Ndiye tizingokhalila kuphana dziko likubwelela kwa kamuzu ili mmmm
@Henry-vw2cz
22 күн бұрын
Chakwela anapha chilima
@priscillamangata4023
22 күн бұрын
Kuchikangawa
@AchalumeSan
21 күн бұрын
Mayo Malawi wutu 😭
@AmosBandula-up4yb
22 күн бұрын
❤
@PetroJack
22 күн бұрын
Boma ladzitsilu ili lagwa basi
@KunyengaMoyo
22 күн бұрын
We're ready tiyeni pamseu
@JaneChimasula
22 күн бұрын
A Malawi maso athu ayang'ane kwa mulungu basi chifukwa die amene azatimenyera nkhondo tili chete 😢
@MandalaChaona
22 күн бұрын
😂😂😂😂😂 President wa Achewa koma zamanyazitu izi Mr Chikangawa Lazarus
@MandalaChaona
22 күн бұрын
Koma Mr Lazarus Chikangawa mwaonjeza,muphe anthu onsewo muwaphe akulakwirani Chani, kukana kudzudzulidwa pa kupha anthu 9 eeeeee Koma ndinu Mulungu wachiwiri,mwafikapo 🔨⚒️⛏️
@user-oc9vl9xz8e
21 күн бұрын
Koma kaliyati ndi mzimayi osagwedezeka sangapange zopusazo kulandila ndalama ku MCP..ngati ndalamazo mai angakupaseni landilani after nguzangolengeza kuti mwatukuka my ngwilizanowo tizaone ngati azaime poyela kuzaitanisa ndalamazo
@user-mi3ot6ms8x
22 күн бұрын
Ntanyiwa iwe ndikawawa
@user-hh4wn4vf9e
21 күн бұрын
Eee koma chakwera chita manyaz
@AyamiMwachande
22 күн бұрын
Bho
@user-do2cs8nf4b
22 күн бұрын
Awonatu maganizo a munthu simaganizo a yehova atafe ndi iwowo b4 2025 Mulungu musalore satana apambane mchititsen manyazi akudziweni inu mulungu
@DeliaKaduya
21 күн бұрын
Amen
@user-hk2ow8ey2g
22 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼
@user-wu4tl2yn9e
22 күн бұрын
Ndimanvela limpopo fm basi ❤
@AyamiMwachande
22 күн бұрын
Hi
@joebrown1158
22 күн бұрын
Koma ku Malawi 🇲🇼 kulidi asitikali kapena asitikali anali nthawi yomwe yija ya operation bwezani? Kodi asitikali amene alipowa anachokera dziko lake liti kuti adziwonelera zotelezi?
@AlexKaunda-ny2eg
22 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 zikhale ng'oma ndi namuudza kutu sarary ya june akagule malaya asiye kukhwima
@gladyschisomo4324
18 күн бұрын
Anaimba nyimbo yoti "abwela posachedwa" ndi ndani please help
@MorisSumaili
22 күн бұрын
angopa Malawi yose
@GraceZumazuma
22 күн бұрын
God have mercy on ur country chakwera akuzitenga ngati ndi Mulungu
@salafinamhone-rd1ku
22 күн бұрын
This is what happens when vote for the Devil 😈 and his angels,we must expect something satanic
@RobertChimenya
22 күн бұрын
Amalawi ife titha ndithu tifa ndi mantha Basi
@RobertChimenya
22 күн бұрын
Asilikali akumalawi amalandira ndalama zaulere ndiadyera kwambiri nchifukwa chake Ali mbali ya chipani osat kuteteza nzika tiyeni tizaona ukazatha udindowo
@FelixRonald-fx9df
22 күн бұрын
Mulungu smunthu, ngakhale angakonze chiwembu km mulungu sangalole
@MillyKachepa
22 күн бұрын
Ndipo peter anamukanika kale 😂😂 tiziona mapemphero amalawi akugwira ntchto
Dziko lathu ndi latulo asilikali ali pwiiiii a police ndi awo akugwirantchito ndi chipani kaya boma ili likaluza azagwira ntchito ndi ndani kaya?
@TroubleMuthala
22 күн бұрын
Angotipha Malawi yonse
@MosesKalenge
22 күн бұрын
MR, NTANYIWA NO, 1 ❤ 🤔👀🫂🫂🫂🫂🫂
@user-eh1mg3ww6d
22 күн бұрын
Ndiye azikana kuti chilima sanamuphe ndipo mulungu atembenuze list imeneo ikhale yao mudzina la yesu
@gladyschisomo4324
18 күн бұрын
List yachuluka yaanthu ofuna kuphedwa sakwanitsa
@harrisbanda5891
22 күн бұрын
Chikangawa yomweyo galu iwee
@AshrafBwanali-un1zz
22 күн бұрын
Comrade mtanyiwa ndi katundu, ing'alule zolimba ,osafooka, osaopa ,osatopa
@CostanceLalli
22 күн бұрын
Zinatha God is in control ñdipo mulungu salola zimenezi achoke chakwela pampando ameneyu
@GraceMwakanema
21 күн бұрын
Kkkkkkk😅😅😅😅😅😅mmkkk
@SolokingChimzy-yt7dj
22 күн бұрын
Upo wawo sungapindule chifukwa imfa amaivomeleza ndi Mulungu..I can tell you kut Chakwela mtendele alibe ngakhale kadontho mkat mwa moyo wake..mwadzi wa Munthu ndi ovuta😢😢...dekhani muone zomwe zichitike
@PhillipNyaugwe
22 күн бұрын
Amalawi ndi mr nthanyiwa chonde musapange ma ndimo yehova akufuna atinthandize kubwela nthenda ya chilendo ku palice yomwe ipangise kupedza amalawi tendele medzi iwili siintha mumva ngati simuva muzaona ndi manso yehova wabwino
Пікірлер: 164