Musiyeni vera,ndipo iweyo zikubwerera sikale ,Ili ndi dziko,ndipo ngati iweyo uli ndi umboni osabwera bwanji,ndipo ukudzisakira tsoka,wabodza iwe,mfiti ndi iweyo,aku Banja ife tili pheee iweyo ndani don't use our brother name pandale zanu ayi,iweyo osabwera kuno bwanji ngati uli ndi nzeru
@actuarialscience2283
Ай бұрын
Verah amachindana ndi Chakwera kuyambira kale!!! Imagine mbusa ochinda mkazi wa mnzake.
@HypeGallery-ur9xd
Ай бұрын
Atsilikali nde mwa popular bwanji😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@brightnyirongo3032
Ай бұрын
Kodi atsilikali athu adzichita kukabwereka ndege ku Zimbia a Airborne Malawi
@ChrisjuZiyaya
Ай бұрын
To say the fact mmene boma la MCP likuyendetsera dzikoli,, Ndukuuzani a Malawi akufuna nkhondo izizi ndebelieve me guys.
@PatrickDambo-e5e
Ай бұрын
Mbambande fadah
@fannyzimba149
Ай бұрын
Basi kumanngophana aaaa koma dzikoli mmmm ayi zosayenda 😭
@RitaKainga
Ай бұрын
Ikwere kwambiri blood pressure imeneyo,ikafuna kutsika izitsikanso mpaka pansi,mzimu ndi ena aja plus kasambala,uwaonetse zinthu,A VP akutumbwatuuu eishhhh! More 🔥🔥🔥🔥 Limpopo
ANTHU MUKUSEKERERA ZOPUSA BWANJI OSAWAMENYA A NRB AKAMUUZE CHIKANGAWA WAOYO
@chitanibenito1109
Ай бұрын
Ritchard chimwendo asmatiophseze machende akeso zopusa basi tili ndi ufulu tu, Ayiwara zomwe ankapanga nthawi ya Dpp Mesa amagona ku msewu amenewa????
@SlindiryLoveness
Ай бұрын
Koma amene mukumvera ntanyiwa ndinu zitsilu za anthu chimunthu chaboza kwambiri ichi koma galu iwe uziwe kuti yizakupha bp galu iwe ndimaboza akowo galu yiwe chitsilu chamunthu iwe koma uziwe uzapanga manyazi chakwera atawinaso iweyo siuli kumalawi koma ukufuna kungogawanisa ntundu wamalawi mbuzi yamunthu iwe ukutinyasapo mumalawi anasegula maso panopa sapanga mademo aumbuli zaziii
@SleepyAnteater-bh5zo
Ай бұрын
Iwenso ndi galu Kodi mavuto Ali kumalawi kuno nsukuwaona pathako pako mphaka iwe akawinanso a mcp achita kubela ifeti Mr chikangawa nsitikuwafuna ukamalakhula uziyamba wanganizila athu akumudzi kt akukhala bwanji ndi momwe dzikoli likuyendela
@spargomw
Ай бұрын
Ngat sufuna kuvetsera Ntanyiwa ndibwino kukhala chete osatsekula Radio ya Limpopo. Sasamba iwe, kafucheche wachabechabe. Ulibe Nzeru, ngat umalandira za Mtukula pakhomo, ife zisatikhudze
Mpaka kumpha asilikali zakhala bwanji our soilder go and check what ntanyuwa say wamisala anawona nkhondo anthu owoneka ngati amisalawa amaulura zisisi zobisika mwa modzi ndi ntanyuwayi akutiuza zobitsika uyu kuti mdziko lidziyenda bwino even government waiting timphudzile kuti ku malawi zibwana ayi tikufuna mtendere ndi chulungamo.....
Пікірлер: 101