On Nyasa VoiceBox, Mr Samuel Lwara talks about Ghost workers in Government with Leah Malekano on Zodiak Broadcasting Station (ZBS) Exclusive Interview. You can Catch the Rest of the Interview on @ZodiakMalawitv Once it has aired.
Pa Nyasa VoiceBox, Mr Samuel Lwara akukamba zanthu amene amalandila malipilo ku boma koma ntchito yawo yeni yeni siwoneka ndi Leah Malekano pa Zodiak Broadcasting Station (ZBS) Exclusive Interview. Mutha Kupeza Mafunso Ena Onse pa @ZodiakMalawitv Akayamba Kuwulutsa.
• EXCLUSIVE INTERVIEW WI...
#malawi
Негізгі бет Ndine Gardener Ku Statehouse - Samuel Lwara
Пікірлер: 9