Abambo ako aweyo Atupele muluzi ndi amene aononga dziko lino la Malawi,,,, dziko akutenga manja mwa ngwadzi kwatcha yathu inali ndi mpavu kwambili
@user-gx8or3yz9u
Ай бұрын
Chakwelayu asavitike ndikugwetsa kwacha chimene chikufunika apa angotipha tonse atsale ndi iyeyo ndi ana ake ntima wake ukondwele chifukwa sakutionela kukondwa 😭😭😭😭 ndalira mokweza ine
@KenChitete-pg3ws
Ай бұрын
Kodi iweyo Atupele unakhalapo president???
@Dickies-mk8cd
Ай бұрын
Malawi vuto mkusamva
@user-do2cs8nf4b
Ай бұрын
Panopa koma zanyanya ndlama ingogwa tsiku ndi tsiku tiyeni timbvomeleze kuti zinthu sizikuyenda bwino ma boma enawo mbuyomo sizinayambe zafika pamene zili leropa
@anniegundaphiri423
Ай бұрын
Chakwera must go
@SteviePatrick-g2p
Ай бұрын
Sound zikhala yomweyo ya makhazi limpopo
@KenChitete-pg3ws
Ай бұрын
Bakili muluzi anali pa nambala 3 kuno ku Africa pama president,,kodi dziko la Malawi inafikapo mu top 10 mumayiko a muno mu Africa???? Pano chakwela atsalemele chifukwa chiyani,,popedza ma president onse aku malawi alemelela mu boma ivini ma minister ma mp mafumu onseo amalemelela mu boma
@GeraldGund
Ай бұрын
Apa nde basi ndalama ija ikupita kuchizude ko chakwela ndiwe sakhwi kwa basi pubwa wa president kuwinaso chakwela tidzamuyatsa ndi mateyala ndithu
@BeckhamDavid-v6c
Ай бұрын
😥😥😥chakwela atipha guys tiyeni amalawi tidzuke tiime ndi born kalindo uja amalawi dzukani
@YasinMusa-ym8lp
Ай бұрын
Koma chakwera sofutha zindu zamuvuta koma kukakamilabe 🤔
@ThokozaniDavismlamba
Ай бұрын
Live on joburg
@luciarashid1961
Ай бұрын
Malawi 🇲🇼 ndi chani😢
@KenChitete-pg3ws
Ай бұрын
Kodi kwatcha yayambila pa chakwela????1994 kwatcha inali pa R1 to 1kwatcha,,,,,kodi anagwetsa kwatcha ndi ndani agalu inu mukunena za kwatcha ndi yakheni
@Twayibu15Chimbama
Ай бұрын
Tiyeuko iwe dog ukulakhulaziti
@samanthamuller7643
Ай бұрын
Uyu amayagula ngati sanabadwe ndi mayi ake galu kwabasi
Пікірлер: 18