Whoever took part on Chilima and 8 others' tragic death, will never have peace.
@RiteRoderick
Күн бұрын
Ndipo zoonad brother
@MussaChilembwe
Күн бұрын
Number one is chakwera
@GraceMwase
20 сағат бұрын
Ndi ana ake omwe ndizidzukulu zomwe ndiotembeleledwa
@JeffreyKambwemba-zs7wy
16 сағат бұрын
Exactly brother
@christinemudziviri8398
13 минут бұрын
Amen 🙏
@bonneygeoffrreya.s.chinund7220
Күн бұрын
Zolepheretsa kuyankhula. Ambuye Ambuye tikudalira inu. I stand with you Mary.
@sahilujameswadison-r9i
22 сағат бұрын
Ngakhale MDIMA utakula motani .kucha ndithu . 😢😢😢
@FidesChandama
Күн бұрын
Adalakwa kwambiri anyamata ang'ona party sadaganizile kuti anthu akuwaphawo ali ndi ma udindo mmabanja awo komaso maso wa anthu ambiri amadalira iye kukawaphela pachikangawa koma chakwela ndi mkazi wako oipa nkhope ngati sing'anga wamizimu mulungu adzikuona
@fredsonmulewa3575
16 сағат бұрын
Fffu Bbgffvgg
@RuthChilobwe
Күн бұрын
Uku ndiye kulankhula madam Mary chilima .indeed you must seek.how your husband was assassinated .cruelly..God bless you and comfort you..with the Holy spirit.refer Exodus 22 vs 14 amen
@MaryTchapo-py4hh
Күн бұрын
Very painful death. Akuyenera kutero mkazi wake. MHSRP
@SilajuMajadinbanda-qn9ue
Күн бұрын
This is too painful and heart break 💔💔 but god comfort you mom and us too we are just brave and waiting Truth from God
@HappyAnt-uz5je
14 сағат бұрын
😢😢😢V
@IshmaelNgeyani
Күн бұрын
Agalu in a mcp mulungu akuoneni pa imfa ya chilima
@danielkalipansi9139
Күн бұрын
Chakwela ndi azako (MCP),,, mmmmm, you are more than DEVIL, koma likwana tsiku lanu nanuso mupita koko, MULUNNGU SIMUNTHU, (njila yachidule sumadutsa chilele),, 😢😢
Munthu alibe pa bwino chikondi ICU chidali chakandiolotse ndikakutafune. Chakwera ndi oipa kwambiri. Rip
@Francis-rz6fv
22 сағат бұрын
Timati 12 midnight.eee amalawi school imativuta pang'onong'ono
@SankpA-t9
Күн бұрын
I know she is passing through hardship but I request you to stand for UTM presidential candidate truth will be come out by yourself and you will win....seriously
@TakalaniGlenda
7 сағат бұрын
For the sake of respect ine ndikuona kuti it's better asayime pa ndale and she will be respected forever am telling you guys
@JoyceChiulika
21 сағат бұрын
Sorry mum Mary chilima tikukupempherelani banja lonse tsiku ndi tsiku Ndipo mulungu sankhala chete ndi mulungu wakumva whatever happened god will reveal it palibe chobisika padziko Keep on praying
@JoyceChirambo
21 сағат бұрын
Sorry for the loss, imfa iyiyi yinatipweteka kwambiri, limba mtima Mary, yang'ana kumwamba, Mulungu ndiye yankho la zonse ndiponso ndi Mulungu wazatheka bwanji, ambuye akusogolele ,kukupatsa nzelu ndi luntha kuti usamale bwino anawo, tili nawe mumapemphero
@AARONCHISUKAMZION-we3vp
Күн бұрын
Mama Chilima may God continue to comfort you. Ndipo zimene zinachitika apa nzeru zopusa ngati zamwana. Munthu wamkulu sakufuna kubwera poyera ,azimulankhulira mpakana liti,kungokhalira kuyendayenda. Munthu ukachimwa siukhala ndi nzeru Ngakhale mumunda wa Eden Adam ndi Eva atachimwa adalibe nzeru amangolubwalubwa kuziphimba ndi masamba kumaona ngati zilibwino. Mwapweteka banja la Kwa nkhazi withu a Mary Anniversary yekha iyi yakwa Chilima imwe uko muli High blood pressure musizgikenge. Anakunyamuliranipo pa mpando Malo mothokoza nkupanga chipongwe. Kutha kwamoyo nkulekana koma siizi zinachitika apa. Yendani maulendo ,koma posachedwa mutopa inu mpakana tikakhale Nanu pansi pa mtengo wakachere analakwanji a Chilima abale Imwe no mtendere,muli kupweteka mkweni watawina Mzimba Muchali "NG,WINA" Imweee!!!!!!
@JulietNyondo
20 сағат бұрын
Zooona tiziwe zoona zwni zeni chifukwa palibe chilungamo apa pa yifwa ya bwana chilima mama ndakunyadira mwabwera poyera kuti anthu aziwe ndi chithu chowawa
@WejesWailes-lk4cz
Күн бұрын
Osataya mtima mama mulungu ndiye akumenya nkhondo ife tili chete ndipo oyipayo akhala poyera
@JohnMankhwala
21 сағат бұрын
ine ifa yachilima ima imandiwawa kwambili ndipo ndikamaona zithuzizake zoti anamwalila ndimaonangati boza, zikomo mama pobwela poyela ndikuyakhulapo ndipo mwayakhula bwino, limbani mtima ama mulungu akuziwa zonse ndipo silelo simawa achitapokathu Ambuye azikutetezani mama zikomo.
@McshonWilliam
Күн бұрын
God bless you mom, apa nde mwayimilira malawi and I'm so glad you
@VicentMalopa
21 сағат бұрын
Stay Very Strong and Courageous Madam.Chilima,❤❤
@YellowmanMalawi-qe8zh
Күн бұрын
Ngozi imeneyo izaziwika boma ili likazachoka
@TamalaMgomezulu-m7q
Күн бұрын
Sorry Mamie may Almighty God continue comforting u and your family 🙏🙏🙏🙏
@annamazingashaibuh6276
22 сағат бұрын
So painful uhmmmm the pain its too much moyoo kuwawa as it is her wedding anniversary samavetsayiii eish zolilitsa iziiii😭😭😭😭😭
Mmmh Zovuta kumvetsa mpaka lero no mankho ndinso sindimakhulupilira ndithu mpaka Pano
@aliwillardkundaje1083
Күн бұрын
Ndale zausaveji
@RiteRoderick
Күн бұрын
Mai Gotani Hara ndi MCP anachita kunena kuti akhesa mwazi ndikuthira nsembe kuti Chakwera azaimebe 2025. Video yake tilinayo tinaisunga tionana next year adziwanso a MCP
@JustinMpunga-c8b
Күн бұрын
Mulungu si James chilungamo chidziwika no matter what may his soul rest in peace
@ThomasTembo-m3d
Күн бұрын
Ndipo achita bwino chifukwa imfa ndiyo wawa yomwe adamwalila Chilima ndipo chilungamo chiwoneke basi
@LinlyMatheweKufakwina
Күн бұрын
Forever in our hearts ❤ambuye atichitile chifundo pa nkhani iyi
@On472Onse-i5f
Күн бұрын
Mulungu wathu adzambulutsa palibe chobisika pasi pathambo
@PraiseShongwe
Күн бұрын
God plz deal with those involved manyazi awagwire
@AyasiWhite-l6s
Күн бұрын
Mmmm chakwera anakwanilitsa zofuna
@RobertNgunga-b4w
Күн бұрын
Ndizimene timadikila kuti atiyankhule
@LovenessBanda-p5s
21 сағат бұрын
Loveness Banda naneso ntemawanga umawa mungu alowelepo
@OliveChatepa
Күн бұрын
Mmmmh so sad. Continue resting in peace Bhiyeni, my beloved principal 😢
@FreddieNkhoma
20 сағат бұрын
Sorry, for we are all in great pain accept MCP members kapenaa mfitiii let us walk to gather as One Triple O OSAOPA, OSATOPA osafoooka
Pepani mama Mary chilima ndi zithu zopseteka kwambiri zosavesetseka 😭😭😭😭
@billybanda7280
Күн бұрын
We were being robbed big time!! Zobisika zonse zidzabwera poyera mudzina la yesu!!!
@RiteRoderick
Күн бұрын
Amen
@DennmichSimb
Күн бұрын
We need new enquiry for how Our leader died on 10June 2024.We cry with you Madam Mary Chilima everyday until the truth comes out,no one involved in the death of Chilima will have peace.I wish the spirits of our beloved Malawians who lost their lives on that day to keep visiting those involved.
@RosinaPatel
Күн бұрын
Tiripa mbuyo Panu Mary..mulungu ndi owona..sanatitaye zibvumbuluka pompano
@patricknthakomwa5613
21 сағат бұрын
The only truth can come out when you personally stand as leader of the party your beloved husband led. It is only a strong woman who can achieve what the foundation of her husband started.
Tipemphe mzimu wa chilima uwamenye koopsa mpaka awulule Kwa Malawi zitsiru kwambiri
@GanizaniKamvazaana
20 сағат бұрын
Ndipo tu achita bwino a maona ngati basi azionatu adzikodzera chakwerayo a maona ngati basi walira kwatsarq kuferana basi ndi chakwerayo ndipo asaope mayoyu ayaluka
@EmanyauZuma
Күн бұрын
Akhakhakha a mcp pamodzi ndi chikangawa 2025 nonse mudayika nzanja pa tsongoleli wathu mukanyela ku police tidzakuyendetsani ma police onse ngati munja muchitila athu munja
@InnahSaeed
20 сағат бұрын
Aliko anatilenga koma chombisika chizaulika basi koma ifa yovesa chisono
@JohnChikoti-e6f
Күн бұрын
Pepan zoona zenizeni za imfa ya SKC idzadziwika chipanichi chikulamulachi
Pepani mayi chilima,boma ilitu silingakupatseni mayankho okhudza imfa ya SKC. Ndi mfiti za anthu
@On472Onse-i5f
Күн бұрын
Ndinakhulupiriradi kuti mcp ndiyakupha
@IshmaelNgeyani
Күн бұрын
Tikafukule thupi mkukalipimaso
@GetrudeJack
Күн бұрын
Mtima wake udakalibe osweka
@twaibupatrick-k1n
Күн бұрын
Ndale zausaveji za mcp
@ManganiStanley
Күн бұрын
😭😭 pepani Koma commission ikufunika kwambiri tonse tiziwe chilungamo a Boma musaope chilungamo
@innocentkapachika6591
Күн бұрын
Unfortunately, the same bloody hands will appoint the Commission of Enquiry. Nothing will stop him/ them to use everything to bring a corrupt report. They have free money from our hard earned taxes to buy people and influence decisions. God is faithful
@manasemaposa
Күн бұрын
Just oooooo GOD
@paulnyondo7572
Күн бұрын
Gotani hara anayankhula live kuti chipani cha mcp chikuyenera kumakhesa mwazi kuti mpaka chipitilire kukhalabe mboma mpaka 2030 .zowophyatu.chipani chamagazi essh.
Nde wina adziti ayimile ku UTM. Momwe akuonekela kuswekabe mtimamo Mphamvu azitenga kuti? The DC its easy for you to say kuti amalawi akuti mary should lead utm and keep skc"s legacy simukuziwa momwe zimamvekela when you lose your loved one especially this way
@Yoxym
Күн бұрын
Koma akakhala president azapeza chilungamo yekha bwino bwino
Mary mama may God protect you and continue giving you courage don't fear but fear almighty we are with you. Thanks for coming in.
@MercymawindoMercy
Күн бұрын
😭😭😭😭😭
@Halima-i4x
Күн бұрын
😢😢😢😢
@lowkey_drey
Күн бұрын
😭😭😭
@ClearKondowe-m3j
4 сағат бұрын
Mama God knows everything.
@LilianKachala-yz2xf
22 сағат бұрын
We have been waiting for that REST IN PEACE SKC
@GreyMtungama
23 сағат бұрын
Even if she calls for peaceful demos we're ready to support her,,an independent body of inquiry must be organized,,RIP Biyeni.
@DanielChikoti
16 сағат бұрын
It's a very sad story. Whatever whatever whatever Guys MCP and Chakwera know everything. coz it was their mission period. God will help us sure 😭😭😭😭 SKC rest in peace
@agnessliwonde
Күн бұрын
Sad. Devine comfort be upon you and the entire family. Mhsrip 😢
@LuckwellMsoti
4 сағат бұрын
Yy ndthu or ine mpaka lero sindinasimikizgebe zaifa ya SKC 😭
@adammwakitalu7959
23 сағат бұрын
Commission of inquiry will not help us. Our beloved ones will not come back . Its titi for tati. Wopha aphedwe
@BrownChitseko
5 сағат бұрын
Chilungamo sichingadziweke till boma litasitha but for now mmm guys tingotaya thawi
@RuthMkangala
15 сағат бұрын
Mary God is watching don't worry Rest well skc
@bridgetmajor3646
Күн бұрын
Zoonadi....atiuze chomwe chinachitika.....Tiziwe ndinthu A malawi......ndipo Ambuye woziwa zonse..chilugamo chizaziwika.... Ambuye alinawe Mary....ndipo sanakusiye.....wekha... ndipo Alinawe...ndipo sazakutaya pamodxi ndi Ana ako🙏
@MarieJana-k9h
5 сағат бұрын
We are still cry with you mamaaa Mary anatidulira mutu God knows
@ShillahLawrence
Күн бұрын
That's true,Chilima was like my brother:IAM also confused and make sure that ,some people has to brought to book
@DANIELNGULUBE-k3k
2 сағат бұрын
Mama Mulungu akukuteni paganizo lanuli chifukwa akhalapo ena akukunyozani paganizo lanuli Mulungu si James
@LuciusChidetsa-c9n
4 сағат бұрын
Mpaka kale, misozi yathu siizauma!! Koma mulungu ovumbulutsa zobisika, tithandizeni kuti tiziwe zoona zomwe zinachitika
@Fatima-db8ut
22 сағат бұрын
The enquiry to be set as per request from Madam Chilima should at some point work together with the German investigators ,,share the findings and recommendations. Its straight forward, Ambuye mulowelere
@ShyfaceJutah
16 сағат бұрын
Don't worry Mama Mary Chilima everything is gonna be alright and the truth is about to come out.
@MarkChibwana-r5e
Күн бұрын
Take heart madam Mary chilima,why Skc?one day the perpetrators shall be brought to book
@andreabanda7838
20 сағат бұрын
Mama Chilima is not asking for condolences apapa. Ai. She is asking for action: She is asking for a commission of enquiry. We all are asking for an enquiry on that tragic incident. Commission of inquiry is a process. At the end of it all people involved will have to be taken to book. Malawians need to know why this happened. And how the courts will deter this in future
Пікірлер: 330