Koma ndiye nyimboyo munaifunatu kumayambiliroko,,, abale taziyesetsani kumapangako upgrade munthu ukufuna uwonele program ya 45 minutes koma 10 minutes yonse kutha ndi nyimbo yoyambila mpaka kutopa ahaaa
@victorbanda9039
4 ай бұрын
Mchifukwa Chake gaga umandibyasa umbava wachikhalidwe kupita nawoso musewero
@adamusaidih8570
4 ай бұрын
Athu ambili samatha kusiyanisa history ndi khani awa akukamba khani osati history 😂😂😂😂😂😂 ndichifukwa makolo amati kunva ndikunvesesa ndikosiyana ndiye amazati tabweleza zomwe ndanena cholinga aziwe kt wanvadi
Пікірлер: 20