Tapezani camera yabwino pls ndinu wailesi yaikulu pls
@aleksawilliams710
Жыл бұрын
Tikuyisatatu nkhaniyi,,,momwe amkakambilana ndi Mr manjolo ndi Enest yo timazimva ndipo akut wakhala business akupanga wagwidwa nayeyu ndiwanambala 5,,,ntchito yake ndi yomweyo koma samagwidwa ,makolowo akungodandaula Poti kubeleka koma nanga akanakhala kut wagwidwa Mathews yo atamupaha kale zikanakhala bwanji? Tiunikepo pamenepo a Abel,from Balaka thank u
Thanks for continuing this story! I feel it for the poor boy! I’m glad that he is saved. His fate was about to be gruesome!!! Kudos to the two people who saved this kid. It hurts to even imagine how traumatizing this is going to be for this kid for the rest of his life. We all need to be following up on him. Just sad. Wish the perpetrators got the death penalty for this.
Пікірлер: 57