Stay safe comrade. May the God in heaven keep u safe my brother.u the only source of true information to us.
@user-kr4wb2th9i
27 күн бұрын
❤❤❤❤more fire 🔥🔥🔥 ndipo titemana serious muno oky mungoti pheee anthu amenewa asazayerekeze kubwera kumangochi serious azaona ngati akufuna kuti azalembe book la history lomkuzana anthu akumangochi 2024 yelekezani kubwera kuno , zimunezo kulilongwe komweko kwa anthu aganiza mwauchitsiluwo try to come here in Mangochi try
@Hudhayf
27 күн бұрын
😂😂😂😂 Mangochi m'bomamo
@augustMag
27 күн бұрын
Tili pano kudikira Chilungamo chioneke ndi Limpopo FM radio 🔥♥️
@sulleahmnyimbili1362
24 күн бұрын
Thanks alot comrade, May God protect u so that a Malawi tipitilize kuziwa zoona zenizeni
@user-rg4du4vu9r
27 күн бұрын
Kunena zowona paziko rapansi pano paribe chinsinsi sure nyimbo ikhare ya grace chinga ndizaurura tchimo rimazunza orichita sure 🥱🙆
Munthu akuyankhula za achewayu wangoonetseratu umbuli waku wonse kuti za democracy sazidziwa. Democracy imabwera ndi ma condition ake. Boma lingapereke ku ma company angati ndi ufulu wa pa malonda omwe ulipowu? Muli ma company angati m'Malawi muno kuti boma lingakwanitse kuperekako ndalama? Taganizirani za fetereza wotsika mtengo momwe zikuyendera, akupindula ndi amphawi kapena anthu andalama? Zomwe zikuchitika ndi fetereza ndi zomwe zikhoza kuchitikanso ndi sopo kaya ndi sugar kaya ndi mafuta ophikira. Omwe ali ndi ndalama zambiri akhoza kumakangozikokololako zonse nkumagulitsa ku amphawiwo modulabe.
@LazaroSinerioSineiro
25 күн бұрын
Mcp omse ndi amagazi manja agalu Eni Eni mbuzi za wanthu
@KeltonKapanda
19 күн бұрын
May God keep you safe comred
@francismlilima
25 күн бұрын
Koma mukuchulikitsa gagadiwa...go straight to the points
@samchibenene4458
26 күн бұрын
Mo fire Limpopo FM
@YatoRoy-kt4lh
27 күн бұрын
2025 they will be no votes. Dziko lonse lapansi kukhala Climate Lockdown(NWO) mufufuze zimenezi
Bwanji ya nzungu wamathanyula sunafune kuti tiyikepo maganidzo
@IssacMateyo
27 күн бұрын
Sangave samadikila kuti amuuzeko ena kkkk
@Musa1828-l5d
25 күн бұрын
Ife tupanga kaye za ifa ya Malawi nzathu, akanakhala Chakwera wafa ifa yotere ifeso sitikanakhala chete tikanafuna chilungamo chioneke
@Sirmax-p3e
3 күн бұрын
Keep on
@partmaulidiPatrick
27 күн бұрын
Adahinuyo makwana
@user-pj9rs6vj8x
27 күн бұрын
Iwe osatulutsa lako lowonalo bwanji?hahaha mabodza awa
@ChipiliroLungu
4 күн бұрын
Ase some you talk truth ,koma zina zikuoneka kt mmmmm ndizonama ngati kuli chaka chimene alimi asangalala ndi fodya nde ndi chinochi ase zafodya usafinamize mwina zinazotu
@languitoneelias9972
26 күн бұрын
Its better kumakamba zinthu ndi umboni coz pamawa uzayankha brother
We are very angry we want to given us good information,we are not joking, Chakwera,Chakwera, Becareful., you will flee and Leave Malawi One Day,zida wagula zija ndi zathu tizazi tenga zonse tiku ziwa Chakwera Ufa ngati Nazombe Malawi uyu ndiwa sopano Siwa Kale munapha uja Chirima ndiye Anali bwana wanu,siku limodzi ma ofesi a MCP aza pshya tsiku ndi limodzi Osati Ndi chipani,Gulu la anyamata liku konzeka wenatu Alípo secret soldiers Malawi an there's is outside, Asirikari mukama gwiri sidwa ntchito Ndi MCP zizakuvutani yang'anirani Amalawi,Os militar não tenho partido, tem dereito para defender população ouviu Malawiano Malawiano não pode deixar Chakwera para vingar cidadão malawiano quidado Chakwera
@GeorgePhiri-ub2of
27 күн бұрын
Lelo akuluwa zolakhula khalangati zasowa
@KennethChagunda-gn8kg
26 күн бұрын
Ndiwa bodza inu munthu uyu. Kd iyeyu akudziwa bwanji zonsezi munthu ali ku SA??
Kagwedwe ka ndege tilibenazo ntchito , kubedwa kwa black box yamu ndege izo tilibenazo ntchito , Mufunilanji umboni wina chonsecho tikudziwa kuti chakwela ndi nduna zake ndizomwe zinapanga plani yogwetsa ndege yomwe inapha anthu 9 kuphatikizamo V'P Claus chilima .
Пікірлер: 146