Mulelemba best comedian in malawi 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼 palibeso akufunika ku fumu kazi katundu omanga ndimawaya uyu mulelemba
@pybenmbewe8462
10 ай бұрын
Wow so interesting i salute you guys , thumbs up👍👍👍👍👍👍
@matembanevermind-po3me
10 ай бұрын
Mrs Mdyangu pakamwa Pangoumiratu no comment kk
@cassimyusuf6683
10 ай бұрын
Miss shokoshoko ndi more fire 🔥🔥 akhoza kukutafunatu nkazi ameneyu
@johnlufai2665
10 ай бұрын
Boma laletsa kudikiza ...mboni ndi mlelemba😂😂😂
@user-Mamie461
10 ай бұрын
Mai shokoshoko sayankhula bwino msaname,,, ngt pa real life amapanga choncho mmmm kunyumba kwawo kuli mavuto,, ndipo ndi misalay zikuwakhala kwabas,, Cecelia 😂😂😂😂
@matembanevermind-po3me
10 ай бұрын
Komatu kukhala maso nd maso aaaaa Mulelemba Ukhoza Kuyenda Mmapewa mafanz.nd Mercy yemwe kutsitsimuka kkkk
Ma shokoshoko ndamunanu mumaitha😂😂😂mbalimu queen, Eunice ndi Mercy
@keita9875
10 ай бұрын
Koma how I wish mai chokochoko tsiku lina zao zikhale pabwino, za chokochoko nd quin ziululike ndithu kut kwa ganie nkongonamizira. Ka quin shd dance to her own music
Пікірлер: 119