Mwana wa Queen alibe bambo ake, mwana wa Mkango akuti, ndi wake komanso a Shokoshoko zimamvekanso zoti anagonanso ndi Queen, Agani ndi awa, akuwatsiyira mwana akuti agogo ake a Mwana ali ku Mwanza chonsecho akusungidwa ndi Mercy.
@AmiFundis-x5h
2 сағат бұрын
Thomas Richard Williams Melissa Taylor Amy
@BlessingsMikeyasi
16 сағат бұрын
Queen is on fire 🔥🔥
@TamaraSeleman-cl2fc
3 күн бұрын
Km queen. Mutu wake sumagwira
@ChireDeville-mh4cu
3 күн бұрын
Brown Kevin Brown Elizabeth Martin Richard
@chikuchimbatata3169
2 күн бұрын
koma chiphwanya amandiwaza mavuto samuchoka , pali uyu gani queen amangokhalira kumukweza bp ... i like this sindifuna kuyimisa
@JaneChimasula
3 күн бұрын
I like mwana wa mkango amangoseka😂😂😂😂😂😂
@RadsonTimoteo
2 күн бұрын
Kkkkkkk sasoka ati chiphwanya olo utamupha sangakwane ndio masana ndi madzulo
@jrculdickson6629
2 күн бұрын
Mnyanyiwa kokafuna mkazi kuchena kumeneko 😂😂😂😂😂
@dominicmphepo-jk8lk
4 күн бұрын
This episode mwapha ndithu Big up team Mdyangu
@ToxAlimonjaimeJaime
Күн бұрын
Manowo ogulisa alipo
@FatimaMaunde
4 күн бұрын
Nxt
@EdythGloryNamponya
3 күн бұрын
Let Mercy n Chuma get married...
@PaulBondo-k7e
4 күн бұрын
Mumakwana watching from white river mpumalanga
@HappyFlipFlops-di5gg
4 күн бұрын
Koma a mdyangu ndi dolo amaziwa kuyiyamba khani...
Пікірлер: 144