Gututu akadzagwira Nagama ndidzakhulupirira kut we are in world of possibilities, can't wait kudzaona ka family akaka. Go Gututu gooo osaopa mkaz akatchena kkk
@user-sw7fw4wd1m
9 ай бұрын
❤❤❤
@user-yn2um5ir1y
10 ай бұрын
😂😂😂😂 a chemwari a karaka 😂😂😂 ndi one eti mfumukazi maluzi amukamata kkkk
@user-kh2di7pj4x
9 ай бұрын
❤❤
@anniewhite3497
10 ай бұрын
Amfumukadzi akumana nazotu ndi alongo awo Akaraka😂 maluzi kuno😂😂😂😂
@cathykawawa9343
10 ай бұрын
Kkkkkk koma Chiphwanya ndi Gututu simuzatheka mumandiwaza inuyo 😂😂😂😂
@user-le9kc2gx1g
10 ай бұрын
😂,😂😂
@immaculatethawani623
10 ай бұрын
Namoyo ndi mfumukazi woyeeeeeee😂😂😂😂
@AnneKafumba-nd9gk
10 ай бұрын
Kom mumatimvesa kukoma kwabas
@keita9875
10 ай бұрын
Lero katha kakukoma kwambiri❤❤❤
@MbwanaAmosi
10 ай бұрын
Good work guys
@antonychika15
10 ай бұрын
Komatu Paderayii aaaaaa kkkkkkk Tomato wa K100 mpaka kunyamulitsa aganyu kkkkk
@lewisjosaya8769
10 ай бұрын
Hayi hamvani
@user-nj5vu8cd5l
2 ай бұрын
Ku honeymoon kale ... I love you guys❤❤
@danielantoniomsutu8736
10 ай бұрын
Nagama, anthu akufelatu awo kkkkkk
@GOEMENGONDWE
10 ай бұрын
Tonde Basi pano suliso mmavuto ayi kumakana koma kantima konko😂😂😂😂
@patrickmkhalipa-my4en
10 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥
@DawoodChamba-cg8pp
10 ай бұрын
Liki liki
@harrisonnavayah6480
10 ай бұрын
Padela walipira
@cassimyusuf6683
10 ай бұрын
Mayi padera she's the best actress
@user-nu3kk8xr4s
10 ай бұрын
Maluzi akukamatan
@user-uj9ob1hs6g
10 ай бұрын
timakunyadilani ❤
@atom3492
10 ай бұрын
This kalanka's sister yoooo...... I like her😍
@rashiddeula5715
10 ай бұрын
Missed Farai in this episode haha. Komanso Titani ndi nkhani zina. Hahaha! I love this! Great job everyone!!
@JamesMalango
10 ай бұрын
So nice 😅
@bernadettechoma
10 ай бұрын
Ati ukudya thukuta la wina😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@teezdada
10 ай бұрын
Achina Flora panga movie ya smoldering charcoal
@MalthaMaltha-mv5fq
10 ай бұрын
Kkkk
@daviekamanga1417
10 ай бұрын
❤❤❤🎉🎉🎉😂😂😂😂
@AleksaWilliams-qc6cn
10 ай бұрын
Nice😅😅😅😅
@patrickmkhalipa-my4en
10 ай бұрын
Funukadzi maludzi akamata 🤣🤣🤣🤣
@GeorgeGeorge-bu6cy
10 ай бұрын
Kkkk yeah
@merviskhongonyowa5621
10 ай бұрын
😂😂😂😂😂mfumukazi
@josephkopakopa284
10 ай бұрын
Nice
@JamesImran
10 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣 km week ikubwerayi ili bwino kwabasi ndipo gyz mukutinvets kukoma kuno
@user-sl8ke2qw6v
10 ай бұрын
Giling'ande samachiminatu akumpasanso ndalama padera kuiwala zot anamutengera zinthu😂😂😂😂 zake sapeleka ndalam
@keita9875
10 ай бұрын
Pajatu anakailandira kwao konko. Komanxo ma boys timamvana kkkkkkk
@user-sl8ke2qw6v
10 ай бұрын
@@keita9875 Sanatengetu pajatu padera akukasiya soap uja sanatulukenso ndi mkazi wake uja watch again muonanso
@yassinrashid7012
10 ай бұрын
Koma mlongo wa akalanka amalapula😂. Koma she's beautiful
@rogeriorafael7207
10 ай бұрын
NDAFUNAKO KUTHOKOZA KAMBA KA NTCHITO IMENE MUMAGWILA,NDINE ROGÉRIO RAFAEL THUIA NDIMAKHALA KU MOÇAMBIQUE,NDIKUFUNA NAMBALA YA ANAMOYO,YA WATSAP NDIKUFUNA TICHEZEKO.
Пікірлер: 62