Anthu akumwera inu koma muli ndi kwiyo koma boma lokha sitisintha munya inu mpaka 2030 woooooo
@AndersonBishop-i2t
3 ай бұрын
Iwe tachoka apa 2030 ndanio machende akowo ndi 2030 yakoyo ukuwona ngat ndi gule kod iweo ndi chakwela wakoyo kupanda kuvota mumwera kuno ku mpoto inuo chigawo chapakati simungawinebe mwamva muzikhala mukuziwa zimenezo ku mwela kuno ndi kumene kuli anthu ochuluka kwambir ndikumapita ku mpoto pakatipo Mesa mwangochuluka ma farm basi ndie mukuona kuti inuyo mungamuwinise chakwelayo inu agalu eti muuzaneso zimenezo ndi kuousa kwanuko
@JohnAsendi
3 ай бұрын
Akambanje ndigulu lanu pazakuti zanu musankha nokha pazomwe muzitukwane papa njoka sitimayang'ana zakuti Pali madzira ankhuku kapena Pali m'phika ine ndikukulupirira Pali chaka chomwe Ana sukulu sanalembe mayeso ndiye anamwalira nyamako mapana chibaanzi 🤣🤣🤣🤣🤣 timadabwa man demo amwezi wamawa kulenge PA 1 amwezi inu iyayi mwatisandusa muno opezera chakundya chanu😭😭😭😭😭😭😭
@InnocentEdasi
2 ай бұрын
Yaaaaaap tidikile kae mayesowa
@DavieMaloya
3 ай бұрын
Bola asadyesoo bazi😢😢
@IssahAluba
3 ай бұрын
Osasitha Deti ifeso zomwe akuchita zikutiwawa iyaaa pakhale pa 10 July pomwepo
Пікірлер: 29