Thanks Mr jokes ndipo mukunanezi ndizoona, vuto anthu timayang'anirana pansi, ineyo mnzanga tinakula limodzi sukulunso taphunzira limodzi, koma anachita mwayi akwatiwa ndiolemera kuti ucheze naye amakuuza pamaso kuti anthu osowa chochita ndimasowa zokamba nawo chifukwa awo ndimadandaulo, since then ndinachivomeleza mmoyo wanga kuti anthu ochita siamnzangaso. Mr jokes God bless you mwina ena akhoza kuphunzirapo mwakambazi🙏
@mroptimistic300
Жыл бұрын
🇿🇲 It's absolutely true if you ask me, you are transforming peoples mind by so doing, keep up good work.🌻 Muthandiza anthu osiyana-siyana m'maganizo awo 🌻 kindly be in progress of giving us all what you can and do it as you have prepared. From my point of view I submit 🙏🙏🙏🙏🇿🇲🙏🙏🙏🙏.
@bs-malawi
3 жыл бұрын
If possible, don't make longer videos longer than 10 minutes. If possible you can cut it and make it part 1 and 2. Suggestion anyway
@mrjokes001
3 жыл бұрын
Zikomo kwambiri boss
@maryzulu8439
Жыл бұрын
Very Perfect said Mr Jokes love you so much
@chisomotembo5176
3 жыл бұрын
Dzulo si lero, lero sim'mawa, tiribe luntha lodziwa za mawa...Phunzirani lero kukhala bwino ndi amzanu.
@isaacfesani2357
3 жыл бұрын
Mau opanda chigamba mr jokes. Nsanje siimanga mudzi
Пікірлер: 33