Dj don't trust iwedi ndipangolini😂😂😂😂😂😂 l,m proud of you
@AmosSamson-q8m
Ай бұрын
Boma lamamafiya wokhawokha iyi
@MoyendaMoyenda-dz8wu
Ай бұрын
Ndipo live mr don't trust ❤❤❤❤
@IshumaerWazakile-u5d
Ай бұрын
amwene mundipepheleko kwa vice president kt andipaseko chisot ndi make ndizipanga masewelo
@MustafaAbdullah-pb5zv
Ай бұрын
More Liiiiiiiiiiiiimpopo
@user-be5fc3ed1i
Ай бұрын
Don't trust please timakunyadirani koma pankhani yanyimbo mzitiyikira zabwino zomwe amakonda kubwera nazo ntanyiwa .ineyo Limpopo FM imandiwaza akandiyikira nyimbo ya Kain Kodi achilima alikuti?😂😂😂
@MrThomas-j9d
Ай бұрын
Port Erazabeth in kostern we are good Peter Thomas sauth Africa
@BenardPeter-pd5mh
Ай бұрын
Hamayo ine tamia uja
@user-cy4pg1bo5o
Ай бұрын
Wooo zaaa kkkk ukunvek
@Kelvin-hj5qv
Ай бұрын
Km Adah awawa amandiwaza kwambilit 😂😂 ukali wawo km
@ChimwemweGwape
Ай бұрын
Mbuzizo ndi mmene ife amalawi tikuchitira mkana akuti amalawi tili ngati mbuzi sitichedwa kuiwala
@ephraimphalawala4720
Ай бұрын
Kkkkkk koma Don't Trust...Mayi wa mitala ya Azimbambo. Vera Kamtukule kkkkk
@ZaccheousPetrol
Ай бұрын
pano atumiza aku Embassy mu ma churches kuno ku South Africa kuti aliyese alembetse amene anabwela kuno ndi pasport.....date line pa 7 September....aliyese akhale atalembetsa ....Johannesburg,cape Town, Petersburg ,petermalisburg...
@wilfredkazembe676
Ай бұрын
Kuno big " Mr don't trust " pa Durban pali mushe yipondeni fadah ndikumvani 😂😂 more!! fire 🔥 mungondiwuzilako a " MCP " tili ku excile tikumana 2025 buuuu!!!
Mukamati mbuzi including your parents? Chifukwa nawonso ndi amalawi bro kumayankhula bwino you don't call peoples kuti ni mbuzi tizasiya kukupanga follow
@JafaliAkimu-ll1bf
Ай бұрын
boma la zigawenga ili mbava zitsiru zokha zokha izi
@medisonkoroma9844
Ай бұрын
Umatha Aise
@JafaliAkimu-ll1bf
Ай бұрын
boma la zigawenga ili
@user-ky4ce9gb6j
Ай бұрын
MBAMBANDE
@user-ql8nf2vb8s
Ай бұрын
Akamuna bambo
@zimmekapachika6784
Ай бұрын
Atamia 😅😅😅😅
@KunyengaMoyo
Ай бұрын
Tili pa following
@user-uy8uk7so9d
Ай бұрын
Kkkkk umakwana
@user-zv3cy2xj5p
Ай бұрын
Udzigwira ntchito pa weka osamadalira boma pachili chonse
Пікірлер: 65