KOMASO ANTANYIWA TIKUUZENI MUKANGOMVA KUTI WINA WAKE AKUBWERA KUNO KU SOUTH AFRICA NDI ZOLINGA ZAUPANDU TIDZIWITSENI, AMENEYO SADZABWERETANSO KU MALAWI, NDIPO UKANANENA KUTI ZIKHALE ALI KUNO, AMENEYO AKAMAPITA ALI MBOLOSI ASATIZOLOWERE
Nkhani ya zoona ngati abwela achilima koma ayi Zikomo kwambiri ambuye
@ThivadoartistDyson
3 ай бұрын
Takoza kale ka team kuno ku juberg kamene kakufufuza kut anthu amene abwela kudzapanga chipongwe Limpopo komanso Bakili tv asabwelele ndi moyo.Akamabwela kuno Azitsazika akwawo onse komanso azikozekanso za siwa ⚒🗡
@JohnAsendi
3 ай бұрын
Akadafusa Kaye anthu adauzidwa kuti tizawateteza antanyiwa ndi Abakili m TV angoononga mitsonkho yathu makape ndiposimudzamupeza 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@IssahAluba
3 ай бұрын
MCP is apdete yatha bas chilugamo
@AubreyMatress
3 ай бұрын
May God protect you Comrade Ntanyiwa, tili komweko pa 10
@GidionLufani
3 ай бұрын
Mcp yapha athu ofunikila ambili kumalawi
@zaitwazaitwa941
3 ай бұрын
Mumakwana Mr Limpopo
@mathewsmakina7845
3 ай бұрын
Ifetilinganga ndi ntanyiwa pa limpompo FM
@ShiraKasekaNyirenda
3 ай бұрын
Ambuye apitilidze kukutetedzani
@SamNkhomo
3 ай бұрын
😢😢😢
@rachidepitamuhamedmuhame-jg9id
3 ай бұрын
Osaopa osafooka
@EyobeAyala
3 ай бұрын
Tionana pa 10 😢😢😢
@EsnarthSulumba
3 ай бұрын
Kumbuyo kwanu😭😭😭😭😭😭
@isaacedsonmabulesi
3 ай бұрын
tikalira mn pa 10
@johnsmamu7590
3 ай бұрын
Iwe ndiwe chisili kwambili, wadyadi chibamsi choka apa, ndimau amenewo anthu Atha kukuonongatu iwe
Пікірлер: 51