M'manjamo mwa mayi Jen kuti phwa phwa phwa ulemu wanu amayi .
@madalitsomakawa9708
Ай бұрын
Tippex pa headline wabwera bwanji
@beinhardkausiwa7107
Ай бұрын
Mai ambuye azikudalitsani kwambiri
@duncanchiyani3879
Ай бұрын
Koma Dziko la Malawi!
@emmanuelmaluwa925
23 күн бұрын
Ine ndlibe nanu mlandu nsaname
@NephtaliKumsenjere
Ай бұрын
Mai oipitstsa uyu .
@itumbagarments6989
20 күн бұрын
Inuo olungama
@MtisungeMandwe
18 күн бұрын
Amai inuyo ndi mmai obheba kwambili ,pano tikuvutika zoziyamba tokha a malawi ,mum konda you
@liki-likiladies---lilongwe6963
Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂ma comment
@4568553
28 күн бұрын
I have bad memories about this woman
@aliedausi9733
29 күн бұрын
Mai wautsiru uyu
@JayMilazi-fv6px
Ай бұрын
Mayi ankalifunira dziko zabwino uyu koma ife kusamva pano ndi izi ndikuona nyekhwe amalira ndipo tilira zeni zeni 😂😂😂😂😂😂sinditha
@MphatsoAmos
27 күн бұрын
Satana anatinyenga , you were genuine mum
@ThandiBinali
Ай бұрын
Mulungu Akutsongoleni mama munagwira nchito ya bwino
@ElinaMkandawire-hy1ct
Ай бұрын
Ananena za mwazi anali lazalo
@SaidiMbawa-st6bj
Ай бұрын
Zisakho sizinayende bwino kuvomereza ndikwabwino
@user-yk1hw8kd5l
Ай бұрын
Kapenatu name umagwira ku MEC
@emmanuelnavaya5703
Ай бұрын
BIG STORIES
@Midy265
Ай бұрын
Forgive Malawi Mai Malawi...
@rodgersdamison2313
Ай бұрын
Mai oipa inu
@asivenathilitye7268
Ай бұрын
🎉😊
@EmercianahKasiku-en6hl
Ай бұрын
Mai ndinu munthu oipa komaso wabodza nokha mukuti simunathawe koma munathawa momwe mwalakhulira apamu and simumkafuna kutsazika Kwa mabwana Anu...mukutiso mumanena kuti asagule tipex nde tipex anapezekapo pamenepo ngati judge simukuona kuti sizinayende bwino poti inuyo ngati munauza Anthu Anu kuti asagwiritse ntchito tipex monga zisakho zinazonse zimakhalira mbuyomu nde mumafuna kuti Anthu asadabwe mesa Inu njira imeneyo munaikana chifukwa ndi yomwe amabelera chisankho a DPP Mai wachabe osakonda dziko lino munapita ku UK kukakhomelera kuti IMF isapeleke zithandizo cholinga Tonse alliance government ioneke yolephera
@Jstanleybeatz
Ай бұрын
Tonse alliance ndiyolephera even chakwera ndi olephera....blame game za ziii.....chakwera muja amayendera kunja muja kukakambila NDA Zungu zimapindula zachi.... MCP inapita ndi mwina wake kamuzu
Back to Sender ungayambe kumwalira Ndi Iweyo Kapena Azibale Ako Galu iwe😠😠😠😠
@abdullahibrahimbacqri3628
Ай бұрын
Satan mesa ndi chakwera wakoy
@user-mj3ms4jt3b
Ай бұрын
Cod knows kuti Mai ameneyu ndi Mai oyipa nkhope ndi mtima omwe. Chilungamo tiyeni tizinena, anali ndi mtima oti anthu pafupifupi 20 million iyeyo akane zigawo zawo ndikuti atipangile chiganizo chopambanitsa DPP pamene anthu tinavotera ena. Zagalu wako usamapatse ine wamva? Iwe ukuchita kumva yekha akuti akuma polling center anawawuza kuti azingonkwatcha nzere, chinavuta ndichani kuwauzaso aku tally center kuwauzaso choncho poti onse amayendetsa chisankho chimodzi chomwecho? Ndi ugalu wakowo sungaone kuti panali chinyengo?
@user-wd9yd1bg9n
Ай бұрын
Iwe ndiye mbuzu yamunthu , nyau yachabechabe
@successm-vt3dx
Ай бұрын
kkk nde ati ndi chisakho choyamba kuyenda bwino kkk
@isaacpelani
Ай бұрын
Definitely yes. It was the best ever. Kungotitu zonse zinachitika post 2019 polls zija inali kale plan. If you don't know mtambo was intercepted talking to a certain politician kuti APM akadzangoti wawina kudzakhala ziwawa zoti boma lidzakhale ungovernable mpaka boma lidzalandidwe and it was exactly what happened. Chitsankho chimene chija a UN auditors anali ntcheru kuonetsetsa kuti pasaberedwe. Majaji ajatu ankayenda chewu chewu mpaka ankayenda pa heavy military escort wokaweruza milandu. Zinyaeu nazo zinavuta mu LLs.
@successm-vt3dx
Ай бұрын
@@isaacpelani andare amwene iiiii
@isaacpelani
Ай бұрын
@@successm-vt3dxndimamafia and anthu azithokoza kuti APM ndi munthu ofatsa and sanafune kutsatira nkhuli yautsogoleri inadzala mmitima mwa anthu analuza 2019 aja.
@isaacpelani
Ай бұрын
@@successm-vt3dxndimamafia and anthu azithokoza kuti APM ndi munthu ofatsa and sanafune kutsatira nkhuli yautsogoleri inadzala mmitima mwa anthu analuza 2019 aja.
@aliedausi9733
29 күн бұрын
Jane Ansah ngwabodza ndalama za deal saperekera pagulu
@NedsonBilly
Ай бұрын
Inde mdzko muno zinthu sizikuyenda bwino koma pachilungamo maiwa adalakwitsa ndthu,, ndpo yankho ndilakut adathawa mademo 😂😂😂
@bayanimponda8746
Ай бұрын
Nkhani ndiyoti mumava bwanji kuti chisakho chomwe mumayendesa aku court nachikana? Ndipo ati chinalakwika chibwerere
Kkkkkkkk anthu amajama za Mai uyu.Koma iyeyo ankafuna kuti sugar asafike pa K4,500
@JoyceGondwe-ve1zu
Ай бұрын
Chiliichose chili ndinthawi. Kulibe wa muyaya. It's time for those ruling to rule. Nothing is wrong.. Ife mu nthawi ya Kamuzu sugar timagula K50. Accept change.
@JoyceGondwe-ve1zu
Ай бұрын
Nthawi ya Kamuzu sugar timagula K50. What are you talking about. Accept change. 4500 yomweyo
@BoniwelZimba-ki1dr
27 күн бұрын
Aaaaa she's was corrupt by using tipex as jugde
@Cittyboy363
Ай бұрын
I told them
@dysonmsamba5778
Ай бұрын
CHOMWE NDINGANENE MAI SIBWINO KUKAKAMILA PA MPNDO INE NDILI KUNONSO KU MANGALANDE TIKHOZA KUTENGAKO CHITSAZO KUCHOKELA KUNOKO
@DeveriuosChitsime
Ай бұрын
Galu uyu wabodza
@pushingpunisher6019
29 күн бұрын
Pansana pako iwe
@user-lg2ws2ki3d
Ай бұрын
Satana akomako ndithu
@YNOTGEORGE8
Ай бұрын
Mastn sopano mukuwalatu
@nellanzimba8181
Ай бұрын
Kodi akutichan
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
Ай бұрын
Kod munthu akakhala paudindo sakuyenela kukhala mfulu wachipan
@user-cc4fm2mn4t
Ай бұрын
Mayi madando mkukamba zabodza izi inu munathawa basi
@PrinceThom-pe6ie
Ай бұрын
Amalawi kunzunzana wokha wokha.a immigration masende anu nonse
@AmosiSingano
Ай бұрын
Kkkkk
@user-qc5hj1gy4s
Ай бұрын
Mrs T ipex my good mum
@josephphiri7161
Ай бұрын
Ndiye mwati amai awawa anali a judge ndithu mmhhh? Akuti tipex anatani? Mai uyu eeeee
@EvanceEdson-fz1vn
Ай бұрын
Atani kusakhala judge?
@user-nq9bg8zo4v
Ай бұрын
I don't trust this one
@starneckkulemero7548
23 күн бұрын
Amateur journalist
@simonkalambo1655
Ай бұрын
The journalist lacks skill of questioning.sensitive questions:1.did you share tippex? 2.your successor used same resources and workforce but there was no tippex used,why? 3.why you didn't report to police for kukhetsa mwazi intimidation? If you go to bank to collect money,all the details and figures are correct but there is tippex, will they allow you to get money,why? There was no cheating at all at examination centre and police were there but a student used a red pen instead of a black pen.will Maneb mark that paper?4.As a referee,why did you attend swearing ceremony while your successor never attended the swearing in ceremony? 5.Do you that mp elections only affect one area.for example tippex used on mp vote in Luchenza will only affect that outcomes of Luchenza but not of Karonga Nyungwe or Migowi but tippex used on president vote in Mzimba for example can affect the outcomes of the whole country?
@mdakakachokammanja7510
Ай бұрын
So tippex used on MPs and councillors was ok cos only affected mma constituencies? Maganizidwe a chinyengotu awa 🤣 Thought the MPs were elected in the same manner as the president ? You don’t pick and choose when you talk about justice, that is a corrupt mindset, kufuna zofuna zako zokha zichitike
Пікірлер: 101