
9 күн бұрын
The mbwitest gv ever
@MphatsoMhoney-xn2ft
9 күн бұрын
Mr ndeve zamwayi inu ndi shasha ndipo every program mukumabwera mwa Moto we need people like you guys ..... Kodi MBC ili kumalawi konko or inasamukako there programs are boring full of nonsense with those madara
Chisanzo liport yandege,m,mene munathanthauzira Bora agwedegwede
@PrinceBlessings-bv5bs
9 күн бұрын
Nenani zilungamozo iwoso atopa kuzukuta nkhani zanu m'malo mokamba zawo 😂😂😂😂. Madolo a ku kanema wa.......
@geraldtuwaga-iz6ll
9 күн бұрын
Nyansi saphimba, enough is enough,
@VictoriaSibande
9 күн бұрын
PP INE IMANDINYASA KWAMBIRI
@JohnChipololpolo
9 күн бұрын
Inuyo ayii mumakwana and mumangobwela ndichilungamo poyela bas 😅😅😅
@JohnsonMaulana
9 күн бұрын
A'm here by mistake but ndaikonda program yanu madolo❤
@AshraffZuliyani
7 күн бұрын
Awanda mutembenura Wezi
@Blessingskazembe-s1r
7 күн бұрын
Akulu akuseli aja anadya chibanzi achitsilu kwabas
@latkecepatrick3019
9 күн бұрын
Ingonenani kuti nkhani nja George Kasakula. He was good while at Times, now he’s talking some BS at MBC cuz he’s under gvt. Money is the root of all evil.
@yassinn5634
9 күн бұрын
Brian Banda amayesa kuti a ndebvu azingovomereza ziri zonse wanena koma zina akumamu crusher ngati mmene wachitira ya Ukraine.
@DigleDafter
9 күн бұрын
Inuyo simungafane ndizisilu zapa MBC zinja 😂
@NicolasKamunga-rv9vr
7 күн бұрын
Komadi bwiting'insidi mcp😂😂😂😂😂
@LeyvanSamuel-pe5tc
9 күн бұрын
Madolo awa amang'alura koma mozimbayisa😅 keep it up guys
Пікірлер: 240