Mayi Mdyangu I salute you mama mumatha zedi, mumakhala serious ulemu wanu basi........komaso team yonse muli bwino zedi
@FosterChakanga
8 ай бұрын
At first ndimangoona ngat nepman mwamutenga coz ndi otchuka koma he is a real actor.Pitiliza bro,,,umatha heavy!!!
@EdythGloryNamponya
8 ай бұрын
Well done mayi shokoshoko queen ndi wamwano iyaaaaa
@raytavares2256
8 ай бұрын
Kkkkkk hilarious hilarious hilarious today my best actor of the night was Mrs M'dyangu the land lady second the music man and pst mlelemba the prophet and finally the sister of Queen. 😅😅😅😅😅😅
@HusseinSsaidi
8 ай бұрын
😊😊😊😅😅😅😊
@HusseinSsaidi
8 ай бұрын
Uu
@GracePhirieh-tv6rl
8 ай бұрын
Mlelemba ngwamabodza😂😂
@HaggetBanda
7 ай бұрын
kkkkkkk🤣🤣🤣🤣 kapangeni mafizo a Ching'ani ng'ani 💪🏋♀️🏋♂️
@clesheinvestments
8 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Ayi koma ndi ndi zikomo ndithu. Mdyangu chisangalalo chosatha Cha a Malawi and beyond.........
@PLANBDAMZY-c7n
7 ай бұрын
Kkkkkk koma mulelemba❤❤❤❤❤😂
@storytambala6088
8 ай бұрын
Shokoshoko, ufatsedi ukulowerera mtundu wa eni zoona umamuyikira queen kumbuyoku. Uyang'ane kuli mtundu wako, abale ako sanafe onse kwanu ayi.
@isaaczidana2914
8 ай бұрын
Norman akuti Chuma akumadontheza mwa Mercy 😂😂😂😂😂😂
@ChristopherLipenga
8 ай бұрын
nde mwati asasoka ndi akazi awo amalira ku chipinda 😂😂😂
@bristonniekammwamba
7 ай бұрын
Mlelemba kkkkkkk izi zili ngat denje
@OsmanIdrissa
8 ай бұрын
Mayi😂njangu😂mumati imilila❤
@AngelChafupikachafupika
8 ай бұрын
Mayi chokochoko mdzikharako ovesta thawidzina I'm watching from Capetown hermanus
@lingstonenagoli7729
8 ай бұрын
Shokoshoko not chokochoko
@shaniahkhephass9925
8 ай бұрын
Koma mayi shokoshoko apa ndiye mwabwela kuzakhala ndithu 😂😂😂😂😂😂
@macuwaynemereck4069
8 ай бұрын
Mamie ndidyeko nanyama waikazinga bwino Mai Mdyangu anakonza
Mwana wa akazi achiphwanya ndiwa sérios iiiiii kamwana koma kosaseka
@harrisonnavayah6480
7 ай бұрын
Chiphwanya wakhululukidwa
@EstherZintambira-sq3yy
8 ай бұрын
Mai shokoshoko dzilungamo zimawapweteka mwana azipitadi kwa bambo ake kkk
@editehissaoisakisak8703
8 ай бұрын
May shoshoko safuna zibwana mwana apite kwa bambo wake kkkk
@MrJChumachiyendaChisale
8 ай бұрын
My question is kod why mdyangu comedies simatheka Ku download pa KZitem pa tell me?
@FelixvanPhiri
8 ай бұрын
You need to have KZitem premium
@MannersonMilla-hi5dr
8 ай бұрын
Mai Shokoshoko milandu kumaitaya
@giftblack7690
8 ай бұрын
😂😂😂😂😂 mulelemba ndiwantopola kwambili
@portianahkalonga
8 ай бұрын
16:04 watch out girl👌😂koma mayi ndyangu
@TadalaWillies
8 ай бұрын
😂😂😂😂am the landlady here😅😅😅
@BigknotKalonga
8 ай бұрын
Chimphanya ndi dolo guys
@MacdonaldMakalani-pl7hx
8 ай бұрын
Km mlelemba 😂😂😂😂😂😂 kt chani iweo 😂😂
@CONLEY265
8 ай бұрын
Nepman 😂😂😂 akut Mercy unadotheza
@GeorgeGeorge-bu6cy
8 ай бұрын
Welcome
@LaikaBwanali
8 ай бұрын
Mlelemba plz ati mahule 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@danielantoniomsutu8736
8 ай бұрын
You are coming guys I appreciate you 👏 even the background music 🎶 is also very sharp ❤❤
@AfickDaud
5 ай бұрын
Amene umalasana nayeo sanakwane? Kkkk
@MKkkk-v3m
8 ай бұрын
Mai shokoshoko mukanamudikira Kaye mwana pang,ono
@shupikayintuwaluwa-5899
8 ай бұрын
Kkkk zilbwno
@anniewhite3497
8 ай бұрын
Mulelemba mimba zanu denje😂mumatha nonse
@ephraimbanda9813
8 ай бұрын
Guys mmatha,mpaka mwakapeza mwana? queen wapepukidwa ndi zisanza zija chifukwa unanyamulatu katundu,mayi shokoshoko muzikhalika simungamudikireko pachoko m bale wanu apume kaye mpaka pa get eeeee Cecilia anakoza,Kaya poti wapita koyenera kupita koma nkhawa yanga ili pa mayi mdyangu satiphera mwanayo pakuti queen ndi ndani wawo mayiwo?Gan watch out mwayi ako ndi afiti amatamba usiku wakutelo Nepie man
@BlessingsLuclus-x2j
8 ай бұрын
Kkkkkkk chipwanya suzatheka
@mphatsolupiabanda6910
8 ай бұрын
Kkkk tama apa nde akuoneka kuti adaudyatu madzi
@danieleneya808
8 ай бұрын
Wawooo first person to view🎉🎉
@SteveShaya-d7r
8 ай бұрын
Mulelemba mabodza 😂😂😂
@lestinakaponda9464
8 ай бұрын
Kkkkkkkkkk a Mlelemba
@MisheckAselo
8 ай бұрын
LIKI_LIKI LADIES YOU DESERVE IT 👍💥💥💥
@GiftMwalabu-c5q
8 ай бұрын
Mlelemba nd 1😅😅😅😅😅😅
@violetwanja9592
8 ай бұрын
Mai shokoshoko
@gidyonmshani5259
8 ай бұрын
Amurelemba mulungu anakhondza
@JuniorLiganga
8 ай бұрын
Kma mlelemba
@kettielozario-px3pl
8 ай бұрын
🔥
@emmanuelkathumba7611
8 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣 Kma
@FelixvanPhiri
8 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@NthakaSinthani
8 ай бұрын
😂😂😂 nyumba yamecy ndiyokopa arendo Kkkkkk km yaaah
@ShabanNicks
8 ай бұрын
Mai shokoshoko pena muzivako za ena please 🎉🎉❤❤
@DonaldPonda-p2q
8 ай бұрын
Zangondimvesa chisoni kukanidwa kwa queen kwa chemwali ake
@christopherpetro-pen3678
8 ай бұрын
Mrs mdyangu vs mercy 😅
@SaymonSaymon-bp8us
8 ай бұрын
Mumanta
@pybenmbewe8462
8 ай бұрын
Mdyangu comedy job well done 👍 so interesting keep it up 👏👏👏👏 queen you're now a mother , is that a baby boy or a girl?
@FranciscoCatlin-m1k
20 күн бұрын
Hartmann Ridge
@ArenaTadala
8 ай бұрын
Mumatha inuyo ❤❤❤
@yassinrashid7012
8 ай бұрын
Akufuna kubereka elephant 😂😂
@YalediGondwe
8 ай бұрын
Koma bambo wa banjalake lo chuluka kusamala ana kumumvuta aa🤔
@ellennchambalinja484
8 ай бұрын
😂😂😂 Mai shokoshoko
@ShareephSmart
8 ай бұрын
Number 5
@AustinBanda-wg5pw
8 ай бұрын
The landlady
@jozyunlury36
8 ай бұрын
Musiyeni abeleke elephant 🐘😂
@mussaganeti
8 ай бұрын
Sasoka chimpwanya 😂😂😂😂😂😂
@etomansailes4932
8 ай бұрын
Km mayi shokoshoko eee 😅😅
@AliAli.aliheassim
8 ай бұрын
❤❤❤
@GanizaniMavuto
8 ай бұрын
I m here mess
@KenedyJolamu-rs9xx
8 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️🔥🔥🔥🔥🇲🇼🤸♀️
@Monicalikhupa
8 ай бұрын
Mai shokoshoko sadzayheka
@PeacefulRiverboat-iw3eu
8 ай бұрын
Eunice I love u..ur so beautiful mami
@portianahkalonga
8 ай бұрын
5:08 ati donayo😂💔ili ndi ana 8
@vukanifracksonchinkonde7324
8 ай бұрын
Kodi queen was really pregnant or it's just an act....?
Пікірлер: 126