Anthu nonse muli pa ndandanda oti muphedwe akunama amenewa moyo wanu uli m'manja mwa Mulungu amene amadziwa za moyo wanu mbuzi za wanrhu adziwona sanati
@daviealabi
10 күн бұрын
Nkhangaaaaaaaaa zaonaaaaaaaaaaa
@fridaygonela
10 күн бұрын
Joyce chitsuro wathamangitsa nzake opikisana pa mp pomupatsa transfer emwe ndi phunzitsi kukamusiya ku thyolo from mwanza west mumudzudzule
@IreenMughogho-z6f
11 күн бұрын
Ameneyo nde nthanyiwa
@marthampunga-r8w
2 күн бұрын
Comrade mumachulutsa nyimbo lkkkkkk
@HamzaMkwanda-bh8dc
10 күн бұрын
My best radio limpopo FM ndi COMRADE NTANYIWA continue
@alexsumani6823
10 күн бұрын
Comrade Ntanyiwa we need to talk 😂😂
@LilianKachala-yz2xf
10 күн бұрын
Takumvani AComured May the Almighty God be with you
@AmandaMdladla-xu9im
10 күн бұрын
Ur the greatest big up
@MussaChilembwe
10 күн бұрын
Welcome back mr comrade ntanyiwa mumakwana kwambili chifukwa timamva true story from you not this others
@raytavares2256
10 күн бұрын
What is the time and date today????? P I need to can someone tell me in which year are we???
@ajasikalonga3210
11 күн бұрын
Nkhanga zaona woyeeeeeeee🎉🎉🎉
@zwiigama1980
15 сағат бұрын
IAm following everyday bro.
@MoosaSame
10 күн бұрын
More fire big man ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉
@ExcitedFallingLeaves-mv3cf
10 күн бұрын
Kuyipasa moto Limpopo AFM awesome big up ❤
@arafatMtyala-bo8ev
10 күн бұрын
Big up Mr mtanyiwa
@PhilaNtozakhe
3 күн бұрын
No one mr ntanyuwa continue
@JuliusBenson-qd1jb
11 күн бұрын
Tiri pa mbuyo panu bwana😂😂😂😂😂
@MuhajirAnusa
10 күн бұрын
Koma mtanyiwa amwene ndi nkhani zina😂😂 ❤ you comrade
@Nelsonmatenda
6 күн бұрын
Limpopo fm great radio
@FelixChikola
7 күн бұрын
Tiyenawo awone nyekhwe
@StaffordKamanga
10 күн бұрын
Lankhulani bwana a Malawi amve , akhalenso tcheru.LongLive bigman.
@WarriorKB-u3k
6 күн бұрын
Comrade tikupemphelelani dzisilu zimenezi dzisabele chisankho adzipita chikangawa ndi MCP yakeo aluza kale asatitayise nthawi a MCP nonse ndinu dzisilu kwambiri
@amontchuwa6876
6 күн бұрын
Bola msafooke kalankhula poti ambiri ali ndi mantha kunena chilungamo Ndiochepa olankhula chilungamo amaopa kt ndiyambila pati Ineso ndili ndi chikanga polankhula chilungamo
@KennedyPhiri-h9h
10 күн бұрын
❤❤ munasowatu a Limpopo FM 🙏 timakudyadila
@milliambandah1939
10 күн бұрын
Ntanyiwa 🔥🔥🔥kuti buuuuu!!! 💪💪💪
@YammsyZebron
6 күн бұрын
Ntanyiwa more fire💯👌
@BandahLemos
7 күн бұрын
❤
@NickUpoche
10 күн бұрын
Mmatiimalira Mr Ntanyiwa
@ErickSaidi-sc4mp
10 күн бұрын
Mr pangolin wathu😊😊
@NancyNyelenda
11 күн бұрын
Umakwana big man
@ErnestChansa
10 күн бұрын
More more fire 🔥🔥 comrade tanyuwa🙏🙏 mulungu iwe tanyuwa azikusogolela
@AbudulJohn
10 күн бұрын
More 🔥 comrade Mtanyiwa inu ndiye Zodiac yathu timakunyadilani
Пікірлер: 202